Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Wapolice usamale 2025 timaziwa kwanu ngakhele mai Ako komaso family members yanu posachedwepa Tipanga za inuyo......
Komatu amayiwa ngati alibe maganizo azachinyengo zilizonse akanatula pansi udindo ndithu a usi ndiye olo atapanda kupereka zikalata zawo alibe ntchito coz ndiye amangooneka kuti mu UTM anachokamo kaletu. Kumakamba za chiliza chonsecho boma likutenga ngongole zogulira mafuta. Ukuku nkuganiza mombwambwana coz izizi sizoona panopa mu dziko muno mukuvuta zinthu zambiri ndiye azitenga ma bilion nkuumati yomangira ziliza za ziiiiiih. Boma ilili ndi lolephera kupanga ziganizo zothandiza amalawi kumawavuta. Coz munthu mnyumba mwako ukugona ndi njala, ukusowa transport and suli financilly stable uzikapanga ma budget achiliza cha ndalama za nkhaninkhani kupha amalawi ndiye kumeneko ka mtima kokuba kameneko cholinga azinama kuti ndalama tinamangira chiliza kuganiza kwabwanji uku
Powerful gays keep it up
😂😂😂😂😂 ndasekaaa kk😂😂😂
Ndiposo atengele ku Mozambique 🇲🇿 zimayambatu choncho Annabelle mtalimanja atulepasi udindo amenewo ndima judge afake aja mwa moziso ndi iwowo
Tatiyeni uko zaluza kale za opposition mukusapotazo
Atulebas
Mayi mtaba nawonso ndi jaji koma anakana kuweluza mulandu wa mr mtaba powaganizila kuti amapha alubino kamba koti mr mtaba m,bale wawo ndi Mayi mtaba
Mwalankhula zomveka bwino
Atuledi udindo ayambisa nkhondo sizoona kuti mwana wa john tembo angalole kuti mcp iludze
Chipani si cha munthu ndi cha aliyense malamulo atha kusintha anytime, zikungovuta kuti mwini wake anapita
Just bring neutral chairman rather izizi zokhala sided
Atuledi pansi udindo angazayambise nkhondo look panopa ku mocambique
How do people in the same house investigate themselves?
Ndiye aJudiciary ansanka mwana wa Tembo. Apresident anasanka mwana wa Tembo. 😢
Akamatula pansi udindo machine a smartmatic achokenso
Upange resign iweyo, MEC Chair zizitheka
Uyutu apanga
Kunena zoona mayiwa sangalole kuti MCP iluze angozitura kuti asakhale pachiopsyeso
Atule pasi udindo basi atalimanja
Chimene tikudabwa ndichoti ainuwake sanayakhe koma a mcp akuthamanga kuyakha amuti achair Sali bias pamene mcp ndi one of the tsake holdets
Tulani pansi udindo.