A Chakwera Ku UNGA Awagwila Kuti Ndi President Wabodza - Samuel Lwara

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 155

  • @YousufMpunga
    @YousufMpunga Місяць тому +26

    Tiyeni tonse tigwirane manja ndi a cided Malawi first tonse tilowe pamseu achoke anthu amenewa

  • @LevisonJere-s7y
    @LevisonJere-s7y Місяць тому +6

    This guy i have been listening to him for a whie he always talk sense

    • @AugustineTheu-of6nv
      @AugustineTheu-of6nv Місяць тому

      Am looking for his number Lwara is not just a person he is sensible

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Місяць тому +11

    Auzeni kt ifeso kuno sitimakhulupilila chifukwa anatiuza kt ndenge yafika kudzuzu km sinafike😂😂

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi Місяць тому +14

    Chakwela chimafuna iye kujambulisa basi anachoka banja luvitika akuxipepesa galu amanei

  • @HarriePearson
    @HarriePearson Місяць тому +2

    Good speech mr Rwara thanks we need people like you

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Місяць тому +1

    Well spoken Mr lwara

  • @Maxielyie
    @Maxielyie Місяць тому +3

    Powerful speech ❤❤❤

  • @AugustineTheu-of6nv
    @AugustineTheu-of6nv Місяць тому

    You are brilliant and wise my brother

  • @ThomasMaulana-u4p
    @ThomasMaulana-u4p Місяць тому +2

    This government is seriously ill, they know what they are suffering from,,,, but they can't give up,,,, just beacause of greedy. As for the whole nation its a shame.

  • @LesterGamula
    @LesterGamula Місяць тому

    Powerful words

  • @DanielZunguza
    @DanielZunguza Місяць тому +3

    Zitsiru ndinuyo amene munavotela chakwera,,ife tingapange zopusa ngati zimenezo!!!mbava ngati ameneyo.

  • @TottiesJackie
    @TottiesJackie Місяць тому +3

    Comrade Lwara this man Chakwela is not good enough to be a leader

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 Місяць тому

    Very Powerful Speech ❤❤❤

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf Місяць тому

    Takumvani Mr Luwala.pepani mwelaimadzi

  • @StanelyPhiri-kg1ix
    @StanelyPhiri-kg1ix Місяць тому

    Let's give Chakwera a second chance .He is developing our nation

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza Місяць тому +1

    ALwali bwanji? akamabwera komwe wapitako bwanji osapanga ipichi please. a.comrade Lwali enough is enough ❤❤

  • @cassimediward4713
    @cassimediward4713 Місяць тому +1

    Mbuli ya president and all ministers kuba basi

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g Місяць тому

    Bolaso ine nkhoza kuchita bwino pa upresindent 😊😂

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo Місяць тому +2

    Chakwera waonjeza ndi president osathandiza sindiziwa ngati amaganiza chimene amaziwa iye ndi kuyenda kuononga ndalama pamene amalawi akufa ndi njala

  • @MathewsRedson
    @MathewsRedson Місяць тому

    Nice talk

  • @RargieMediaclassic
    @RargieMediaclassic Місяць тому +4

    Tsutsanitu a chimwendo banda ngat akunjao akunama. Chakwela wanuyo wagwidwa ufiti kunjakonko kut nditambwali komanso wabodza mmene ife timanenera kom makani okhaokha ndi chimutu ngat yellow banz

  • @AndrewManna-l6x
    @AndrewManna-l6x Місяць тому

    Tell us your point!

  • @LawrenceNdala
    @LawrenceNdala Місяць тому

    Nkhani mungolirira Federation basi......kulirira kwanu kwa nthawi ndi nthawi!

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 Місяць тому

    Powerful 🎉

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 Місяць тому

    Kodi paja ndege idayenda bwanji from LL to Chikangawa😢😢..... Waiting

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm Місяць тому +1

    Mau amphanvu 🙏

  • @shattamoxy2393
    @shattamoxy2393 Місяць тому

    The Best thing is to Stop Paying Tax ....Komanso Tigawane Dzikoli Basi .... We're tired with these Fools.......We the Northerners Lets us have Our Own Government

  • @SolomonMumba-i5n
    @SolomonMumba-i5n Місяць тому +1

    He has indeed worsted our time n energy. We are all sad as Malawians

  • @stanleymdala4003
    @stanleymdala4003 Місяць тому

    I agree with Samuel Lwara your critical assessment of Chakwera is spot on.Malawi under Chakwera is going backwards because of this useless and clueless leadership. He is busy buying deadwood from desperate so called opposition politicians into his underperforming administration which hasn't been effective since they moved into government. Time is almost there to kick out idiot Chakwera. He has let Malawi down. Get rid of this stupid man.

