One day I misjudged Jonah Pankuku on this program with regard to UTM withdraw from Tonse Alliance, however, after analyzing him for the past 30 days I have concluded that he is a real journalist, non-bias and wise contributor. Unfortunately, in Malawi there is only one TV and Radio that's; "TIMES"
Zomwe report ikunenazi is it egual pa zomwe zinakambidwa ndi Minister of information pa 18 June ngozi itangochitika kumene ndiyeno communication yomwe amanena yomwe unalipo pa nthawi yomwe ndege imanyamka from lilongwe inatheka in what ways hence report likuti ngegeyi inalibe zinthu zoti ndikutha kulumikizana nawo ma pilot, bvuto amalawi mumati tenga ngati anthu osaganiza aii
I like the program koma the rush is putting us off guard. You can not be cutting zoyakhula saying chifukwa cha thawi. Almost every one of you guys is saying chifukwa cha nthawi. Either you have too much to say or you have limited time indeed. Improve
Anyamata inu anthu andalewatu enawa sakulila ndipo alibe chisoni ndi imfa ya chilima koma kuti instead atengelapo advantage yoyendetsela ndale zanu for the benefit of u all akupha.mudapha njaunji ,chasowa,malubino,gadama ,chiwanga.nonse akupha inu.
A Wonder ndi a Pankuku you are diluted, kodi statement yoyamba ya mtsogoleri anati chani? Ndege inadzadza a Chimunthu anatsika kenaka statement ina ndege a pulezident akuti inabwezedwa ku Mzizu chifukwa chachifunga. Dziwani kuti kunja kuno muli Mulungu.
Ine sindingakhulupire report la chikangawa anayamba kunama ngozi itachitika kt ndege inafika ku mzuzu pomwe sinafike..amapanga za kafukufuku ndi aku German report lisanatuluke iwe anapita kumweko amakatani...kunamizira kumakwera njira..khalan ozindikila Malawi ..ichi chikangawa ndicha satanic
Chindege mkati kumachita kuwoneka ngati chi bus cha concord ,ndiponso ngakhale nditakhala ine chindege chija sindingakwelemo .inu chithu chouluka mmwamba koma chosasuka nchonchija kkk
Report yomwe mkunenayi palibe chomwe ingazanene kuposela pa primaliry report yanuyi aii cz nkhani mwaisintha cz ngati mkut ndege mnalibe zipangizo zopangila communicate ndiyeno information ipezeka bwanji mkamakhala muziziwa kuti a malawife ndi anthu oganiza this is new generation report ili ndilabodza it's fake zalowa ndale izi period
Pa nkhani ya report pakhala povuta kuti ife anthu tilirandire report mdi program pamene boma linauendesera maliro a anthu 9 sizikuhwirizana. And amapita lukatani ku Germany? Pakhani ya report palibe chazeru mwalakhulapo bwezi mukanasiya. Mwina poti zaveka kuti muli nawo paulendo waku China. Timakukondani koma apa pokha sindinakuveni amalawi tikuona patali kwambiri
Very good speech yanu anyamata inu
My question is, by the time this plane get late kasambala, those devices were there or not?
Ngona zamabango izi a mwadya chibaz bc
Muguys mwayankhula bho hvy mosayanga'ana mbali kaupangiriso Ka bho
We Love you Guys very Much....Timakunyadirani kwambiri ❤❤❤❤❤
I agree with you guys 100% , lipoti siikukamba zomwe amafuna kkkkk
We love you guys very much, you're more less like western journalists. TIMES TV is like BBC now.
Ndalama zimamusinthadi munthu anyamatawo asochera poyerayera ndithu ,guys ntchito yanuyi ndi kulandira ziphuphu it's parallel,zamanyanzi ndithu.
One day I misjudged Jonah Pankuku on this program with regard to UTM withdraw from Tonse Alliance, however, after analyzing him for the past 30 days I have concluded that he is a real journalist, non-bias and wise contributor. Unfortunately, in Malawi there is only one TV and Radio that's; "TIMES"
Zomwe report ikunenazi is it egual pa zomwe zinakambidwa ndi Minister of information pa 18 June ngozi itangochitika kumene ndiyeno communication yomwe amanena yomwe unalipo pa nthawi yomwe ndege imanyamka from lilongwe inatheka in what ways hence report likuti ngegeyi inalibe zinthu zoti ndikutha kulumikizana nawo ma pilot, bvuto amalawi mumati tenga ngati anthu osaganiza aii
I like the program koma the rush is putting us off guard. You can not be cutting zoyakhula saying chifukwa cha thawi. Almost every one of you guys is saying chifukwa cha nthawi. Either you have too much to say or you have limited time indeed. Improve
Mukatero warandira ndrama a garu inu. Mwalandira zingati kodi makape inu
Anyamata inu anthu andalewatu enawa sakulila ndipo alibe chisoni ndi imfa ya chilima koma kuti instead atengelapo advantage yoyendetsela ndale zanu for the benefit of u all akupha.mudapha njaunji ,chasowa,malubino,gadama ,chiwanga.nonse akupha inu.
