MDF ubweleko , ntchito ilikuno ku MALAWI , nkhalango zikutha anthu akuotcha makala mopanda mantha , Komanso paul kagame akulandila chithandizo kuchokela ku France ,
A SILIKALI ATHU SI OWAMVERA CHISONI CHIFUKWA KUNO KWATHU PALIBE CHOMWE AKUTITHANDIZA , ANASANKHA KUGWIRA NTCHITO NDI CHIPANI CHA MCP ZA MOMWE NZIKA ZAO ZIKUCHITIRIDWA NKHANZA ALIBE NAZO NDIYE BOLA AZIONE KUMENEKO KUZOLOWERA KULEMBEDWA NTCHITO NKUMANGOYENDA BAWO KU BARRACKS MPAKA KUPANGA RETIREMENT, KUMANGOONERERA CHAKWERA AKUONONGA DZIKO KUZUNZA NZIKA , KUONERERA CHAKWERA AKUPHA CHILIMA NDI ZIMENEZOTU SIPAJA AMANGOONERERA A SILIKALI A PAUL KAGAME AKULOWA MWATHU MUNO MENE AKUFUNIRA , KWATSALA PANG'ONO AKUUKIRANINSO CHIFUKWA CHA TULO CHITETEZO CHA ARMY MUDZIKOLATHU CHINATHA CHIFUKWA CHA DYERA
Rwanda idayambila kale kuba gold ndi diamond 💎 ndikumapha,anthu.nkhani,yaikulu si,kulimbana,ndi zika koma kuba gold yo akumamukumbila mu ziko lache.kagame,ndi wachabe kwambili kumuona,kuonda koma mutima mwache woipa.moti,ku Malawi kuno,ku kasiya ikayambika ntchito yokumba mwala azanamaso kuti, ku Malawi mukutsunga, zigawenga.cholinga,azabe.
Amalawi mukuma yankhula nkhanngati ndinu mfiri nzeru lulibe nangaimnyamata wazisukulu zanu basi kuchilimika kuka tchula and blaming president coz of war
ASILIKALI A MALAWI AZINGOFA KUMENEKO NANGA ALI NDI PHINDU LANJI KWA AMALAWI?A MALAWI AKULIRA PANO KOMA IWOALI KAKAKA KU MBALI YA BOMA NDIYE IFE AMALAWI TIZIWADANDAULIRA KUTI CHANI IWO AKUDYA NDI BOMA AKUTHANDIZA BOMA .BOMALOMWERO LIWALIRIRE
Mesa chakwera ndikupha paja amasekelelatu anthuaziphedwa nayeso mesa ndi chigawenga chakwera ndi zake ka gameyoso kod simungakwanise kupha kagameyo kuti chakwera akhawule chakwera ndi munthu woipa kwambir hvy
Gululi n la kagame,la private, maiko n mabungwenso amadziwa, n wachabe ngati mukukumbukira awa sioyamba taikanso mitembo Ina kuno,ku Tanzania komanso ku SA konko.osaganiza n amene amamutenga munthuyi ngati mzao.
Good news for ever and enjoyed it good newsssssssss ndpo nkhani yabooooooooooo afaso ochepa atatu basiiiiii zandinyasa bwanji onsewo anapita Amalawio zikanafa zonsezoooooooooooooo gud newssssssss
Good news asilikali athu omwewa akulephera kuteteza dziko lawo zaziiiiiii is not bad news for us but good news
Zafikapa bola kuwasiya azigagadana okhaokha coz nkhondoyi ndiyakale simatha ai,amene akufa ndi abale athu omwenso akusiya mabanja ndi ana akuvutika, ndiye funso Langa mkumati asilikali omwewa akulephera kuteteza dziko lathu lomwe mbava zili mbwee, kuphana sinkhani, Kuti manga ndie iiii osanena. Bwanji asalawo kumeneko mokupemphani atabwera kumudzi Kuno adzateteze dziko laoli😢
😂😂😂 m23 akwapuleni iwo akupangako chani ku congo kulibe asilikari enao akupitila kuba Diamond
Komatu ine izi kunyimaku mbeeee!!! Nyanja yapita akukateteza diamond ziko la Eni wake, djela apulesidenti anuwo manyiiiii
MDF ubweleko , ntchito ilikuno ku MALAWI , nkhalango zikutha anthu akuotcha makala mopanda mantha ,
Komanso paul kagame akulandila chithandizo kuchokela ku France ,
Nde pot asilikari athuwo akapita ku DRC ndipomwe amalemera chifukwa salary sizikwanira vuto ndiumphawi
Kusiya nyanja kuno😂😂😂😂😂Koma kuteteza zayeni
Ndemesa seu WA pugagame anayamba kucheza ndi bingu