  • @CharityGoza-vi6qx
    @CharityGoza-vi6qx Місяць тому

    Ndipo anthu onsewo akukapangako chani kumeneko? Dziko lathu ndilomvetsa chisoni.

  • @Mwenda-sr9ro
    @Mwenda-sr9ro Місяць тому +1

    Anthu akufa ndi njalla chakwera kuononga ndalama za amalawi

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e Місяць тому +2

    He went to vote for Israel and to make money for himself

    • @RosinaPatel
      @RosinaPatel Місяць тому

      Uchitsilu kukabvotera kuti anthu aziphedwa ku palestines..umunthu ndi chisoni alibe..mulungu akukang'antheni

  • @WesleyAnub
    @WesleyAnub Місяць тому

    Kodi achimwendo sukulu analekeza pat

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza Місяць тому +3

    Zowona chakwera amapanga nsanje ndi anthu ophunzira komanso wozindikira ndi chifukwa anamupha chilima

  • @ToweraMfune-pk9on
    @ToweraMfune-pk9on Місяць тому

    Nsanje yikuphani a Lwara. Zinamani mulipidwa ndiokutumani. Ikani apa zomwe akunena kunjako Ufiti ndiumenewo

  • @DavidMalewa
    @DavidMalewa Місяць тому

    Koma kumbukirani kuti Lazalo ankanena kuti sadxiwa kulikonse koma tidasankha kusamva lero ndiizi angoyenda ndibanja lake lonse kudya misonkho yaboma la Malawi, indeed very shame

  • @Felie-p7l
    @Felie-p7l Місяць тому

    Mmmmmm so sad ambuyeatiendele amalawi tavutika

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal Місяць тому +2

    Akuthawa milandu amenewo achikangawa party sikuti amapitila msonkhano ayi

  • @VeronicaMatiki
    @VeronicaMatiki Місяць тому

    Koma A Lwara kuswa kuswa kumeneko

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel Місяць тому

    Kungoononga ndalama kutenda maiko osiyanasiyana zopanda phindu

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho Місяць тому

    Munthu angasankhe Zikhale Ng'oma ndi Harry Mkandawire kukhala nduna, ma crooks okhaokha.

  • @Tamandanipasuli-ci1no
    @Tamandanipasuli-ci1no Місяць тому +2

    Chakwela watitopetsa ife

  • @memoryziyaya2593
    @memoryziyaya2593 Місяць тому +1

    zosaendatu eeeish..
    feel very sorry &shameful
    may God help us 👋

  • @KhumboChirwa-z2u
    @KhumboChirwa-z2u Місяць тому

    Police chilichonse chanzeru apa, it's just a campaign platform, useless one for that matter,

  • @OsmanYusuf-u1v
    @OsmanYusuf-u1v Місяць тому

    Ife nde anatinamiza kale kut ndege yafika kunzuzu

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g Місяць тому

    Achimwendo banda achimwene anga mwadzuka bwanji

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Місяць тому

    Wina wadyako nkhumba kutengeka mmmmm

  • @DumisaniMhango-e4i
    @DumisaniMhango-e4i Місяць тому +1

    Wamilomo ikulu ikulu ndiutiyo kod😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe Місяць тому

    Oyankhila ndiye akutankhula koma ine sindikuonapo chosinthika china chilichose antaa,kumangoti amalawi tiyeni tigwilane manja koma cholinga chogwililana manjacho sichikuchitika

  • @tamikathadzi
    @tamikathadzi Місяць тому +1

    He's such an embarrassment. He should step down....