Oooooooh ndalama anakozadi ndithu
Ndiye akambe zabodza ndiye kuti sanapatsidwe ndalama mesa akunena zoona
Woooooo a times basi kuopyezani mwayamba kukhala ndi mbali
Apasidwa ndalama ati satana sakufuna akapse yekha mpake anthuwa akomedwa ndi za dziko asankha satana awa
Kuzimva kudziwa chizungu ndikuwerenga kwambiri inuyo aaaaaah.....komaso zinazo adafufuza or kuwuzidwa? Who told them?????
Anthu akutuluka mbuzi inu. Program mumusiyire Brian banda ndi bishop chafumuka inuyo ndi zitsiru.. Ndege imanyamukiranji akuziwa kuti kuli nkhungu?
A UTM akufunanso president yemwe akumuloza chala kuti akhazikitse commission of inquiry.How?
A Wonder ndi a Pankuku you are diluted, kodi statement yoyamba ya mtsogoleri anati chani? Ndege inadzadza a Chimunthu anatsika kenaka statement ina ndege a pulezident akuti inabwezedwa ku Mzizu chifukwa chachifunga. Dziwani kuti kunja kuno muli Mulungu.
Kodi kuzungulira kwa ndenge Ku chikangawa kumeneko ndikuwononga? Kodi kunkuyu sananene KUTI black box adayisunga?
Ine sindingakhulupire report la chikangawa anayamba kunama ngozi itachitika kt ndege inafika ku mzuzu pomwe sinafike..amapanga za kafukufuku ndi aku German report lisanatuluke iwe anapita kumweko amakatani...kunamizira kumakwera njira..khalan ozindikila Malawi ..ichi chikangawa ndicha satanic
Kodi guys mwagundika ngati munamiza ana what about anthu anapezeka opanda zovala kodi ukunaso kunali kukhalisa kwa ndege?
Chilungamo chiyende ngati madzi 😢😢😢😢 chakwela komwe uliko hmmm 🤔🤔🤔🤔
Nimbama yakumasod 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 tiona zinthu ndithu
Wander this is the report from capital hill.... Not Germany aviation expats. Tiyeni nazo zitichoke nde zachitika apa
As a country , we should minimize importation of luxuries such as cars ,and comfortable items for the Luling elite .
Bon kalindo uja osadzamudelera
Kodi zachulugam athu anauzidwa kuti welukani muzaambaso mawa ndizowoona tiyeni tiziyakhura zooona kunjaku kuli mulugu
Inu kupha anthu amachita mnjira zosiyana siyana kuchedwatsa nthawi yomuthandizira munthu dala ndikupha
Achunga ndi anzanuwo dyelanitu ndalamazo likubwela tsiku musanza zimenezo mizimu ya anthu 9 ikukunvani muziwona mulimbetu
Agaru awa ayambadi kudya drama apa ndakhulupiliradi
Mwadya bread inu ndipo ngati ndi chocho program yanu ya Hot current mungoyithesa. Osamangotithera bundle apa
Kukhala ndani inuyo kuti mfike poletsa program?
Big up bayana chule
A techinical sangatuluke okha,,boma snalamula kuti oziziwa abwere poyela
Chilima anachita kuphedwa inu.kodi ngozi ya ndenge yimavula zovala? Yimavula sapato?
A wonder mumati mungatani.
Times yakhalaso ngati zodiak mmm.
Ndege yamatenda kale, kukanyamura tsogoleri wadziko, matenda alipo ambiri
Anyamata inu machende anu chilungamo mwayamba kuchisiya
Pologamu yanui wenao alandola ndalama chilima sibalewawo adakakhala m,balewao sadamalankhula mopusa chonchi kodi ngozi imavula zovala imatenga mafoni
Chindege mkati kumachita kuwoneka ngati chi bus cha concord ,ndiponso ngakhale nditakhala ine chindege chija sindingakwelemo .inu chithu chouluka mmwamba koma chosasuka nchonchija kkk
Kodi awa kuyakhula kopusa kwaoko amaonangati Ife zimatisangalasa ndimene zikoli likukhalilamu andevu zamwayi muzisamala pofuna kuyakhula zikoli anthu akulila kwambili ndiye muzisamala
Anyamata inu mumalankhula chilungamo opanda mikwiyo mumtima Koma brain amachita kuonetsetatu Kuti alindimkwiyo ndipo akujama ya gogo kunyanja
Kikikiki ntungule ma battery andeke
Mukunena zimenezo koma mukuganiza? Mafuta mmene akweleramu nde mukutichani kkkk ngati akulonjwzani kuti muzalandila aulere ife zisatikhunze mukuziwa impact yake kungokwezanso mafuta osamakonda anzanu bwanji ? Miyoyo yoipatu imeneyo kulankhula ku gulu laanthu osamazitenga ngati inuyo nde opambana ai mafuta asakwele basi makampeni ife tivulazidwe kamba kofuna kuti mafuta Zizagwila ntchito pakampeni aaaaa kk.
