Ain't a fun of politics but minister uyu wayankhula m'malo mwa DPPyo wayankhula za nzeru. As for Usi. Let him do whatever he is doing. There are unseen issues going on in his life.
Tinanena kale kuti manganya ndi wa mcp ndipo ndi mmodzi wa anthu amene anapha cilima ku utm kunali kongobisalira suyi waulula yekha manganya ndi yudasi. Eeee boma ndilomweli la mai wace manganyayo
Nthira kuwili Micheal usi
Kanapelekera dzida kuti chilima aphedwe kamunthu koyipa kwambili kachokeso ku seventh day.
Tinaziwa kale kuti usi ndi wa Mcp Palibe chodabwitsa apa
Mulungu salakwitsa kalikose awona pomuyika aliyese wokhudxiwa pa ifa ya chilima
Yadasi weweni ,Enafe tinaziwa kale..kuti uyu ndi wa MCP.......ndimachitidwe ake nthawi imene denge inagwa ku Chikangawa 😢😢😢😢😢
Mukhale ndimntendere wanu amanganya chidakukomerani kumupereka chilima kwadani kuti amuphe inunutenge udindo lero mumafuna kutenga mchipanichomwe mukhaleko manyazi ausi ndiyerero mutiuzakuti mwalowa MCP zikomo
Munthu oipa kwambili
Ain't a fun of politics but minister uyu wayankhula m'malo mwa DPPyo wayankhula za nzeru. As for Usi. Let him do whatever he is doing. There are unseen issues going on in his life.
Usi ndi yudasi
Akhalenso runningmate wa Mcp
Biziwik usile ndi yemwe anagulisa chilima apa wayamba kuonekela ng'amba tiyenazo wasala ndiwe chakwelago akukankha thako ngati sidik mia
Uyaphapha Usi
Kandondocha kameneka ndikamfiti ndithu, anampeleka Chilima garu ameneyu
Tinadziwa kale kuti usi ndiswa MCP mkona anamupha chilima munthu oipa kwambiri nthawi zonse anthu afupiafupiwa amakhala oipitsitsa
A Zakeyu
Timadziwa kale kuti Boma ndi lomweli ife a MCP
Koma ufiti urikod ndaonera pa manganya eeee koma😢😢😢😢😢
Palibe kukaikira Micheal usi ndi caen kupha abel sanali wa utm komano his intention ndikutenga utm kuti ilowe komwe iwo anali kale
Boma ndi lomweli 😂😂😂 more fire 🔥
Mnyamata wadyera,komanso hule mbava
Ndimadandaula IMFA ya Biyeni tsiku Lina Mulungu adzatiululira chinsisi Cha IMFA
Ameneyi ndichitsilu
Boma ndilomweli la Malawi koma president tikusintha 2025 😂😂😂❤🎉
Mthiko ndi ameneyo, ndi amene ndimamudziwa
He was never accepted there, I don't think anyone of us would stay in a community where our existence is forced.
Asiyeni awusiwo nawonso atafunidwe maiko usi chachiziwikire kuyambira kale ndi wa mcp
😭😭😭😭
Takhala tikunena kut azimayi akumayenda ndi Usi aja si a Utm koma MCP lero ndizimenezi
Tinanena kale kuti manganya ndi wa mcp ndipo ndi mmodzi wa anthu amene anapha cilima ku utm kunali kongobisalira suyi waulula yekha manganya ndi yudasi. Eeee boma ndilomweli la mai wace manganyayo
Kodi Usi osangonena kuti wajoina MCP bwanji? Ndiwamtopoladi iyeyu.
Mwatopa kubisalatu lero mwati mutulukire poyera
Tinadziwa kale ife
Mkung,ung,u uwuu
Udasi
Ausi ndi wa MCP
Hamayooo😂😂😂😂
Opepela😂
Mwachindule manganyayo ndi vhitsilu kwambili ndipo galu
Kkkkk tinaziwa kale after atamupele skc kuifa
Uyu ndi mfiti ndithu
Ok zabwino zonse
Munthuoyipa usi unamupereka usi
Usi alibe tsogolo pa ndale
Eeeee koma ndale amweneeee.....
Wachitabwino kape ameneyi
Umanganyayo uthela komweko
Ndiwe galu kwabasi unyaa uona
Uyu nd wa chkangawa ndkale
Yudasi uyu ,akathera komweko
Wakupha uyu
😂😂😂😂😂
Yudasi galu uyu
Judas