OSAPHWEKESA OMWE AKUTULUKA ZIPANIWA..zachitika ku south Africa tiphunzirepo..HOT CURRENT 02/06//2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 27

  • @OwenMajoni-qv3eg
    @OwenMajoni-qv3eg 3 місяці тому +2

    Kodi zomwe anagwirizana a chilima ndi a chakwela, mu malamulo a dziko la Malawi zikuloledwa? Kapena malamulo asinthidwanso?

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 3 місяці тому +1

    Andalewa ndi amene akupitiriza kuononga dzikoli

  • @MuhireDominic-rw4vf
    @MuhireDominic-rw4vf 3 місяці тому +1

    Hot current 😂🔥

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 3 місяці тому +1

    Dyela ndiloipa kwambili,,umaiwala lonjezo

  • @stevenbanda2409
    @stevenbanda2409 3 місяці тому

    Vice president, wamwa ambuye mutengeni, waononga UTM. 😂😂😅

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 3 місяці тому +3

    Ndiwolose ndikakutafune anatsikira bwato pakati pa nyanja, atawona mafunde.

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 3 місяці тому +1

    Let him stand and fail miserably shame oh him agalatiya

  • @Allan-bk1
    @Allan-bk1 3 місяці тому +1

    Kkkkkkkk mpakana zezeze eti

  • @ishmaeldama8906
    @ishmaeldama8906 3 місяці тому +2

    UTM ikuchedwa kwambili koma Bon kalindo adayankhulapotu izi

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira 3 місяці тому +1

    Ine ndikuona kuti anthuwo anakambirana nso kachikena kuseri ndipo a Chilima akudziwapo kanthu adagulitsa chipani chawo ku MCP ndichifukwa chake angosankha kukhala chete

  • @HopeLiwonde
    @HopeLiwonde 3 місяці тому +1

    Km Wanda

  • @Allan-bk1
    @Allan-bk1 3 місяці тому +1

    Kalumo timuuzire chilima athana nae

  • @charlesmapiri3854
    @charlesmapiri3854 3 місяці тому +1

    A ndevu zamwayi cnt shed his mcp bias

  • @FosterChakanga
    @FosterChakanga 3 місяці тому +1

    Lakukhalani lopha ng'ombeyo bwana.Mumakwana guys

  • @EmilyEmuzy
    @EmilyEmuzy 3 місяці тому +1

    Yes Mr Maphang'ombe lakuyanjani ndithu chifukwa simunyengelera Azibambo inuyo always be true more 🔥🔥. Koma Abanda tawasowatu

  • @hardworkkayuza6353
    @hardworkkayuza6353 3 місяці тому +1

    Firs to comment

  • @danielsulani8689
    @danielsulani8689 3 місяці тому +1

    😂😂😂😂oganiza boh!!

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 3 місяці тому +1

    Wonder ndale suidziwa,,unvetsele a pankukuwuwo ndi a Chunga

    • @maxwellmajawa6091
      @maxwellmajawa6091 3 місяці тому

      Yatokhara njilwa ?? Kuti asaiziwe?? Mulibe zonena

  • @isaacchipatala1618
    @isaacchipatala1618 3 місяці тому +1

    SKC my vote

  • @thomantony433
    @thomantony433 3 місяці тому +1

    Best ❤ 27:29

  • @Marlu_AmJustReadingNews
    @Marlu_AmJustReadingNews 3 місяці тому

    Chakwera said he will be on the ballot...he didn't specify kuti as a what. President or vice. 2. For their agreement to achieve, Chakwera needs to win at MCP convection ...so I don't see why people are not seeing this...unless Chakwera will try to betray Chilima after convection

    • @jumbradoone4164
      @jumbradoone4164 3 місяці тому

      Ba Ballot iyeyo adzayimira ngati president... Sukunvapati?

    • @jennyx6914
      @jennyx6914 3 місяці тому

      umvetsere bwino statement ya chakwera iwe ndi kachizungu kako ka ku cteache..he dint say he will be on the bsllot but he said If they will chose him then he eill compete.this means as Apresident paja anayamna ndi mawu oti Malamulo adziko lino limavomereza kyyima kawiri
      ndiye iwe nawenso ndiwe mbuzi sumvetsa