Evance Meleka ft Dr Chilima -Patsogolo official mp3 🇲🇼

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 41

  • @nyasongimhango6337
    @nyasongimhango6337 3 місяці тому +3

    I will always remember chilima ndi nyimbo iyi

  • @fairmpinganjira4496
    @fairmpinganjira4496 3 місяці тому +1

    Rest well Doc CHilima. Inspiration to many

  • @austinmakulun4447
    @austinmakulun4447 20 днів тому

    May soul RIP 🙏🙏chilima munali regend.. Sitidzakuyiwalani

  • @GeoffreyMtope
    @GeoffreyMtope 5 місяців тому +1

    Zitsomo za Yehova zikhale ndinu koma a deputy take note of this song we are together in blood

  • @edinamlinde
    @edinamlinde 3 місяці тому +1

    Tizamusowa Chilima 😭😭😭😭😭

  • @yakamemes
    @yakamemes 3 місяці тому

    ❤Chilima 😢tizakusowani😢

  • @RichardMalunga-dw1oj
    @RichardMalunga-dw1oj 3 місяці тому +1

    Rest in peace Dr Chilima

  • @richiePushie-hq5cy
    @richiePushie-hq5cy 3 місяці тому

    Rest well Legend 😭

  • @yamikanimdala5955
    @yamikanimdala5955 3 місяці тому

    The hope of Malawians has gone too early zatipweteka kwambiri. Mzimu wa dr Saulosi Chilima ukause mu ntendere osatha😢😢😢

  • @anthonysaidi5636
    @anthonysaidi5636 2 роки тому +1

    Kkkkkkk umatha iweyo adah,
    Akaka mumponyerenso chilimayo

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 4 місяці тому +1

    Musiyeni mulungu akhale mulungu ana agogo patsogolo muzachita manyazi ma plan A mulungu safanana ndi munthu wina

  • @saulstafforddube
    @saulstafforddube 3 місяці тому

    🇲🇼 malawi tisawope anatelo saulos chilima Rip 😭😭

  • @blessingmanda
    @blessingmanda 3 місяці тому +1

    rest in peace champ

  • @SamsonKamgusha-gp5fw
    @SamsonKamgusha-gp5fw 3 місяці тому

    Mulungu wanga ine

  • @AidaGremu
    @AidaGremu 2 місяці тому

    Rest well chilima

  • @PromiseChidzungu-x4y
    @PromiseChidzungu-x4y Місяць тому

    💥💥💥💥

  • @binwellchunga4986
    @binwellchunga4986 2 роки тому +2

    koma chimene chandisangalatsa kwambili munyimboyi. Mmmmm zida guys mwazigwila bwino kwambili

  • @CharlesMbewe-qo2hm
    @CharlesMbewe-qo2hm 3 місяці тому +2

    Rest in peace Hero. SKC

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 8 днів тому

    Continue rest in peace

  • @hamdanmasuku4800
    @hamdanmasuku4800 Рік тому

    Uvance pitilidzan kumatiyankhulira ife a Malawi akumudzi

  • @rashirdyusuf6111
    @rashirdyusuf6111 2 роки тому

    Amen 🙏 km chilima ulape wamva wande zawhiti iwe galu wamuna

  • @shaziyarodrick631
    @shaziyarodrick631 2 роки тому +1

    Olakkwa ndiovotera Chilima ndiobalalika Iwo samadziwa😂😂😂

  • @paulnkhama3621
    @paulnkhama3621 2 роки тому +1

    Kungoziwa kulalata kuyendesa dziko kwakunyelani

  • @muuse7481
    @muuse7481 Рік тому

    Zisilu zaandu💔😭🙏🕊️

  • @williammhoni5729
    @williammhoni5729 2 роки тому

    Nyimbo yabwino kwambili man

  • @janemanyamba7201
    @janemanyamba7201 4 місяці тому

    Ndi zoona koma?

  • @drbanda6105
    @drbanda6105 2 роки тому

    Big. Boos

  • @muuse7481
    @muuse7481 Рік тому

    Don't trust anyone because when someone to come to your life mum's not hot she needed something to you

  • @giftkungani8072
    @giftkungani8072 Рік тому

    Ndamva kwatuluka yona ndikuyisaka sikupezeka
    Ndikhoza kuyipeza motani?

  • @christopherbanda3529
    @christopherbanda3529 2 роки тому +1

    I can’t say anything because Malawi 🇲🇼 its just hell

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 4 місяці тому

    Dziko aononga achakwera and chilima basi chifukwa chama bosa

  • @shafiamidu6573
    @shafiamidu6573 2 роки тому

    Kd big sumakonda kuyika pa video bwanji

  • @leviphiri1547
    @leviphiri1547 2 роки тому +1

    Dziko linaonongeka kale akhala zaka zingati. Munaononga dziko ndinu osati chilima kapena chakwera. Ndalama zonse munachosa mu boma.

    • @piliranimphepo1920
      @piliranimphepo1920 2 роки тому +2

      Ine ndidziwe nawo abale, mukamati ena anachotsa ndalama m'boma kodi iwo ndalama zolipilira ndege ija amachita hire nkumapereka 10,000 USD per hour zija amazitenga kuti? Bomatu silosauka koma akulisaukitsa ndi atsogoleri (mbava) athuwa

    • @mphatsojere2639
      @mphatsojere2639 2 роки тому +1

      Ndifunsileni abale after 2 years mkumatibe anapeza ndalama mulibe mu mboma?? Ndiye drama iyiii

    • @banetsan9410
      @banetsan9410 Рік тому +1

      Wakuba uyu akumumasura

    • @omarcharlie5247
      @omarcharlie5247 Рік тому

      Nose muli limozi mbava inu mwabamo mwayambampo joice anaba aliyese amaziw alipo antenna anthawa yekha

    • @BendejiesChakaka
      @BendejiesChakaka 5 місяців тому

      Chilima alibe vuto inuu