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Місяць тому

    Anangotenga mudzi onse wakwao ku Kasiya ndamvanso gule wakwera nawo ndege kkkkk tiziona

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu Місяць тому

    Ndi zoona mu cabinet ya chakwera ni mbuli zokha zokha, sakudziwa zpmwe akuchita. Chakwera azipita basi. Akungotiwonongela misonkho ya a Malawi.

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 Місяць тому

    Ndi chimuthu chaboza ichi Mr chikangawa ifeso sitikuchifuna chinatinamiza kt ndege yinafika ku mzuzu koma siyinafike 😂😂

  • @ROSEKATHYOLA
    @ROSEKATHYOLA Місяць тому

    Olo atolankhani sakuyankhuako ayi kuchokera Ku ungako Mesa tolankhani amalankhulira amalawi aziziwa chomwe akupanga kumenekoko

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 Місяць тому

    Ok ndiyekuti bwana chakwerawo ndi abodza koma sangapose iweyo ukutinamizawe ndi nsanje yakoyo boma ndi lomweri komaso opposition ndi yomweyi sitikusintha

    • @SelediaNdilowe
      @SelediaNdilowe Місяць тому

      Akudyetsan zngat agalu inu

    • @alexandermeke6994
      @alexandermeke6994 Місяць тому

      @@SelediaNdilowe ifetu sitisapota zopusa ngati enanu kamba Ka zipani zanuzo koma kuziwona momwe zilili yesu ankuuzani kale mudzawona izi, njala nkhondo,matenda ndi zinazo koma mwasnkha kuti ndi vuto la atsogoleri aaaaa misala

  • @WitnessCharles-s7p
    @WitnessCharles-s7p Місяць тому

    Wakuba ndi wakuba

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Місяць тому

    Eshi atiyakhulira bwino athu Aku unga bwanji

  • @FlechaChipeta
    @FlechaChipeta Місяць тому

    Chakwera panyopako iwe chakwera wakuziwa kupha wanthu basi chakwera manyeghako

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 Місяць тому

    Wabodza iwe

  • @josephalfred5138
    @josephalfred5138 Місяць тому

    Just tell them to come back zitsilu Za anthu

  • @UmaliMmussa
    @UmaliMmussa Місяць тому

    Achakwera idayenda bwanji ndege yopanda Battery

  • @LucyThambo
    @LucyThambo Місяць тому

    Mau anzeru abambo awa ndipo andigwira mtima, Ndale zizikhala ndi anthu axool

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g Місяць тому

    Koma chikangawa ayi mau nilibe😕😕

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g Місяць тому

    Osangomuchoselathu bwa

  • @RamusiCassmu-m1x
    @RamusiCassmu-m1x Місяць тому

    I think mkuluyu sizimaendadi basi how can you kutenga anthu more than 50 how anzanu akutenga awiri okha basi ife beging yatitopera eti kkkkkkkkkkkkk poverty is a big problem in Malawi

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza Місяць тому +1

    Akuwona ngati akakhalitsako ku Unga ko anthu tiyiwala kukamba za report ya ndege, nde ena mkumati boma ndi lomwelo nonses mbuzi za anthu ntchito kuba misonkho ya anthu

  • @AlexKatete
    @AlexKatete Місяць тому

    Mbuzi yamunthu chakwera

  • @MeriaMasinga
    @MeriaMasinga Місяць тому

    Chikangawa

  • @crytoniegrantliffa2431
    @crytoniegrantliffa2431 Місяць тому

    Chakwera ndi munthu wosadziwa inu.........mcp ngati ikufuna ku wina 2025 chakwera achoke basi

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k Місяць тому

    Chakwera ankawona ngat u president ngopweka yona mmimba mwansomba kkkkkkk mutu wajama kamba kothawa ntchito ya murungu

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x Місяць тому

    Auzeni kuti chakwera anatenga boma kulisi munyumba mwake mpkana kunena kti tikamatenga mchenga tizisonkhela misonkho awa achakwera bola mwana wanga nda bala zana pano ali ndi two days

  • @gibsonkhumalo6649
    @gibsonkhumalo6649 Місяць тому

    Galu jiwe akutuma akukuuxa ximenrzo ndindani

  • @BrownMaseko-f2h
    @BrownMaseko-f2h Місяць тому

    Chakwela alibe usogoleri woyendetsa boma 2025 abwerere ku ubusa basi,koma chakwela watikwana kwabasi

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n Місяць тому

    Ndipo ochititsa manyazi

  • @JosephMfuni-r1d
    @JosephMfuni-r1d Місяць тому

    So far you are not clear as to exactly what you mean by "akumukaikira" bcoz you are giving no examples things about which akumukaikira?

