BOMA LAMANGA MAYI PATRICIA KALIATI NDIPO ZASIMIKIZIKA KUTI CHIFUKWA CHOMWE AWAMANGIRA NDI ICHI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 25 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 553

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 День тому +32

    Iyiyi ndi move akufuna asakayime nawo pa President adziyenda ndi Bello mu thumba... 🙆‍♀️🙆‍♀️🙆‍♀️

  • @JoycieMbaya
    @JoycieMbaya День тому +11

    Eeeh Koma! There is just too much evil happening in this country. May the Almighty God come to our rescue.

  • @JosephMkuzi
    @JosephMkuzi День тому +2

    Ine Joseph Mkuziwaduka Osadanda masten Sweet for sweat keep it up

  • @ChimwemweZuze
    @ChimwemweZuze 19 годин тому

    Koma ife nde zatizunga mutu msaname ,zungokhala ngati za ma aged person ndithu kuti mwina akula anthuwa abwelera ku wumwana aaaaah 😊

  • @KhadijahMuhammadah-my7lc
    @KhadijahMuhammadah-my7lc День тому +1

    Never give up pk

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu День тому +12

    BomA la MCP ,,, mwatasa kwambili... Kufuna kubisa imafa ya SKC

  • @EddahKaunda
    @EddahKaunda День тому +1

    History is best teacher koma kusanva anthu

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 День тому +8

    Iyi ndi pulani kuti asaime pa koveshoni ndi Michael usi wagwirizana ndi chikangawa

  • @MerryBiyela
    @MerryBiyela 22 години тому

    Good make it truth on one life

  • @AKMASEKO
    @AKMASEKO День тому +1

    Komatu utsi sufuka opanda moto dziko lonseli sangangoma Mayi Kaliyati! Akulu anati kang'oma kolilitsa sikachedwa kung'ambika osangoti poti ndimzimayi koma ngati alakwa afunika akumane m'chigamulo osamangonyoza boma.

  • @JafaliAdams-l5k
    @JafaliAdams-l5k День тому +1

    Amawonjeza kma kupanga ndale sanyozana mayi uyu akhale nd displin

  • @davidbulla5128
    @davidbulla5128 День тому +1

    Politics yo dyetsana Manyi..
    .We ready to die for this flag
    Zachimizi
    .Lilongwe sewage kwacha down youth struggling...and you want to bring fear to my head...No ! This is not 1993

  • @blessingbanda6206
    @blessingbanda6206 День тому +1

    But why mukumayika zithuzi nkhope yamagazi ngati munthuyo wakhapi propaganda

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam День тому +5

    From Cape Town mitchells plain town centre. Chakwela ukufuna chiyani. Iweyo manganya ndimbuzi yamuthu kwambili ukuziwa kt upule sungatenge ndichingangawa wakoyo

  • @IbrahimUseni-p8f
    @IbrahimUseni-p8f День тому +7

    Manganya ameneyo,,mafuta kulibe kummanga munthu wa utm akulira maliro achirima

  • @OmarMakawa
    @OmarMakawa День тому +1

    Mayi ameneyu nayeso ndiosokoneza achita bwno kumutapa mesa ndi amene anathandiza bomali kt likhale pa pando eya uliziwe ziko zomwevlimapanga mwina uleka

  • @Isakaymw
    @Isakaymw 22 години тому

    Ndi plan yachikangawa imeneyo ndiyemwe wamuona Kut atha kumupasa bizy thaw ya kampeni ino.amanga bwanji Muthu opanda milandu, zake izo Ife nde boma tikusitha Patt!!?

