A Chimwendo Banda Tengani Ndalama Mukonze Chipani Mosangalatsa A Malawi Osati Kuwapatsa Oyimba

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 26 вер 2024
  • On Nyasa VoiceBox, a concerned citizen asked Honourable Richard Chimwendo Banda, Secretary General of the Malawi Congress Party, to use the money to buy maize for hunger-stricken Malawians instead of distributing cash to celebrities and recycled politicians as a means to win votes.
    Ku Nyasa VoiceBox, nzika yokhudzidwa idapempha Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress a Richard Chimwendo Banda kuti agwiritse ntchito ndalamazi pogulira Amalawi omwe ali ndi njala chimanga m'malo mogawa ndalama kwa anthu otchuka komanso andale omwe amawagwiritsanso ntchito ngati njira yopezera mavoti.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 35

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 2 дні тому +7

    Bwana chipani chathuchi chaonongeka ine kuchokela kale ndili mu mcp koma panopa chipani chathuchi chaola bwana, ndipo panopa ndili okhudwa kwambili ndi tsogoleli wathu chakwela, nzelu mulibe kunena choona,ndipo ifa ya chilima ndikaziyan'gana kuchokela pachiyambi kufika lelo mmmm chakwela anapha chilima ,apa palibeso kukhonza bwana athu ndokwiya,chilima amakondedwa, bola akanakambilana osati kuphaa

  • @FelixNyirenda-c4y
    @FelixNyirenda-c4y 2 дні тому +6

    Chimwendo Banda will no going anywhere with his dirty politics.

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 дні тому +4

    Chifukwa ndi ndalama zamasiye zotembeleledwa sizimagwila ntchito azazindikila ali kunja kwa boma ndi zitsilu zokha zokha ku bomako kulibe owalangiza

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 2 дні тому +5

    2025 no more Chikangawa party

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 2 дні тому +2

    Well spoken ndalama zikuwonongedwa anthu tikuvutika,..

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 2 дні тому +2

    M'mene amavutikira a police kukhala 5 days panja ngati kubwera Chikangawa kupangitsa msonkhano kuwapatsa ma 2 thousand koma oyimba kuwapatsa ma million.
    Koma boma kudelera a police

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 дні тому +4

    Auzeni chilungamo malawi walero si wa 2019 anthu akuona patali

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 2 дні тому +3

    Dan analandila 50million taganinzani talama yotseyo ndipo munthu amene wamugulayo zangabwelenze anthu chipani tawonani yemweyo adayimba chimo yoti atule pansi udindo lero akulowa chipani chatu tingakhuluphilile amenye akufuna ndalama zangatandinze chipani dan alibe ntchito kuyimba ndindale ndizotsiyana kwabasi

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 2 дні тому +3

    Ndipo mcp ikupeleka matama chipani cha dpp nanga tawonani dpp inapita kupoto mcp nayotso komweko malo moti asiyeni adpp apange zawo pomwe anthu adazindikila pano amata kuwona olakwitsa tiyeni ife amcp tilongosole chipani km zoti dpp ili kwakuti ifetso komwe ndikulakwa kumeneko mapeto ake dpp izinyawuda kwambiri tiyeni ife tilongotsele chipani nthawi ikadali amalawi akwiya kunjaku tiyeni tanyengelele

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 дні тому +2

    Ndipo awuzeni nkhale zitsili zikumamenya anthu chifukwa cha 5000 kuvina azimai zitsilu akatha nkuwapasa 2000 nkhale nyumba alibe akukhala mma rent zitsilu wina kubwela kuzangoimba akupasidwa 50 million wovina 2000 uchitsilu weni weni agalu..nymba mulibenso ..

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 2 дні тому +2

    MCP ikuononga ndalama oimba uyuyu mpaka kumupatsa mk1.8millins ndi yantchito yanji? MCP yanyanya.

  • @JEFFERYJUMA
    @JEFFERYJUMA 2 дні тому +3

    Truth talk Mr apenga a mcp

  • @KandayaCharles
    @KandayaCharles 2 дні тому +2

    Dzoowona alendo ndi amene akudyelela.

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 дні тому +2

    Facts big man ❤❤

  • @WillamLawson-gk1lw
    @WillamLawson-gk1lw 2 дні тому +2

    No tikufuna agule chimanga kwa anthu ovutika

  • @thokozanindalama
    @thokozanindalama 2 дні тому +3

    nzeru palibe

  • @MusaMatola-r7i
    @MusaMatola-r7i 2 дні тому +3

    Dan lu watha ngat makatani

  • @MlaziJames
    @MlaziJames 2 дні тому +3

    Vote yanga ndi DPP

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 День тому

    Big man ulemu wanu MCP akupanga dzachikale munthu sangavotele MCP chifukwa wina otchuka walowa MCP aaaa otsatheka

  • @thomasjesale
    @thomasjesale 2 дні тому +2

    Koma MCP mukumva nayo nyunyunyu

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs День тому

    Nkhani ndi ndalama ndithu anthu osewa akuthawa kuzipani zao

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pg 2 дні тому +2

    Truth to be told

  • @LucasBatoni
    @LucasBatoni 2 дні тому +2

    Wayankhula mukwAnila sangamukwaniseso malawi kkkkkkkkk

  • @munyenyembe
    @munyenyembe День тому

    Mawu anzeru kwambiri😊

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 2 дні тому

    zoona munthu wakhulu malo moti mcp ikanalongosola chipani alibusy kugula anthu oyimba zopanda ntchito malo moti apange kapeni kukopa anthu kd Dan lufani wamugulayo angabweleze anthu mchipani kodi more over pali blunder yomalila chilima bwenzi akumakopa anthu mchipani alibusy kugula anthu

  • @ImediJames-b4u
    @ImediJames-b4u 2 дні тому

    Wapenga misala?

  • @OskallKatandula
    @OskallKatandula 2 дні тому +1

    😂😂😂😂😂😂😂

    • @astonbotha2860
      @astonbotha2860 2 дні тому

      inuso man mutha ku thandizako anthu akufa ndi njara

  • @joelphili4779
    @joelphili4779 2 дні тому

    Kwinaku mutukwana

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 дні тому +1

    NDALAMA SI VOTE TIONANA 2025 AKUONANGATI ADZAWINA CHIFUKWA CHOGULA OIMBA AONA NYEKWE

  • @christopherchikankhen
    @christopherchikankhen 2 дні тому

    Cadet

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 15 годин тому

    Akuyetsa kale
    Pano Malawi idakwima awavotera oimbawo
    Ndipotso nanetso ngati akufuna kudikulako ndingapatse 20 rand ndalama yochepa ngati imeneyo

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 15 годин тому

    Wachoka ku DPP wachoka basi
    Palibetso kubwelela ku chipani
    Kameneko kanali kale kale
    Panopa wachoka ku DPP watha ameneyo
    Kaya oimba kaya wandale watha basi
    Kwasala ndikumangidwa a MCP

  • @MveraNambala
    @MveraNambala 15 годин тому

    Kma chimutu chimenecho chili Nd mzeru chimwendo khope yonyassyo