What Baghaya says there is reference. Chakwela was poor when he was leading the Church but now is parted with God is swiming in monies. Think on this area of his line of thinking.
Ase iwe ndiwoputsa basi ifetu kuchani sitima sililako olo pangono bolaso ku South Africa if koma USA 🇺🇸 Chitsilu kwabas jb sangafane ndiwe jb ndi dolo dzinga bunyila kumeneko basi
Koma poti akagula chinsapato chodula chigalimoto chachikulu kumakhala kulira izo ndikhoza kumpanga tag wina ati kupita ku HD kuti tiziti zikuyenda ulira magazi adha
Amwene,muleke kudya achule kumeneko ndi njoka zija, your body is responding badly to those kind of food.Langizo la ulele.Look at the mirror, and see how your body looked like before.
Aliyese ndidolo payekha komaso adha awawa ndi dolo pazomwe amathazi, even JB ndi dolo pazomwe amatha zija, aliyese azipanga zomwe amatha aliyese ndi dolo nkhani ndi ma facts bas osati dolo who dolo what
Uyu amati mouton baghaya uyu amaoneka ozelezeka
Ndee silamu saziwa Yesu kd?
Umakwana Man,am from South Africa Cape town.
Mbuzi ndiweyo ndinkhope yonyasayo iiiii
Komano bwana kuzikweza kwanuko ndinkhope yanuo sizikugwirizana be humble ......only death will humble you
I'm muslim bwana yesu timamudziwa asilamu tamunven uyu akut yesu sitimudziwa iwee
Adawa kodi ndindani guys .....r u okay my brother😂😂😂😂
Aslamu amakhulupilila aneneli onse amulungu, kuphatikizaso yesuyo
Onyasaiwe
akulu inuyo ngati mukuphudzila kuchenjela ngani yamulunguyi chonde muyenela mulape ndalama dzodzisisiya
Umuziwe yesu iwe
Koma Wabunyula kale . ameneyu...?
We are one Malawi, let tikakhe a youth, for future
JB NUMBER ONE ❤
To be honest this guy has hit the facts
Zomwe ukukakamilazo zoti JB anayankhula bwino zachani
Ulibe zelu iwe
Ndimaganiza bho chifukwa cha iwe brother ❤
Mulungu aliko iwe usiye kusakhulupirila Mulungu, zimene ukuyankhazo zikuonekadi kuti iwe sukhulupirila Mulungu, koma ziwa kuti Mulungu ndi nzimu ndipo saoneka ndimaso choncho kunena kuti Mulungu kulibe ndikulakwa.
Acha matusi mwanakwetu 😂😂😂 wamkenya lori
Iweyo unatukana malemu Bingu directly apapa waoneka kut ndiwe wabodza. Ukuyankhula moziyeneleza iweyo si munthu wabwino
Iwe ulije zeru
Iwe morton beghayo Jb azakusowesatu
Kodi mukugañiza tizitha ma data nkhani zake zimenèzi ùkumamuyàmba dala JB
JB ndinamùziwa kalekale ndili mwanà ndipo akàmatùwaña aatukwaña amfiti amcp
Usauka ndi Mzimu omwe
Koma nditukwana kwinako 🥴🌚
Ubwera liti
zoona a jb amalankhula za mulungu mene akutukwanila jb mwina sakuziwa kut akutukwana
Ichi pena chimathoka wise 👌 mutabaluka. Koma zomabunyulazo
umu muli nzeru zakuya
JB amaziwa chilungamo ❤
Iwe opoira kwambili nkhan ya mulungu musazakambeso muzingopanga zanuzo apa
Achisilu awa pachkamwa tawaonen😮
Only jb ndi dolo
Awa ndobowa koopsa
Iwe usamupute JB ohooo 😂
Komano iweyo uli ndi ukape pang'ono
Koma nde chinkhope cho dzadzana 😊
ichi ndichisilu kwabasi machinde ako pamozi ndi mcp
Ndiwe galu kwanasi
Ndinu achitsiru abambo
Baghaya ponyoza Mulungupo iweyo Moyo wako uli pa moto
Ine uyu ndikamuona amanditchititsa mantha. Ndimaona ngati ndakumana ndi chipembere mu nkhalango
Nkhopeyo ukuonekadi kuti ndiwe kape kwambiri
Machende akò JB usamamuyambè kodì iweyo wamwèlà liti
Jb ndi top chatter
😂😂❤ akumanapo machine okha okha morton v JB❤❤
Kape iwe mbuz
Inu malonekedwe okha sungallibane ndi JB ukuzivuta zomeleza kuti JB ndabwana ako ndipo JB akhuza kudyetsa banja lako lonse moyo wako onse
Akulu inu ndi ambuzi et
inuyo amwene mulibe zeru 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Ineso ndine mtumbuka kwen iwe ndiwe mutu wako ngukulu wambula zeru
Kukumpangitsa ndikukula Mphunoko chinkhope Chikwinyikacho koma iyeyu sichoophyezela Anthu Aaaaa Ayi Ananyanya kunyasa kwambli ndpo alibenso fundonkose
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Mphuno kuphatikiza ndi maso
😂😂😂komabe iweo aseh ine ndudabwa nawetu
Nanu mutu ngati nsabwe iwedi ndiozerezeka jB samana
Timawufuna kusintha life Koma connection Mr Bra
Panyapako ayise udzafa ifa yowawa galu iwe machende wamako
Iwe ndiosekoneza za mulungu useretu akulanga
There's still sense
chiyambi cha nzeru ndi kuopa Mulungu .