  • @AlfredJuliusTemboh
    @AlfredJuliusTemboh День тому

    Bwana Chakwera zomwe akupangazi adzafa ngati mwana ndipo sikale chifukwa pano anthu atopa nazo. Inu muzigona ndithu

  • @James-w6j8z
    @James-w6j8z День тому

    Boma ili ndiloyipa kwambili don't warry amalawi tiligwesa popanopopano Muthu sumaluma Chala chimene chimakudyesa phala

  • @DesireMjojo
    @DesireMjojo День тому +11

    Kalindo adanena kale izi ,sizodabwitsa

    • @dalitson3558
      @dalitson3558 День тому

      Kalindo ndi Katundu he never disappoints

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss7360 День тому

    Politics in Malawi is cleartivity that dazzles

  • @ShanifaMustafer
    @ShanifaMustafer День тому +4

    Our country now is more 𝕎𝕠𝕣𝕤𝕖 𝕥𝕙𝕒𝕟 𝕓𝕖𝕗𝕠𝕣𝕖

  • @AubreyShaba-b5d
    @AubreyShaba-b5d День тому +3

    Perekani chifukwa chomangira ...kungoti felony...timve zifukwa... felony sichifukwa..mukutisokoneza...

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x День тому +3

    Mulungu si James pemphero mulungu amutetezere mai a kweni ndipo mzimu wa chilima uwakanthe anthuwo

  • @IreenChilingulo
    @IreenChilingulo День тому

    Mulandu apalamula liti nanga masiku onsewa amadikila chani poti tava kuti anapalamula Mulandu ndiye masiku onsewa munalikiti

  • @PreciousElijahKayinga-li3cn
    @PreciousElijahKayinga-li3cn День тому +1

    Mukamabweretsa nkhani zanuzo timaona ngati mwafufuza nkupeza chimene wamangidwira koma inunso muli mbuli pankhaniyiii moti mkumakasaka mma comments aanthu

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 День тому

    ILI NDIBODZA KOMA ZOWONA ZAKE MCP IKUFUNA KUSOKONEZA UTM KOMATU MANGANYA NDI CHAKWERA NDIWO WAPANGA IZI MANGANYA

  • @SitithanaSonani
    @SitithanaSonani День тому +1

    God deliver our beloved country whr r we going

  • @BrightZionga
    @BrightZionga День тому

    Chakwera chitukuko ndichimenocho? failed president ever

  • @RonnMtafya
    @RonnMtafya День тому +3

    Muja Paulos amanzunzira osatira Yesu ndi pamene Chikhristu chinafalikira kwambiri.Mungoonjejera mkwiyo wa pa 29 ndi 30 OCTOBER.

  • @EmmanuelSteve-q7b
    @EmmanuelSteve-q7b День тому

    Izo ndindare manganya ndichikangawa afuna kuzunza azawo mmalo mosakha njira zotesera mavuto mmalawi muli bize kukorezer mukwiyo amalawi

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama День тому +2

    Basi manyodza dpp ameneyo lelo adziwona okha kuti boma ndi dpp chipani cha ulemu

  • @LuciousMulipo
    @LuciousMulipo День тому

    As MCP tries to kill UTM and entire opposition using Kape manganya,, shame

  • @GraceKamanga-k8v
    @GraceKamanga-k8v День тому +2

    Ku Malawi timayankhula Chichewa,chitumbuka atinthandauzire mlandu wake timve bwino bwino

  • @victoriasamarthankhata
    @victoriasamarthankhata День тому

    Ndingoziwa nawwo kuti azukako bwanji amai lero kuchitokolosi,ndadzuka ndi matha zedi😢😢😢,so God help us

  • @JoelMwenegamba
    @JoelMwenegamba День тому +9

    Angofuna kuti kweni asapedze ku convention it's like government want to finish U T M. But God is watching.

