ZOOPSYA NDI ZOMVETSA CHISONI ZIMENE MWANA WA MAYI OYENDAYENDA (HULE) ANAKUMANA NAZO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 1 лют 2025

КОМЕНТАРІ • 32

  • @mateyudyton4739
    @mateyudyton4739 20 годин тому +3

    Pena umasiya mabvuto ako nkuyang'ana aanzako nkuzati zikomo ambuye eish😢😢😢

  • @NdendeuliMangani-d2q
    @NdendeuliMangani-d2q 2 години тому

    Ma God bless u continuously...

  • @FortunateMpinganjira
    @FortunateMpinganjira Годину тому

    😭😭😭 zukhuza kwambiri god bless you mr maseko 🙏🙏

  • @LindaKanthiti
    @LindaKanthiti 9 годин тому +1

    Ineo cholankhula chikundisowa😢😢😢😢 mokupemphani amene mwamtenga mwanai musamamuonetsere nkhaza chonde aMaseko ndagwira mwendo ambuye akudalitseni ndithu😢😢😢

  • @StellaKhwilipa
    @StellaKhwilipa 10 годин тому +1

    Ambuye akuze malire a moyo ndi kukupasani madalitso owirikiza Mr maseko

  • @FynessBotha-i5p
    @FynessBotha-i5p 13 годин тому +2

    😢😢😢Km ndalira ine eish

  • @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id
    @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id 14 годин тому +1

    Bambo maseko mulungu Akusamalileni mwapadeladela amen thumma amen yaganfaru ya allah😢mudaliseni mwapadeladela

  • @atupelemposa4786
    @atupelemposa4786 8 годин тому

    Ngati sukonda ana kuli bwino osabereka , kusiya kumanzuzitsa ana chonchi

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer 3 години тому

    Mmmmmh km ndankhumudwa kwambili azimai vuto ndi Chan kwen kwen uhure opanda phindu umeneo kumuzuza mwana osalakwa chifukwa chan eeeesh 💔💔💔💔💔😭😭😭😭

  • @MariaSoza-e1m
    @MariaSoza-e1m 7 годин тому

    Esh😢😢😢

  • @stevengama494
    @stevengama494 21 годину тому +1

    Yehova akudaliseni pa ntchito yomwe mukugwila ku family yanu, ndimayitanidwe ochokela kwamulungu musaleke kuchita zabwino kwaonse

  • @BrandinaJoseph-m5g
    @BrandinaJoseph-m5g 23 години тому +1

    Eish ndakhuzika moy mwanga😢

  • @EzekielBanda-r7r
    @EzekielBanda-r7r 3 години тому

    Ndinatsatila nkhan ya God knows koma mulungu akudalitseni

  • @Tabia-q1k
    @Tabia-q1k 8 годин тому

    Eshii kulimba mtima kwake kwa mtundu wanji

  • @AnnieHarawa-o4w
    @AnnieHarawa-o4w 4 години тому

    Zokhuza abale 😭😭

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy 22 години тому +1

    Mai ake mwanayu ndiopusa achisiluu andinyasa zedi 😢

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 23 години тому

    Mulungu apitilize kukusamalila Mai ndi bambo amene mukulela mwanayu mulungu apitilize kukusamalila amen ndakunyadilan❤

  • @FanessayassinFanessayassin
    @FanessayassinFanessayassin 22 години тому

    Mulungu amuyendele mwapadela hule ameneyo mmnn mulungu ndichani 😭😭😭 💔💔 eshiii ambuye zaweluseni ziko lanuli

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy 22 години тому +1

    Ziwanda maiwo mmh mwana obeleka okha ambuye bdalila

  • @LindaKanthiti
    @LindaKanthiti 9 годин тому

    😢😢😢😢

  • @AnnieThipa
    @AnnieThipa 14 годин тому

    Ndife opereweredwa zedi koma izizi mpaka utasiya zako ndithu mmmmh..Any contact please ....Tili kutali ndi kumudziko ndiye kaya nkufikira pati kuti kangachepe mumuthandizireko..Eish zolilitsa izi.

  • @AliceBotha-o4h
    @AliceBotha-o4h 4 години тому

    Mulungu akudalitaeni ndi. Kukuonjezerani masiku.abusa

  • @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id
    @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id 14 годин тому

    Koma thawi zina azibambofe timalakwa timango ziwa kubeleka ndikuthawa idindo wathu zimayiyo ndi ndifiti

  • @JudithNthini
    @JudithNthini 20 годин тому

    Ambuye akudalitseni inu ndi akadzi anu

  • @EstherLuka-t4l
    @EstherLuka-t4l 8 годин тому

    Nkhani yolilisa iyi

  • @JoaquimElidioChiwisse
    @JoaquimElidioChiwisse Годину тому

    Koma anthu amakhala olimba mtima mwana obereka wekha mpaka sayizi imeneneyi

  • @markbanda7434
    @markbanda7434 21 годину тому +1

    Mmai oipakwakwambili

  • @BlessingsMcnight
    @BlessingsMcnight 21 годину тому

    Khani yokhudza poyimva ana akudzudzika pa dziko lapansi kamba kamakolo opusa

  • @FaissonMzilo
    @FaissonMzilo 21 годину тому

    Mulungu amudalitse mwanay

  • @DanChimaliro-j7f
    @DanChimaliro-j7f 21 годину тому

    Mulungu azikudalisan inuyo ndakaz anu

  • @FalidahIbrahimSadalah
    @FalidahIbrahimSadalah 22 години тому

    Zandikhudza kwambiri

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 23 години тому

    Zoovota