Report yomwe mkunenayi palibe chomwe ingazanene kuposela pa primaliry report yanuyi aii cz nkhani mwaisintha cz ngati mkut ndege mnalibe zipangizo zopangila communicate ndiyeno information ipezeka bwanji mkamakhala muziziwa kuti a malawife ndi anthu oganiza this is new generation report ili ndilabodza it's fake zalowa ndale izi period
Tinakusowani a wonder
Chilima will never be forgotten 😢😢
The guity are afraid to institute a commission of enquiry of the Chikangawa tragedy .
Kodi zikutani sikumvekatu mau mwatani Kodi paja mwadya zimabanzi anyamata Inu timakudarilani koma apa ayi ndithu tamva kale kut mwalandila ndalama
Mbuzi izi zadya cash
Shee!! Anthu Pali CHOTI muzitukwanila azanuwa? Azanu akugwila nchito away, mukufuna nawoso azinama nawo mabodza Ali kunjawa? Koma mukudziwa kuti moto wanu ulindi chimalizilo? Muziwopa Yehova anakulengani Inu. Kutukwana kumeneku mukudzipalira Makala Amoto inu mukanena chiyani pamaso pa Mulungu. Ndalë mudzazisiya pasi pompano. Bible limati usamunamizile mzako. God have mercy upon people of Malawi.
Zomwe mukukambazo ubwino wake bon kalindo wanena kale kuti kutipeza ma activis enaaa alandila makobid ndi anamapwala awawa akuthoka nyero zawozii awaaa mapwala anu anamakhatcha kumthumboko ,,,,komaaa muziwe kuti ndalama zo mudya komaaa muziwe kuti kubeleka ndikumodzi mmene munavel mawondo anuwooo ndimmeneso adavela amene adaluza abale awooo kumtumbo kwanu ma illiterate kunyero kwanu
Awonder wayamba manyiii ndianzakowa cz ife tikudziwa kut Chakwera wapha Chilima cz black box ilikut GBS adayisokonedza ndani adali ndicholinga chanji afisi Ng,ona zi mwayamba kuzibakira anapamtumbo inu nanunso akudyeserani
Andu zamwayi mwayamba kulemela eti manja akudao
Koma vuto report likukamba zina zosemphana ndi zomwe apulezidenti anatiuza
They're now talking this guy's
ndinu opusa kwambiri
U t m ilowe ku dpp tigwetse chakwera anyongedwe basi chifukwa dpp ndi u t m kukhara limodzi chakwera adzanyeredwa sadzampatsa or mpumulo
Pa nkhani ya report pakhala povuta kuti ife anthu tilirandire report mdi program pamene boma linauendesera maliro a anthu 9 sizikuhwirizana. And amapita lukatani ku Germany? Pakhani ya report palibe chazeru mwalakhulapo bwezi mukanasiya. Mwina poti zaveka kuti muli nawo paulendo waku China. Timakukondani koma apa pokha sindinakuveni amalawi tikuona patali kwambiri
Pakuku lero ango khosomola abwela anyiniyake a ttv
Mwadya sikono agalu mboli zamanu.mukuikila kumbuyo zaboza.bus ikapanda kukhala ndida zokwanila amayigwila analola bwanji ku mpasa vp ndenge yopelewela zinthu
Ndinu achikangawa eti?Zopusa basi
Munagudwa inu kuboma
A Msiksa mwafika pamenepa zoona
Inu nde mmayankhula zabhoo
Chotupa chija chaphulika nchere uja anthu adyadi.
Chifukwa chiyani ndege adailora kuyenda
Mwanya ndalama ku china munapitako tamvakale
report was edited this is not original report
Inuyo guys mumatiimirira amalawife
Makape awawa Ali mbali ya boma
Awander wadya bans ya mcp
Musatinamizepo inu
Skipping too much
A mcp inu mukuchita kuonesela
Ziko lathu ndi lolemera chifukwa zambiri ni zaulele 1madzi
Kujeremani amapitako cakwelayo
Paja awa awadyetsa banz
Ndakhumudwa nanu a Chunga enawo ndesindiwakhulupilira nkale. Nkhangazawona idakamba kale kuti mwalandilako kanthu ndesiizi 😢 ayi ndithu tingompempha mulungu atithandize pamavuto azangozi ya Chilima plus nkhaza za mcp, ndikukwera kuononga ndalama zaboma mmmmmh. RIP Saulos Chilima and anthu onse anakhudzika paimfayi ndi lucius banda. Lero limenelo achunga ndia wonder 😢 iwe manganya tukuonatu Ohoo mzimu wa president wathu ukukuonani ndipo udzakantha
Brian Banda mwinako ndi Pankukuyo ndimaonako kuti ndi bola
Mukatero mwadya chibanzi
Madolo kwambir 😂
Your full of sheet you guys 😢
Tinava kare pankhazawona
Why you so beating the bush
kuswakuswa
Nabobolelmba
very stupid report
Zaboza basi
Mwadya bans inu si amalawi
A UTM akufunanso president yemwe iwo akumamuloza chala kuti akhazikitse commission of inquiry.How??