  • @GreysonChilongo
    @GreysonChilongo День тому

    MCP yikuopa chisankho ndichifukwa ayamba musokoneza mwapha chilima mwayamba kaliati nikufuna kusokoneza UTM afiti imwe a satanic imwe ba MCP agalu inu from Zambia 🇿🇲

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k День тому +2

    Tru,,God z watching,,Mulungu awamenyera Mai kaliati nkhondo Ali cete

  • @ShemjuniorMweramkulu
    @ShemjuniorMweramkulu День тому

    This is what we expected from Mcp with it's president too bad

  • @johnchirwa8505
    @johnchirwa8505 День тому

    MCP become scared of Kaliyati

  • @EdsonchilongoSitoe
    @EdsonchilongoSitoe День тому +1

    Iri si boma ayi akufuna kuti kumbutsa nthawi ya kamuzu banda from mocambique

  • @EliaSiska-n6r
    @EliaSiska-n6r День тому +1

    Inka Malawian politics very few women speak out. Kaliati is a voice for women.

  • @ChirwaFebe
    @ChirwaFebe День тому

    mulandu wanji wosachulidwa
    Malawi wawola chikangawa ukuwononga ziko lathu uzinka kwanu satana iwe

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 День тому

    Michael Usi amadziwa kuti sangakhale president, Akweni for President,we are praying for you Akweni and our country Malawi

  • @victoriasamarthankhata
    @victoriasamarthankhata День тому

    JESUS JESUS INTERVINE IN THIS SITUATION 😢😢

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis День тому

    Ausi ndi munthu oyipa kodi. Usi iwe kayin. Umapemphera chani

  • @EnockLichenya
    @EnockLichenya День тому +4

    Masiku atha kale awa tionana this coming year, kutha nzeru kwa Boma uku😢😢😢😢

  • @lawrencedanielmandauka
    @lawrencedanielmandauka День тому +1

    Nde mukanangokhala chete osabwera ndi nkhani zossmveka spa mudziyamba mwafufuza kuti anthu adziwe chenicheni

  • @johnchirwa8505
    @johnchirwa8505 День тому

    Leave her alone this government bin Laden are at Malawi

  • @AnnahMpamati
    @AnnahMpamati 17 годин тому

    Nde bwanji mlandu woo sakuwutchula, iziituu khaza akupanga ,kod zonsezi akuchitachi akufuna chani kwenikweni

  • @AllanGonthi
    @AllanGonthi День тому +1

    Anthu a MCP ma plan awo amakhala olephera nthawi zonse adapanga plan ya Chilima anthu adawatulukiranso mwachangu lero apangaso izi anthu awatulukiranso nonse a MCP mulibe m'zeru ndale zanu ndi za anadi nokhanokha

  • @WelosChifunga
    @WelosChifunga День тому +2

    Boma limeneli ndi loipa kwambili tionetsana 2025

  • @SostenPiyo
    @SostenPiyo День тому +2

    Manganya akudziwa za kumangidwaku, Mulungu akuona, opposition be careful about

  • @cuthbertjafali6059
    @cuthbertjafali6059 День тому +3

    Koma ndi chani makamaka, God have mercy on us

  • @PhalesNotta
    @PhalesNotta День тому

    Nkhani yonseyi ndi manganya ndipo khulupirirani kut manganya akudziwapo kanthu koma mulungu ndiwabwino Patricia kaliati atuluka mudzina layesu chikangawa koma umaziwa kut ku police skwabwino

  • @dennisbanda4751
    @dennisbanda4751 День тому

    Ana ambuzi inu mumangophatikiza zinkhani Tive ziti zopusa zimenezo mukufuna anthu akalakwa asamamangidwe dzitsiru zaanthu

  • @HappyThom-i1s
    @HappyThom-i1s День тому

    Mcp mukunama uyuyu amupanga realise mukuona ngat tiopa anthu opusa inu chakwera ulibe nzeru

  • @CastomuJosephy-z3o
    @CastomuJosephy-z3o День тому

    Koma APA titamangisane basi amalawi

  • @AbduKalhackimKadzuwa
    @AbduKalhackimKadzuwa День тому

    Zopusa basi.Mulibe umboni weniweni chotipangila tag ndichani.