Ngati ukunenetsa kuti unasankha JEGENA,dikira mayankho a MULUNGU akupeza
Iwe mesa unamutukwapo the late bingu wamuthalika anakudzudzula ndani
Muuze zoona bro
Kkkkk esssshiii
What Baghaya says there is reference. Chakwela was poor when he was leading the Church but now is parted with God is swiming in monies. Think on this area of his line of thinking.
Kodi zopusazi simungasiye muyambe kunena zina zakuti zizithandiza anthu ena kunjaku
iwe usatinamize Ife Kaya ndindalama zikupwetekesa kuyambila lelo uziwe kuti mulungu aliko komaso moyo wakowo anakulenga ndi mulungu
Amati kulibe mulungu pita uko iwe
Koma uyuyu
Ndiwe mbuzi iwe
Komabe aise osazaphweketsa strength of street knowledge
Akulu ngati umakulupilira kuti mulungu kulibe ndiyekuti inu ndiatchisil galu mukukula mophephela kwambiri
Iiiiiiio ndi mbuzi yamunthu
Opusa iwe galu iwe
Ase iwe ndiwoputsa basi ifetu kuchani sitima sililako olo pangono bolaso ku South Africa if koma USA 🇺🇸 Chitsilu kwabas jb sangafane ndiwe jb ndi dolo dzinga bunyila kumeneko basi
Iponden fada😂
Plz try to do things inorder becouse utha kukhala munthu wafunika ku ziko coz mindset change 😅mwa iwe ilimo 😅😅😅
Wunenesko baghaya
Iwe ndi mphwala leni leni..!! 😅
Umawopa kutukwana boma,Koma sumawopa kutukwana mulungu pomwe jb amawopa mulungu koma samawopa munthu (boma) pamenepo wazeru ndi ndani❓❓❓❓
Inu nanu nde mukucita ku ciuza cicakwera cakoco zaziii JB nd wa bho cikhope ngat 👹
awa ndiopusa basi
Inu ndi opoila mn koma
Nagona mochedwa kwali natolapo chazelu kwali nadokelako business iyo
Chigafa sayika wireline.
bwelaniko kudziko laeniko mwapepelako mpaka mwayamba kukana kuti mulungu kulibe coz muli china
Iwe ndi mbuzi
Koma poti akagula chinsapato chodula chigalimoto chachikulu kumakhala kulira izo ndikhoza kumpanga tag wina ati kupita ku HD kuti tiziti zikuyenda ulira magazi adha
Paja school sichotsa uchitsirudi eti anthu ophuzila kumanyozana pamaso padzuko lose
Machende ako boy ukurimbana ndi chigawenga jb simpare wako
Iwe ndi nkhukhudi
Koma mangani nyumba
Oupusa iwe onena kuti mulungu kulibe mbuzi ya muthu iwe kuyipa nkhope ndi mtima omwe
Zinangochitika kutii uli ku china koma kachimidzi kalimo man
King baghaya am zambia open company which business starting
Ndayesetsa kumvera zaoneselatu kuti mutu mwako muli mphemvu, iwe undikila bwanji court pamene president ndi amene amalamulira zonse mxx,
Amwene,muleke kudya achule kumeneko ndi njoka zija, your body is responding badly to those kind of food.Langizo la ulele.Look at the mirror, and see how your body looked like before.
Amalawi mchifukwa chake sititukuka kumangolimbana nokha nokha 😂
Koma inu man ndi opoila sungafane ndi JB
Kodi Morton pakati pa JB ndi iwe omphudzila ndani?
Galu iwe
Aliyese ndidolo payekha komaso adha awawa ndi dolo pazomwe amathazi, even JB ndi dolo pazomwe amatha zija, aliyese azipanga zomwe amatha aliyese ndi dolo nkhani ndi ma facts bas osati dolo who dolo what