    • @GerardFelixDyson-tp1sp
      @GerardFelixDyson-tp1sp Місяць тому

      Tamamvani kuti he is mfundoless kumeneko. Koditu opemphedwa amaona munthu zomwe akuyankhula. Ndo okaikitsa president wathu

  • @JulietMunthali-g9b
    @JulietMunthali-g9b Місяць тому

    Chazelezeka chichakwelqcho

  • @VincentMudoda
    @VincentMudoda Місяць тому

    Angomuthamangisako kumeneko

  • @LewisFrancisco-o3b
    @LewisFrancisco-o3b Місяць тому +1

    Chakwera is evil

  • @LimbikaniMakwandu
    @LimbikaniMakwandu Місяць тому

    Bodza ,nsanje imeneyo

  • @innocentkandulu2825
    @innocentkandulu2825 Місяць тому

    apita kopempha ndalama zokuti abe aziyike mumabanki awo

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l Місяць тому

    Tauzani Enawo poti dzitsilu zina zikuti Boma ndi lomweri mbuli zawanthu Amthakati,,,,komaso Saonera ma TV

  • @JusticeKalemba
    @JusticeKalemba Місяць тому

    Lwara pangolin weni weni

  • @FrankJumah-l7f
    @FrankJumah-l7f Місяць тому

    Sakumunamuzila

  • @BrightZionga
    @BrightZionga Місяць тому

    Chakwera ndi mbava

  • @JesseKanjanga
    @JesseKanjanga Місяць тому

    Aiuzeni cilungamo kuti ndiwabodzadi ndipo ndiciphe

  • @HalimaDamiano
    @HalimaDamiano Місяць тому

    Galu chakwera

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g Місяць тому

    Samamva zamunthu lazarous

  • @IdreesahManyamba
    @IdreesahManyamba Місяць тому

    Chakwera atipwetek uyu kobasi tiyen tisampatsenso mpata amney this coming 2025

  • @DauglasBowa
    @DauglasBowa Місяць тому

    La 40 Latsala pang'ono kukwana

  • @IbrahimDailes
    @IbrahimDailes Місяць тому

    Galu chakwela opusa kwa basi president wa mkabudula mbuzi ya munthu

  • @SurprisedDarts-di6fs
    @SurprisedDarts-di6fs Місяць тому

    Sukunama

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi Місяць тому

    Larwa kkkkkk akulu mitud

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson Місяць тому

    Kodi inu munali kuti athu oganizi bwino. Osamasapota nyasi za mcp👹

  • @RargieMediaclassic
    @RargieMediaclassic Місяць тому +1

    Chakwera ndiinetu bola ine ndingayeseleko kutsogolera bwno kom osat mbuli yomphunzirayi.ndi kape watuthu...very useless person 😢😢😢

  • @HenryNanthuwa
    @HenryNanthuwa Місяць тому

    😅😅

  • @Mcfiedmwanja
    @Mcfiedmwanja Місяць тому

    Koma ku opposition simasewera kkkkkkkkkk musanati ndipo musayembekezere kuti akupatsani chitseka pakamwa chifukwa chooti mwalankhula. Munya muona

    • @JanuaryGwere
      @JanuaryGwere Місяць тому

      You don't know nothing that's why ukulankhula mopepela

    • @ThokoIChinsinga
      @ThokoIChinsinga Місяць тому

      Lwara ndi wa MCP musaiware si wa opposition.

  • @mbonilekisebe2286
    @mbonilekisebe2286 Місяць тому

    Chakwera is a headless chicken. Empty tin, the dumbest president Malawi has ever had. Gule adzipita kwawo Basi. Kuzolowela kuvala nyau.

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 Місяць тому

    😂😂😂😂 chisilu chakwela

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi Місяць тому

    Koma chakwela ukutionesa nyekwe

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 Місяць тому

    Koma yah mmmmmmm ziliko