  • @HashrouYassin
    @HashrouYassin День тому

    Awamanga chifukwa Choti anawakana chibwenzi apule,zoona mungamalimbane ndi mzimai mukufuna muzikhala busy kumugwilira kumeneko

  • @SamuelMponda-y3d
    @SamuelMponda-y3d День тому +1

    Angofuna kupeza mpata osokoneza nsonkhano waukulu wa UTM pa 17 Nov. 2024

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera День тому

    Channel cha bakili muluzi tv chija musazachipwekese iyewuja amaziwa chinachilichotse ndipo

  • @SafariBvumbwe
    @SafariBvumbwe День тому

    Or utakhala ndiphamvu motani km zimatha or udindo umantha km asiyeni apange chimene akufunacho km siku lina malawi uzabwereraso muchimake

  • @mathewsthawe5270
    @mathewsthawe5270 15 годин тому

    Kod tamakambani ndi PK apalamula mulandu waukulu mlandu wake uti felony simulandutu tanenani Mulandu wake

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 День тому

    CHAKWERA NDI MBULI AMADANA NDI ANTHU AZERU

  • @OmarMakawa
    @OmarMakawa День тому

    Azimai boza osayenda maliseche muzangoyaluka musiyen ngat mukuona mavuto gulu lake ndilomweli lomwe linalimhlbikisa zisokonezo nthaw ya pita

  • @YankhoRumwila
    @YankhoRumwila 20 годин тому

    Akudziwana awa ndi momwe amadyera. Anthu a ndale zawo ndi zimodzi.

  • @ChimwemweSamson-l5s
    @ChimwemweSamson-l5s День тому +1

    Ndale zaku Malawi

  • @mikekaliza-bw4yg
    @mikekaliza-bw4yg День тому

    amalawi sisamapange chochi zosezi wapanga ndi usi pofuna kumulepere kuti asamenyere ufulu wa malawi basi tiwuzeni chomwe a mcp mukufuna chencheni

  • @PercivalKalua
    @PercivalKalua День тому

    Uku ndi kuwonjezela nkwiyo wa chikangawa airport.

  • @AdamusuwediMandela
    @AdamusuwediMandela День тому

    Kunzuza azimayi ndi mavuto akulu kwambili kaliati amatukwana bakili muluzi koma sanammange boma la chakwela ndi lolephela atetezeni azimayi onse nzdiko muno kusaziwa ndale ndi matenda

  • @isaaczuze
    @isaaczuze День тому

    Boma loyendesedwa ndi zigawenga komanso mbava chonchi tikavotere anthu okuti akumanga anthu popanda zifukwa zenizeni

  • @ThandiShandu-l6w
    @ThandiShandu-l6w День тому

    Akanango chepetsa mwano azipanga ndale bwinobwino ngati anzake

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx День тому +1

    Akufuna manganya kuti atenge chipani kuti chibwerere ku mcp a kunama tu manganya anthu savoteratu

  • @JohnMankhwala
    @JohnMankhwala День тому

    kulakwa uku asamutelo muthu

  • @MiracleRose-f9x
    @MiracleRose-f9x День тому +1

    Kodi akufuna kumpha athu angati chifukwa chani m dima umadana ndikuujika bas tikufunabe commission of equrery

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka День тому +2

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima

  • @mariawachesterweluzan
    @mariawachesterweluzan День тому

    mcp mantha ayambika ndi chipan chomwe chinawayika pa mpando

  • @StaffordNgalande
    @StaffordNgalande День тому

    Kod ufulu wa Azimai uja uli kuti Achakwela sizona mwachitazo

  • @ViegasThubuaArmando
    @ViegasThubuaArmando День тому

    Boma koma lachakwera peter Samatha upulezident

  • @GraceMwene
    @GraceMwene День тому

    Koma chakwera zikusata zomwe kuchita tikumana 2025

  • @stephenchavula1162
    @stephenchavula1162 День тому

    kenaka mumva kuti winwa atenga injuction yolepheretsa convetion,so that rumour is true,shame we are becoming a lawless nation

