MCP yakonza chiwembu chothana ndi Lytone Mangochi.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 13 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 66

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t Місяць тому

    Zoonadi brother Mangochi chilungamo. Osaopa osatopa osafooka

  • @KhonzoBlose-wq7zm
    @KhonzoBlose-wq7zm 10 місяців тому

    Mwaiyitha a bro mukutiyimilira pa chilungamo God bless and protect you till malawi change

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 9 місяців тому

    Bwana mangochi mumayakulachochi eee mumakwana

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 10 місяців тому

    Awuze agule akwamsundwe'wa mchimwene, akuwona ngati malawiyu ndiwake yekha wagule ameneyu, mxiiiiiiimu

  • @JamesKamtedza
    @JamesKamtedza 8 місяців тому

    Kod mene akuonekera awa or kwapasa 1 million angakene aaaaaa

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 10 місяців тому

    Anthu woima poyera ndiwo akusowa
    Mr inu ndi Mr Kalindo God protect you guys mukutiimilira.

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 10 місяців тому

    Mr mangochi more fire❤❤❤❤❤❤

  • @HanishaissahKagansa
    @HanishaissahKagansa 10 місяців тому +2

    We need more people like this

  • @TaitasMakombe-ql4rr
    @TaitasMakombe-ql4rr 10 місяців тому

    Kape iwe

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 10 місяців тому

    Yaaaaa...anthu osaopa akwana awiri......timakunyadirani😂😂😂😂😂😂😂

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 10 місяців тому

    Chilungamo chokha chokha

  • @Maxielyies
    @Maxielyies 10 місяців тому

    Powerful talking Bwana Mangochi, proud of you comrade, we are really feeling pain

  • @NovemberMmangathayo
    @NovemberMmangathayo 10 місяців тому

    Ndipondizoona

  • @GiftRichard-f8d
    @GiftRichard-f8d 10 місяців тому

    Auzen zoona osaopa

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 10 місяців тому +1

    Ndipo zoonad kwambiri big, osaopayi tithana nawo boss

  • @JosephBotoman
    @JosephBotoman 10 місяців тому

    Akutumani inu

  • @JOSEPHYbchisale
    @JOSEPHYbchisale 10 місяців тому

    Kuyankhula monveka bwino mbuzi imeneyi yatikwana

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 10 місяців тому

    Lululululululululu😂😂😂😂😂😂

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 10 місяців тому

    Boma lanji lofuna kuthana ndi anthu wonena chilungamo, mmalo mothana ndi mavuto alimdziko munowa????? Fullish leadership

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 6 місяців тому

    Machende ake ameneyo tamuoneni kuseliku zomwe wayankhura galu wachabe chabe

  • @GenialaChalera
    @GenialaChalera 10 місяців тому

    Mantha amenewo ndinu wopusa kapani zanu samalimbana ndi boma

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 10 місяців тому

    Eti eti mawu 👏👏

  • @eliouschambayamoyowatha4300
    @eliouschambayamoyowatha4300 10 місяців тому

    Ena amakondwa ena kulila

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 10 місяців тому

    Osadandaula bro sangakupheni likali boma la Chakwera ndilopha anthu bwenzi ataphedwa Bon Kalindo amatukwana Chakwera tsiku liri lonse koma uyo alipoyo ndiye a Lytone musaope chinthunzi chanu chomwe

  • @4.30inohio
    @4.30inohio 10 місяців тому

    Mawu mr❤

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 10 місяців тому

    Muma kwana abambo chilima bamaaa

  • @yusufbanda4980
    @yusufbanda4980 10 місяців тому

    Osadandaula sitngalole kt akuvulazen tkuona 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @Zolonimo-f9e
    @Zolonimo-f9e 10 місяців тому

    Mr mangochi more fire

  • @PetrolDonasiyano
    @PetrolDonasiyano 10 місяців тому

    Akamandaulidwa aziva ,osat kupha anthu,peter samabweza

  • @JujuMussa-z1w
    @JujuMussa-z1w 10 місяців тому

    Chakwela ndi galu kwabas

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 10 місяців тому

    lnuso penapake mumalankhura mwa uchitsilu kumene unganenepo munthu amene anaphedwapo ndi chakwera kalankhulani ngati muli ndi zizukulu

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 10 місяців тому

    mumbili yadzikoli munathandizapo ndani ndare zopanda nzelu

  • @MosesBanda-ef6fj
    @MosesBanda-ef6fj 10 місяців тому

    Chakwela bagamoyo moyenda ndiwe galu kwabansi nyau yoputsa

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam 10 місяців тому

    Mr mangochi ❤❤❤

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 10 місяців тому

    No fear for nothing moti mukonze zinthu mukukhala busy kumasaka anthu akakuzuzulani mcp ndinu anthu otani muziwe kuti popanda anthu sipangskhale boma you must know that

  • @DonaldPonda-p2q
    @DonaldPonda-p2q 10 місяців тому

    Kodi iweyo chakwera ukungokhalira kulimbana ndi anthu osalakwa cholinga aziombera m'manja umbuli wakowo ?

