Ulemu wanu bambo aife mwatilela zambiri talandila zaulele moti nyengo ya makolo athu samakwanisa kugura respect for you our father and thanks Brian potionesa atcheya
That's true His Excellence Dr Bakili Muluzi could stop just to give someone a lift in his Ministerial Car. For example is my Father (Late Stephen Eliya Banda) and myself, His Excellence the Former President gave us a lift in his Official Car while he was the Administrative General of the Mighty Malawi Congress Party.
This man! Ayayayay.....the humour is just great. Brian on a lighter note question eish.....ayayayay ndaseka mpaka misonzi. Mpaka odziponyaponya eti? 😂😂😂😂😂
Sitinaone nawo utsogoleri wanu komabe timanyadira chifukwa Cha zithu zochepa zomwe tinapeza kamba ka utsogoreri wanu taona ma k50 opanda mitu ife ndalama mumkatigaira ndi manja Anu akulu inu osati zinazi
The first program kuonera ndikuseka nawo limodzi 😊 pamene enawa kumangokhala kulozana zala basi. What a great man
Long live our former president
Respect to you our X President Dr Bakili Muluzi🙏🙏🙏💕
Long live Dr Bakili Muluzi❤❤❤❤❤❤
Pule amene anawafesa kukoma amalawi paka nthawi yochepa😢😢 mulungu akudaleseni mr muluz ndi wumoyo ndimakukondan❤❤❤❤❤
Ulemu wanu bambo aife mwatilela zambiri talandila zaulele moti nyengo ya makolo athu samakwanisa kugura respect for you our father and thanks Brian potionesa atcheya
what a wonderful interview, ViVa a tcheya, the best well dressed president in Malawi
Atcheya tsopanoooo!!! timakunyadirani president wamsangala odziwa kuseka, osakhala zinazi aaaah
Long live Dr. Bakili Muluzi
Abwanawa ndi munthu wabwino
Well spoken Dr Bakili Muluzi atsogoleri azitero tikufunilani moyo wautali pamodzi ndi family yanu Mulungu azikudalisani nthawi zonse
Bakili knows how to choose but bingu was the best ayao simuziwa economy
Nantahala ife muthawi yanu long life atcheya
That's true His Excellence Dr Bakili Muluzi could stop just to give someone a lift in his Ministerial Car. For example is my Father (Late Stephen Eliya Banda) and myself, His Excellence the Former President gave us a lift in his Official Car while he was the Administrative General of the Mighty Malawi Congress Party.
This man his is another level just hear his voice 😊
This man! Ayayayay.....the humour is just great. Brian on a lighter note question eish.....ayayayay ndaseka mpaka misonzi. Mpaka odziponyaponya eti? 😂😂😂😂😂
Achalume kuchitekete God be with you
Long live Muluzi
We will always Love you a chair.❤❤
Long live.
Quran on shelf mashala habibi
Long live atcheya❤
I like his voice
The great man 🎉❤
Munthu amene anapangitsa Malawi kukhala owawa kwambiri panopa. Chomwe ankagulitsira ma company kwa amwenye sichikudziwika
Great man
Allah akudalitseni a chair
Long live former president a chair anthu
Malawi ndi dziko lokhalo lomwe mapresident opuma akumva kukoma. Ulemu wanu a Chakwera.
Taonani a Muluzi,mayi JB, Khumbo, APM, Chilupha n ena.
Watching live from SA Durban KZN
Long live achair!we love u!
Pa town kumachenjela ❤❤❤achalume
Kuti enafe tisakhuzidwe ndi nkhaza za chipani chimodzi for that time Achair,,,munatinvetsa kukoma mu nthawi yanu❤❤❤❤❤
kuntunda 🔥
Big man ever
Much respect to our granny mumakwana 🎉🎉🎉🎉
The most likeable PULE of Malawi kuseka continuous
Big man tsopano ❤❤❤
Anamva mtunda ukufotokoza, anamva zonsezo ( I remember Mkasa's song. A Chair ndi mtunda)
Kholo pa ndale
Watch live from Nyambadwe
Nice
A Gama we love you,long live
Big man
Bakili vuto linapo ndi umbuli komanso business yake o i hope anali kupikulitsa bonya. Nfi masamba
Government doesn't run a business. It should create atmosphere for people to do business.
Ndani wamva zimenezi bwinobwino?
Ine ndinamva, tcheya si munthu wamba baba anakonza
umenewu ndi ntondo endeed
Sizaiwa former President pa free education primary sizophweka
Mwana wakwathu
Achair Allah bless you ❤❤❤❤❤
Ulemu wanu acheya timakunyadirani kwambiri potibweretsela ufulu Allah bless you more
Simungathe kusangalatsa aliyese koma ndinu big man muthu wa bwino kwambili
Atcheya woeeee!
putin waku malawi bakili
Achakulungwa wachiyao
Kuchitekete
Ndale ndi tchimodi cz muli kuba muli bodza
❤❤❤
Kumtunda
Atcheya
Achair ine ndilipo nkubwera konko ndithu
Ku machinga Kwa chikweo ndiye kwathu 😂😂😂
Sitinaone nawo utsogoleri wanu komabe timanyadira chifukwa Cha zithu zochepa zomwe tinapeza kamba ka utsogoreri wanu taona ma k50 opanda mitu ife ndalama mumkatigaira ndi manja Anu akulu inu osati zinazi
Awa ndatcheya kuchikweza kkkkkk
Mumakwana acheir
To be honest this man is a greatest man,,,,,,,,,,,,,,,,,long live Dr Bakili Muluzi we love you very much ❤❤❤❤
Achalume koma atcheya mmm amathandiza
Sogoreri aziseka abale .Atcheya inuyo ndati inuyo inuyo Atcheya mulungu azikudalitsani
Mr fake money... Kape wina amene anazesa mavuto mmalawi.kugulitsa ma company chitsiru
10:20
Bambo anagwila ntchito yotamandika awa. Mulungu adziwapatsa dza bwino iwowa
Atcheya mmakwanila
Tcheya ndikaswiri
Bigy...
Muthu wakulu kwambiri
President olankhula zonveka bwino,,,not zinaziyi
Byson mwaona
M,tunda wa m,ndale
A Chair palibenso
Tate wokondeka
Kungogulitsa ma company a boma basi ndalama kupochera achalume anali ochenjera
professor
Tionele zimenezi
Kungocho kela kuchalichi kuvuna udndo ngamti chakwera
Awa anali adindo
Achalume🥸
Uyu ndi amene anayamba kugwirisana ndi amwennye nkhani yobera amalawi
Achisilu inu
munali munthu
Munthu wamkulu
Munthu wamkulu ❤❤
Mbava iyi ndi yomwe inaononga zuko lamalawi
Achisilu inu you know not
Umbuli
Owononga sukumuona
By mentioning Late Chikufwa Chihana he was being honest, that name contributed a lot to Malawi democracy!
Mukatero ndinu mtumbuka , mumapopanatu
The worst present ever
Anakulamulirabe 10 yrs for sure