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 День тому

    NDNAKAKONDA MANGANYA KUKOVESHONI ASAMULOLA AI NDI ANENE WAPANGITSA KUTI MAIWA AMANGIDWA AKU NDIKUPANIKIZA ANTHU ADZIKO MUNO PAKUFUNIKA PHAMVU MCP NDI CHAKWERA NDI ANTHU AKE WALITENGA DZIKOLI NGATI MUNDA WAMASIYE

  • @ZaithwaMatchado
    @ZaithwaMatchado День тому

    Ukundiye kumulakwira kale lonse lija bwanji osamupha iiiii Koma ndale zakumalawi inu akangopezeka Kuti Wafa ndithu munditsimikiza Kuti khondo iyamba ndithu

  • @ChisomoMzumala
    @ChisomoMzumala День тому

    Tisamakhale ngati malawi siyophunzila

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 День тому +1

    Manganya panga manyazi ulibe umunthu Chocho kumati muzakhale president

  • @JacobVictor-z7r
    @JacobVictor-z7r День тому

    Munamutenga nokha Lazalo ku chipiku kuti akhale president wanu lero akumangansoni mukhaula naye Chikangawayo

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c День тому

    Koma apolice amene mikugwirisidwa ntchito achipan tizaona boma likadzasintha ntchito za mcp ndizimenezo chipani chakupha iweso jezebelo ziwa kt paudindo umenewo uzachokapo

  • @Harrsoni
    @Harrsoni День тому +2

    Mulandu waukulu oponsa wakugwa kwa ndege ?

  • @ConlardNkhoma
    @ConlardNkhoma День тому +1

    Ukayenda usasiye mlomo amayiwa amazitenga ngati adzao alibe pakamwa

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni День тому

    Ndipo zikuonesadi kuti ndichina manganya inu aboma mukulemhera kukongola zakuchikanga nanuso muzamqngidwa

  • @MatthewsJanuary
    @MatthewsJanuary День тому

    Michael usi ndiamene akupanga zonsezi

  • @MaryStanley-n3b
    @MaryStanley-n3b День тому

    Kufunatu kukwiisa azimai uku aaaa anthu Ali mu mkwiyo kale mukufuna Malawi atani?

  • @SharonNdadza
    @SharonNdadza День тому

    Dzulo tamva nkhani yonyoza yokhuza Malatavkodi mwamupanga chani?mwamusiya kamba ndinzanu?Kodi bwanji a Mcp simukupanga manyazi ndizomwe mukupanga manyazi? Dziwani ichiiiiii mukamapanga zinthu musamayangane pansies koma muziyangana kumwamba chifukwa mwini wa zonse alikumwamba.Timuope mulungu tisagwilise ntchito nzeru zathu chifukwa tizayankha patsogolo.Mulungu simunthu okondedwa.kubwenzera mkwayehova...........

  • @edsonphangula5817
    @edsonphangula5817 День тому

    She got problem I don't trust her the way I saw briefing with other party talking MEC and MCP and she can make big crime

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 День тому

    YAA NDIZOWONA CHAKWERA MANGANYA NDI PLAN YOCHITA KUKOZA MISANA YANU MBUZI WHY OSAMANGA AMENE ANAPHA CHILIMA MUKUMANGA ANTHU OSALAKWA OSACHITA MANYAZI KUNKUYU ANAPHA MUNTHU BWANJI SIMUKUMANGA APOLICE IZI MUKUCHITAZI MADZAYIVA KUWAWA

  • @KelevraKatesa-g3z
    @KelevraKatesa-g3z День тому

    Strong we stand,free up PK

  • @Harrychilamwa
    @Harrychilamwa День тому

    Sizowona zimene zikuchitika ngakhale atapanga zimenezi ifeyo sitikubwerela buyo boma lokupha zotumidwa

  • @WillianBanda-p7d
    @WillianBanda-p7d День тому

    Chikangawa political party has failed to run malawi gvt

  • @ChipiriroDumba
    @ChipiriroDumba День тому

    ndiye bwino kupllice kumangopita aphawi