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 10 місяців тому

    Awuuze big zoona zokhazokha

  • @CleverChiumia
    @CleverChiumia 10 місяців тому

    Mukunena zoona. Ameneo osawasekerera. Methane nao ndipo atengerepo phunziro

  • @mikekhamusi1807
    @mikekhamusi1807 10 місяців тому

    Mzika izitelo pakakhala zolakwika

  • @IntiusKayombe
    @IntiusKayombe 10 місяців тому

    Mumakwana kumeneko nde kuyakhula kuno kumangochi imtianz

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 10 місяців тому

    Azipita kwawo ndalama zamthela lyton ufiti kapangile kwanu mwatha inu

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 10 місяців тому

    Kuona,kwanga anthuwatu,timasankha ndi vote.kulikwabwino,tidzawachonsetso,ndi vote.than,kumangolankhula,zimatopetsetsa, kwambili.

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 10 місяців тому

    Awuze apuludzu amenewa, mbava zachabe chabe

  • @user-lf6qf2tw5o
    @user-lf6qf2tw5o 10 місяців тому +1

    Panja boma ili limadana ndi chilungamo

  • @francismungu7749
    @francismungu7749 10 місяців тому

    Tikufuna anthu ngati awa opanda mantha ❤

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 10 місяців тому

      Ndipo zedi big❤❤❤❤

  • @IMURANHUSSEIN
    @IMURANHUSSEIN 10 місяців тому

    Tilinawe limodzi m bale laiton

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 10 місяців тому

    Kkkkkkk azakumana ndimphepo kkkkkkk amarawi ziko ramarawi nkawona ndirosauka anthu amadarira zisamba 🥱 mmaro mosogoza murungu pari yesu apa 🤷

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 10 місяців тому

    What happened in 1992 to1994 why Malawian can't wake up?

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 10 місяців тому

    Chilungamo koma osalimbana njala kusokoneza passport koma mukulimbana ndi muthu akuuzilani mayeso aaaa athu andale kusangalala bonza

  • @nellikkmwenda7087
    @nellikkmwenda7087 10 місяців тому

    Awuzeni zowoza chilungamo ulemu wanu amangochi mulungu ankhalenanu

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 10 місяців тому

    God protect this guy please

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 10 місяців тому

    Mumalawi muno tikufuna anthu ngati awawa not afiti opembeza chinthu chokuphacho choononga zinthu chi Chakweracho

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 10 місяців тому +1

    😆😆😆 awuze chilungamo kumupoto mcp isatenge ngati ndi kulilongwe. President wabwino wotukwana womunyoza amakhala wochepa. Koma Chakwera pa Facebook pa UA-cam pa TV palipose pamene ungalowe upeza anthu akunyoza Chakwera ndi cabinet yake means kuti walephera kuyendesa ziko la Malawi. Amene akumuyamikira ndiakubanja kwawo ndi amene amadya nawo ndalama zakuba. Munthu amene ali ndiumunthu wachilungamo oopa chauta sangayamikire Chakwera pamene wafika Malawi.

    • @GreshamKadzembe-tn8cq
      @GreshamKadzembe-tn8cq 10 місяців тому

      Anthu ake mukunena alhomwe, kodi mnchifukwa chani mavuto akabwera simuvomeredza koma mumayamba kulodza dzala azitsogoleri malo mothandidza Kapena kupemphera kuti dziko liyambenso kuyenda bwino

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 10 місяців тому

    Mbuzi zawanthu zayemusipi

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 10 місяців тому

    This another D.C. ccc

  • @HendryChiwezo
    @HendryChiwezo 10 місяців тому

    Kodi every day kunena anzako iwo osamabwezela munthu sungatope

  • @ZachariaZacharia-u7x
    @ZachariaZacharia-u7x 10 місяців тому

    Koma iweyo ulibe zeru boma Mene likupangiramu chabwino Mene anthu akuvutikiramo iweyo wapangapo chani dikirani dpp yanuyo osaipitsa anthu akukalongawo ayi awotu NDI a MCP udzawona povota chibwana upangacho udzalira poulutsa dzina la president wadziko iwe

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 10 місяців тому

    Zimene ukuyankhula uzikayankhulila kwanu ku mangoch osat kukaronga kuno business yanu yakaunjika yimene munabwelela mukaronga inakuthelani bwelelani kwanu kumwela uko

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 10 місяців тому

    Uli ndichani iwe kut ulimbane ndi president chitsiru Cha munthu ,a lighton sukulu mulibe koma pa Malawi ndi pophweka ,nyumba yolozeka ulibe mene unayambira business palibe chomwe unapangapo

    • @Wisdom-y4t
      @Wisdom-y4t 10 місяців тому

      Kumenyera ufulu sizitanthauza zomwe mwatchulazi koma kulimba mtima basi. 😮

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 10 місяців тому

    Lighton muzinvere chison ndinu odwala inu MOTi uzilimbikila zako kut moyo wako ukhale wamphanvu uli busy kulimbana ndi president munthu wopanda kena kalikonse ,sukulu yeniyeni mulbe even chizungu sungayankhule suziwapo china chilichose mene akuyendela ziko olo atakupasa mpando wau president ungayendese ,shame on u

    • @cadohjabu5565
      @cadohjabu5565 10 місяців тому +1

      ziveleni Chisoni dziko nda Anthu akuyankhulila a Malawi ngat iwe zako zikuenda osanyoza anzako

    • @IntiusKayombe
      @IntiusKayombe 10 місяців тому

      Inu