A SILIKALI ATHU SI OWAMVERA CHISONI CHIFUKWA KUNO KWATHU PALIBE CHOMWE AKUTITHANDIZA , ANASANKHA KUGWIRA NTCHITO NDI CHIPANI CHA MCP ZA MOMWE NZIKA ZAO ZIKUCHITIRIDWA NKHANZA ALIBE NAZO NDIYE BOLA AZIONE KUMENEKO KUZOLOWERA KULEMBEDWA NTCHITO NKUMANGOYENDA BAWO KU BARRACKS MPAKA KUPANGA RETIREMENT, KUMANGOONERERA CHAKWERA AKUONONGA DZIKO KUZUNZA NZIKA , KUONERERA CHAKWERA AKUPHA CHILIMA NDI ZIMENEZOTU SIPAJA AMANGOONERERA A SILIKALI A PAUL KAGAME AKULOWA MWATHU MUNO MENE AKUFUNIRA , KWATSALA PANG'ONO AKUUKIRANINSO CHIFUKWA CHA TULO CHITETEZO CHA ARMY MUDZIKOLATHU CHINATHA CHIFUKWA CHA DYERA
Anayambira muja kukhazikitsa mtendere mpaka pano osangonenena kt amakabako diamond bwanji
Rwanda idayambila kale kuba gold ndi diamond 💎 ndikumapha,anthu.nkhani,yaikulu si,kulimbana,ndi zika koma kuba gold yo akumamukumbila mu ziko lache.kagame,ndi wachabe kwambili kumuona,kuonda koma mutima mwache woipa.moti,ku Malawi kuno,ku kasiya ikayambika ntchito yokumba mwala azanamaso kuti, ku Malawi mukutsunga, zigawenga.cholinga,azabe.
Amalawi mukuma yankhula nkhanngati ndinu mfiri nzeru lulibe nangaimnyamata wazisukulu zanu basi kuchilimika kuka tchula and blaming president coz of war
ASILIKALI A MALAWI AZINGOFA KUMENEKO NANGA ALI NDI PHINDU LANJI KWA AMALAWI?A MALAWI AKULIRA PANO KOMA IWOALI KAKAKA KU MBALI YA BOMA NDIYE IFE AMALAWI TIZIWADANDAULIRA KUTI CHANI IWO AKUDYA NDI BOMA AKUTHANDIZA BOMA .BOMALOMWERO LIWALIRIRE
South Africa asilikali amwalira pano chiwelengero chakwana 13 omwe amwalira.
Moti mwadziwa kumene kuti Rwanda ndiyonwe imapanga support M23 ndithandizo lochokera ku France ?
Atsiyeni akafele konko mesa ndi atsilikali chipani cha mcp .Atsiyeni
Ndiye akungofanana ndi zake kagame
Oo my ;
God we
Iost our brothers
Mesa chakwera ndikupha paja amasekelelatu anthuaziphedwa nayeso mesa ndi chigawenga chakwera ndi zake ka gameyoso kod simungakwanise kupha kagameyo kuti chakwera akhawule chakwera ndi munthu woipa kwambir hvy
Chakwela is a mmedaraa
Tibvomeleze kutkumeneko ndku nkhondo
Gululi n la kagame,la private, maiko n mabungwenso amadziwa, n wachabe ngati mukukumbukira awa sioyamba taikanso mitembo Ina kuno,ku Tanzania komanso ku SA konko.osaganiza n amene amamutenga munthuyi ngati mzao.
Guu la kagame m 23 like chikangawa
That is acivil war
Ngati zakunyatsani zaku mayiko ena musatumizeko asilikali akwathu kuno
Paul kagame roadanayi tcha dzina ndBingu koma iwe ndiwe wakuchitipa takudziwa ulibe nzeu po yankhulila nkhanii
Good news for ever and enjoyed it good newsssssssss ndpo nkhani yabooooooooooo afaso ochepa atatu basiiiiii zandinyasa bwanji onsewo anapita Amalawio zikanafa zonsezoooooooooooooo gud newssssssss
Gati amacheza ndi chakwera sizikugwirizana iyi ndi khani ina
Ndiye president wathu amakondwa anthu akamaphedwa chochi
Osangomusiila bwanji kagame athanane nazo yekha muthuopanda chikondi olo
Tonsetigwrane manja pothana ndi kagame
Asilikalathu sanayambe pano kupita ku DRCi
Bola afako ndpo afa ochepa mudikire kulandra ma shekazi omwe alimabokosi
Kagam aazabwele ku Malawi zaugalu zithe.Chakwera stop nonsense with your friend Kagàme
Ine ndakuona ndi chifukwa chaketu
Chakwera stop nonsense with your freind Kagame.No more Kagame in Malawi.Faque.
South Africa 9 aphedwa komweko.
Kodi Un mulibe azungu
Let those who no sense to be
No sense
😭😭😭😭😭😭
No sense j
Zovuta
Nanga zogawenga zafa zingati
Palibe
No sense j