I like the story line, yochita kunveka bwino, A to Z, all the Actors very good man, ndinu madolo guys... Malawi is ready for the future, kwangovuta ndikumalo kwake kuno. This is the stuff that needs to trend, ma TV stations needs to air this serie seriously.. big up
Hello guys! I'm from Mozambique, I don't understand Chichewa very well, but I'm really liking, this story is perfect, go ahead... we can also have a great movie industry...❤
I like the story line, yochita kunveka bwino, A to Z, all the Actors very good man, ndinu madolo guys... Malawi is ready for the future, kwangovuta ndikumalo kwake kuno. This is the stuff that needs to trend, ma TV stations needs to air this serie seriously.. big up
at first i was ignoring this comedy but i have watched all episodes from one up to this one. so inspiring next please tudikira
Ngakhale ine koma mmmm ndayamba dzulo kuonela koma simmene ikukomelamo ai❤
Ndipo ineyo ndimangoona ngt ndiyosabeba kma eeee ndikupezamo ma lesson ambiri
Ndayamba kuonera dzulo
But jimmy is straight forward i like his confidence 🤣🤣🤣
One of the best series in Malawi at the moment. keep it up guys.
Lawyer woipa iwe.....let God handle scot situation.
Heavy
Mkazi ongokhalira kupepha😂😂😂😂Kodi ndikatani nawe😂😅
Mi favorites actor Richard.... mumuuze amandiwaza hvy Richard yo🙌🙌🙌
Inuyo mwabwera kudzakhala. I love these series
Hello guys! I'm from Mozambique, I don't understand Chichewa very well, but I'm really liking, this story is perfect, go ahead... we can also have a great movie industry...❤
I just love the fact that you have beautiful ladies who are good actors at the same time
Susana is acting matured, Aubrey didn't deserve her
Exactly
Or mpang'ono
Aphwedo mwana akudelera uku
Bwana Scot mwayamba kukhulupira Mulungu lero zinthu di zimasintha😂💔🙌
😂😂😂akundisekesa bwana scot
Koma ndipo
Moti iwe suumandifila😂 aaah Mwayi ada😂😂
Big mama nawo alandire ulemu ❤
Nice move koma iso nde amakwezedwa kwambiri
Akut zaka 16 years eeee kkkkk😂😂😂😂km amalawi tikutsalirabe kuyakhula kwabwanj kumeneko zaka 16 years kkkkk
😂😂
Ladies muzilimbukira kusaka coz mutukwanika😂😂😂 Jimmy🔥🔥🔥
Kunja kuli anthu oipa uku Scot alimunyengo yoipa yomwe ikuoneka kuti Jimmy is involved
Susana muli fundo pa ekha, pakatha zaka 5 tizizat tagonjetsa chan??
Jimmy nailed this episode 😂😂😂Ana ama skin😂😂
Iiiiiiiiiiii Jimmy mpaka ndalama yomaliza ndi iyi ya drinkyi😂😂😂😂😂❤ iweyo ndi Galu
Mwana wavala vest ya red ndi ujah wa xool days eti
Atiii kayaa nalakwisa kukhala okongola🤣🤣🤣moti iwee sumandifila?
Susana your a good actress❤
I like Susana in this episode she is dope 😍 nc acting keep 🔥 burning
Ati ndimatani nako akaka🤣🤣 Jimmy🙌
So Richard kuyankhula kuja munatengera uncle jimmy😅😅😅
Jimmy anakonza😂😂
Ndapanga Follow Ma Episode onse Guys ur the best Actor's❤
Dan ndiwopepera kwambili akumuzuza Richard
Mukumachedwatu kutulusa pakana tikumaiwala kuti kuli dear x bwanji kod zithuzi zimafunika kut kutumiza muthawi yake kut aku aziyisatila nde sapotiyo
Lachitatu ndi Saturday basi. Dikilani mawa.
