MUTIUZE BWINO PAZA IMFA YA CHILIMA - DAVID MBEWE WADZAMBATUKA MWAUKALI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 37

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 14 годин тому +1

    Yes yes exactly what we want viva pastor mbewe

  • @kingssalema3364
    @kingssalema3364 17 годин тому +6

    Komanso zomachoka ku Church nkubwelaa ku ndalee ayiiii.
    Ndi iziiiii tikulila nazo lerozi.

  • @ChikutaEmmanuel
    @ChikutaEmmanuel 5 годин тому +1

    Kusiya yesu mmmmm

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 14 годин тому +1

    More beautiful Mr mbewe

  • @JustinWBanda
    @JustinWBanda 4 години тому +1

    Masiku nde amapekekedwa koma zosatila nothing

  • @Costance-nf7ue
    @Costance-nf7ue 16 годин тому +2

    More fire more fire tiimilileni amalawi

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 16 годин тому +1

    Good pastor mbewe zikomo kwambiri

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 15 годин тому +1

    🙏🙏🙏🙏🙏🙏 Dr mbewe ❤❤❤❤❤

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 14 годин тому +1

    Zoona zake a mbewe..menyerano nkhondo nonse a opposition

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 15 годин тому +1

    Yeah malawi wa lero

  • @SharifWad
    @SharifWad 14 годин тому +1

    Zoona zake

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 16 годин тому +1

    Viva mbewe❤❤❤

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 3 години тому

    Mwaiwala kuti munasankhidwa ndi mwini moyo wayamba za dziko sopano ndi izi tusowa nazo ntendere lerozi

  • @HarryChindiwo
    @HarryChindiwo 13 годин тому +1

    Munthu ochoks ku church kupita ku ndale..... A Malawi takana

  • @giftngombeyakuyera8703
    @giftngombeyakuyera8703 14 годин тому +1

    I like chizungucho

  • @Enless-n2c
    @Enless-n2c 16 годин тому +1

    prophet wandale km tili matsiku otsikiza ndithu

  • @JacksonNamathawa
    @JacksonNamathawa 16 годин тому +1

    That's true bishop

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 15 годин тому +1

    "A vote of a common doesnt count"

  • @MarcyKamaga
    @MarcyKamaga 15 годин тому +1

    Ineyo zandisangarasa kwambiri ndipo ambuye akutsogorere pamoyo wanu wose pokumbukira mzanu doctor sauros chirima tanthokoza kwambiri ari bizy kugawa zindarama sorry ambuye akurangeni

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 15 годин тому +1

    Baba zinthu musangozipititsa ku ndale ngakhale ku america kaya southafrica nzika yopanda l.d simavota.

    • @RosinaPatel
      @RosinaPatel 14 годин тому

      Izi zikunenedwa chifukwa a NRB sanalembe ambiri chigawo cha kumwela..

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l 14 годин тому +1

    Zabwino kwabasi, zilibhoo akujaila kwambili

  • @NewmanMunthali-od9yk
    @NewmanMunthali-od9yk 16 годин тому +1

    Awa please apite ku church komaso ndi a prophet alosere chabwino za denge please tizivutika iwo a prophet alipo no going through investigators

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 16 годин тому +1

    Scriptures to sleep with rain and thunder

  • @MoosaMuhammed-se5sd
    @MoosaMuhammed-se5sd 15 годин тому +1

    Tiyenidi tikavute ku parliament

  • @RoseNjaidi
    @RoseNjaidi 16 годин тому +1

    apro osangolosela bwanji

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 3 години тому

    Kugwa manja mwa chauta ndikoopsya zedi

  • @chiletsokazembe-ri4ic
    @chiletsokazembe-ri4ic 15 годин тому +1

    Mmmm inu ma ID inayamba ndi adpp

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 12 годин тому

      Inayamba ndi DPP yes kmano sanalamuleko kt anthu azivotera id yokha ai, DPP inkalora kalata yakwa mfumu, passport n driving license Inu mukukana zonsezi y

  • @lingstonenagoli7729
    @lingstonenagoli7729 17 годин тому

    First watch

  • @Figobaulen
    @Figobaulen 17 годин тому +1

    Namugwilila ntchito sanandipase ndalam ndiovuta kape ameneyo

  • @Figobaulen
    @Figobaulen 17 годин тому +1

    Wamanyi ameneyo

  • @EviChio
    @EviChio 16 годин тому +1

    Zoona zake