Koma change goal ndi akatundu,koma congradulation joab yr so gud jounalist umatha kucheza ndi anthu kuti amasuke kusiyana ndikumawatutumutsa pa ma interview chifukwa kutelo siungathe kumva zambiri.lelo change goal wamasuka kwambiri kamba ka luso lako joabu.
The previous TA Ndindi was my father Mr WM Matola. He was a superintendent in Malawi Police Service The TA Ndindi that is now is my father's younger brother
Please Joab yesesani kumapangira interview pa malo opanda echo
Kusankha nyimbo mpaka zitatu nthawi imodzi😂
Koma panopa khazikikani a Uladi Mussa mwakula mukhale mentor wa ma young politicians
Koma change goal ndi akatundu,koma congradulation joab yr so gud jounalist umatha kucheza ndi anthu kuti amasuke kusiyana ndikumawatutumutsa pa ma interview chifukwa kutelo siungathe kumva zambiri.lelo change goal wamasuka kwambiri kamba ka luso lako joabu.
Nde mwayi English literature?
😂 first kutokota the whole book then kufunsa mafunso😂😂
In 1993 salima secondary and in 1985 I sang for kamuzu while I was at secondary
One word, akuluwa lidakula ndi dyera la ndalama. Kuyankhula mosalekeza.
Yooh?.
🤦🏽♂️😆😆.
Za covid musamaname a change golo what about Uklain
Zodiak, are you using a calculator to record ? Who uploaded this klap ?😊😊
Bona ndilomweli
Boma ndilomwe
Awo ndi achitsiru
Kaidi iwe boza
The previous TA Ndindi was my father Mr WM Matola. He was a superintendent in Malawi Police Service
The TA Ndindi that is now is my father's younger brother
ulandi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Zodiak Plz Work on Sound , THis is Unprofessional.. Technicians, what are they doing?
When was this
Ine nditenga matongawo 😂😂😂😂 nyama ikuthamangayi
Joab kufunsa nyimbo koma kutchula 4 😂😂😂
Mbuli ya bodza uladi musa
That was a nice program but with poor sound
Dpp was doing well to keep dollars for fuel projects after.
Boma Ndilomweli sitikusintha
Umakwana Joab tambwali uyu afuna akane corruption 😂
Big timati tipephe nawo pa program yanuyi timati mutakacheza bwanji nd kado tamusowa tikufuna tiziwe kut alikut
Paja anapita ku Mozambique kuyambakunamiza anthu KUT ndi sing'anga anabela anthu then anamukwenyako
komatu sound yo zativuta onga masanje
Joab is another level.
Chakwela amakanika kumutuma chilima vice president wake kalikonse anapita yekha anangomutuma tsiku loti amuphe
Anthuwa Amakhwima kuti azingovoteledwa u MP. That's why malawi sizatukuka forever
Ndiwachiyawo uyu akuziti ndi nchewa kuti azigulile maudindo mu MCP poti mu MCP amakondela achewa
no break speaking uladi
Nanga 2 years ku mcp mambership ndi 9 months ku dpp discipline chabwino ndi chani
eee kma sound si ilibho
Uladi mussa katundu, wise talking
First to view and comment
Eya musazabwereso ku chipani chathu chokoma cha DPP....APM my vote
Kma interview iyiyi kkkk😅
Sound engineer mumupititsenso Ku school
Voice yokha yanu Nde ili poor kwambili 😝
poor sound zodiak
Tsopano Inu Abwana Musa mukufuna Anankhumwa akachikuza chipani cha pdp ndiye mudzabwere.
😮
.mnchawa uyu anathwa nkamwa
Joab is a journalist kkkkk
Awawa angalankhule 24hours
Sound nde mbolatu quality
Anthu safunana
Chisilu ichi chadyera
Room sound siilibwino
Poor sound zodiac 😢
Audio has some mumbles
Poor poor very poorly voice unprofessional recorder
Very poor sound
Ku team ya Dpp kulibe amene angamake kwa uyu
Vomerani bwana change golo sibwino kumasintha chipani
Poor recording for Zodiak Joab
Poor sounding
Sound not perfect
Tumva movutikilatu
Poor sound
Sound is bad
Grt
Very bad sound indeed
Worst sound
Poor sound zodiak very poor sound
Phone yanu yofoira
Why you political readers don't put effort on gdp growth domestic products
Wakomdwa mopusa nkului...
Poor sound