Ati matani nawe iweyo😂😂😂😂
Ana amasikini😂😂
As always beautiful bangers....i think i deserve a top fan badge...been a fan since u were uploading on tiktok
Ndee Jimmie akufuna mowa uwiri koma alipo yekha,,, bwanji kumaitanisa 1 by 1 😂😂 kuochosa Kaye mu fridge kuika poteropo utenthe Kaye kkkk
Bayala salakwitsa kkkk
Kaya ndinalakwkitsa kukhala okongola😂😂
Umumu nde mulibemo kape guys team yosulidwa bwino
Dan 😂😂😂😂😂 ku garage kumagunika ma spenara kkkkkk muuze reach adziwe kkkkkk mo 🔥🔥🔥
Scott sanabe ndalama,, Ndalama anaba ndi Jimmie
Kod kut munthu uzipanga nawo zimafunika chani abale 😢titengeni tidzipanga nawo
Momwe akumusungla majidu wanga ku police szkundsangalasai😅
Nde mwati kulakwitsa kukongola
Susan's character 🔥🔥🔥🔥🇲🇼🙌
Nde mau a chard muli confidence ❤❤
Mukhozaso kutengaso ka drink muzimalizitsa munjira
Guys mukundinvetsa kukoma sicot khulupilila mulungu chilungamo chiyende ngati madzi
Komatu mtsikana uyu ..kukonda ndalama😂zikupha
Kaya nnalakwitsa kukhala okongola😂🤣
ine nde pazandivuta kuima kaye za studio mkuyamba zina kaye eeeeeeeeeee zinandilowa kkk muli bho ma guys
😂😂😂 Jimmy. Straight forward
Akt ndalama akagule ma spanner ku garage😂😂😂😂😂😂
Anyamata awa aphana
Next guys Tione ku khefu ko 😅😂😂
🔥🔥 next please 🥺 maguy awa ndimadolo
mmanja mwanu guys !...Full of goodies.
Iiih koma Jimmy amayankhulitsa😂😂😂
Eeee koma zithu zimasithadi scot mpaka kudziwa mulungu
These brothers 😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 Naye Dan ndipha muthu😊
Koma Jimmy akuti akaka ndimatani nako.....Akuti nkazi wongakhalira kupepha ndi tani naye koma Jimmy umalalata
Sakulalatayi kma akuyankhura chilungamo atsikana tikunyanya kwambri.....m'malo mopeza zochita ntchito kupempha basi .
Ana maskin😅😅😅 koma jemmy amandiwazaa
Eeeeee kma Jimmy umayakhula😂😂😂😂😂
Best Malawian serie ever
Madhala Jimmy kwatiran mwakula😂💔
Jimmy mpaka ana ama skin😂
🔥🔥🔥🔥
😂 😂 😂 😂 😂 it's giving
Eeh koma jimmy amanyoza😂
❤️❤️❤️❤️🔥🔥🔥🔥
Richie, umakwana❤️
These brothers🤣🤣
Jimmy😂😂
Susana and Aubrey sopano😂😂
Fatsani is a good actor
❤❤❤❤❤❤❤
😂😂😂 big Mama 😂😂😂
🔥
Iwe barman bweretsa uwiri
Aaaa mwayi😂😂
Fatsani mwana wachabe
ana maskini 😂😂kagwereni
Ati ana amasike😂😂😂
Ana ama skin 😅😅😅 km Jimmy asee
koma Jimmy muli kunyoza😅
Jimmy wayaka bwino
Tabweletsa uwili
Ana amaskin
Richard anatenga jimmy kuyankhula
Indee amai 1kg yanyama sagagure amenewoo
Aubrey😂😂aaaaa
Ati moti iwe sumandifila😂😂😂
Kkkkkkkkk koma Jimmy kulalata
Komatu Jimmy umalalata
waiting for ep 10 can't wait
Next please zikubeba
Akuti ......Ana amasikini....koma yaa ,
Episode 10 please am failing to wait😂
Dekhani kkkkkkkkkk
Nice comedy
Kodi episode ilipo abalee
kkkkk tili ku cafe