Unfortunately munthu wakumudzi alibe access to UA-cam and all social media platforms at large to scrutinize mabodza amene akupwetekesa Malawi. Lets wake-up up Malawi. Vote ndiumtima. Tiyeni tizingolimbikira kugwira ntchito, ndale sizipeleka nsima pa tebulo😢. Personally ill vote koma mtima wanga okha ndiomwe ukudziwa yemwe nditakamvotele😢
Brian wanjoyatu ku Mwanza, ķp up the good work.
🎉 but this is only a constituency rally remember that. What about the mega rally guys do not underestmate them
Fanziiiii inalikoooo kwabasiiii koma nkhan nd Bwana SKC munatinyikitsaaaaaa
Gagaga dedede anali pa msonkhano uwu et😅😅😅
😂😂😂😂 koma kumenekoooo!!!!!! Kuyakhula osanyengelera
Abanda mukuonjeza mwamva mumaonjeza mafunso kkkkk keep it up my brother kkkkkkkk
Ndipoo tinataya kale chikhulupiliro ndi utsogoleri uli panowu 😢😢😢😢😢!
Kodi tipange bwanji
U T M kuphupha kumeku
iwe momwe wanenepelamu umalima mkumadalira fertilizer olandira zowona🤣🤣🤣
ndiwe mbuzi yachabechabe
Yomweyooooooo ndalama anakagula nyama zoonadi
Kkkkk wakwanila
PEPANI Mai Jane Ansah muwakhululukire anthu oyipa, themberelo lija laoneka poyera, anthu anzunzidwa mokwana. UTM musatiseweretse a Malawi mukutsutsula Zilonda mudativulaza zija.
😢
Kkkkkkkk chisonkhano chamoto buuuuuu!!!!!!
kanjawala got my vote. Chilima really changed malawis politics
Koma,abale amalawi tinatoledwa, kwambili.zoona,izi.ambulance,yachani.malawi,waipa tonse alliance ndi UTM yalephela.ndipo,kusagendedwa,ndi mwala,aziimba,lokoma.kukupitaku,aona mbwaza
Koma Brian Banda inuyo mutionetsa zinthu 😂😂😂😂😂mumaitha
😂😂😂😂😂apa ndipamene mutaziwe kuti anthu sakukufunani ndipo mukungozivutisa kupanga misonkhano simuzawina ataaaa
Ayambe bodza tsopano
Mmmm koma Malawi
Ameneyu akunam jubek ya itiyo
Ifet tili kinkuno kom ameneyu sindikumudziw akungonamiz anthu zabodz zokh zokh
🎉 but this is only a constituency rally remember that. What about the mega rally
Abweretsa a mbulance chifukwa akuziwa kuti athu amwalira kwambiri ndi njala, chifukwa mmalawi mulibe chakudya.
Kuba mwaba,koma 2025 its better to change TONSE ALLAINCY.
CHILIMA wabesa game...TUPERE MULUZI 2025 BOMA
Utm on fire.
Zaziiiiii,utm inathadi basi
Zaziiii mukutani kukonza mesa muli komweko kubomako
Kkkkkkkk komatu kudya katatu amanena ndiamene mwapitila ku nsokhanowo kkkk
komatu mukutiseweresa kwambili
chilima sangawine ata!!!!
Uzawina iweyo
Unfortunately munthu wakumudzi alibe access to UA-cam and all social media platforms at large to scrutinize mabodza amene akupwetekesa Malawi.
Lets wake-up up Malawi. Vote ndiumtima. Tiyeni tizingolimbikira kugwira ntchito, ndale sizipeleka nsima pa tebulo😢.
Personally ill vote koma mtima wanga okha ndiomwe ukudziwa yemwe nditakamvotele😢
Sogoleri wanu wakubayo
I couldn't wait to see Chilima's next move until today😂
Zazi koma azimayi njala yilitho
Ambulance yo yachipani kapena yawina aliyense mpana kuilemba UTM mwalephela pamenepo
Madness on its pick, kumwanza anthu amadya chamba chokukuta😢
Umphawi siuzantha kumalawi. Za chamba basi. Kumangokhalira kuvina basi ngati zitsilu.
Somba imodzi ikavunda zonse zavunda. Osakakamiza athu zawubwino wanu anthu a kuwona okha. Tizavotela Ena basi😜
Izizizi ndi za utm iweyo wa dpp ukufuna chani? Tiye uko
😂 kkkkk tulani zida pansi join APM
Tikufuna chimanga
🎉 but this is only a constituency rally remember that. What about the mega rally guys do not underestmate
Utm boma mufune musafune
Komatu A UTM muli ndi misala Zedi
Brian banda kukonda kuvala zipewa za atabwali bwanji
Ndikudikira ndidzamve malonjezo a atsogoleri a UTM ndi MCP pakampeni wa 2024, Bola osadzalonjeza zomwe mwalephera kalezi!😂😂
kkkk utm woyee
Brian banda ndi wa aMCP basi ndawona
Amalawi tatopa ndi anthu andale
Chairman wo mwina aledzera
Wamwano
Zavuta basi
😂😂😂 kuli ti anatu ,avote ana omwewo
Anawonso angolondola nyimbozo😂
Kumwanza kwathu kunachema😅
Mama ninth amaiwala eesh
Ndi Andale awa he knows that akazawina his money will be back thats alll
Koma ziliko
UTM also you the one to damage country of Malawi government you talking what
And it is a nonsense ones
Pena kumalembako chichewa kupangila enafe okuti maso anatimana(chikulu
Aaaaa❌❌❌⚠️🤣
Koma anthu kulibe ambilitu
zitsiru zokuba mukuwona ngati mubanso shupiti
Ukundiyeno kupusa how can u bring ambulance instead of bring food
Opusa ndiweyo. Chakudya ndi matenda chofunika mchani?
@@tingamasi106 iwetu misala yayamba kukuzembelela m'mene wakuliramo ungamanene kuti ambulance ndiyofunika kuposa chakudya?
Kkkkkkk
Which joburg? No sense.!
Kkkkkk km Malawi ase😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Chilima mbava kuyankhula kochenjera mwakuba
Koma kosowa chochita really kungopereka ambulance mupakana rally .
Testing the waters.
Imagine ngati kunalibe ambulance
Koma kumwadza kuli anthu Amisala
🎉 but this is only a constituency rally remember that. What about the mega rally guys do not underestmate them