NKHANGA ZAONA KULINDERA(RSA) KUNALI CHIPWIRIKITI POMWE AMALAWI AMAMENYANA NDI MZIKA ZA KU MOZAMBIQUE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 1 жов 2023
  • Tidzwe tv

КОМЕНТАРІ • 25

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 6 місяців тому

    MCP government please help people 😮

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 4 дні тому

    Zosakhala bwino ata

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 9 місяців тому +1

    Embassy wathu wakuno Ku south Africa ndi wa chinyengo

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 9 місяців тому +2

    Zosayenda azanga

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk 9 місяців тому +1

    Zomvetsa Chisoni kwambiri

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f 9 місяців тому +1

    Very sad

  • @ebstonekonzani9126
    @ebstonekonzani9126 9 місяців тому

    Malawi nayetu wafika powawa, komanso anthu nzofuna

  • @AmosBook
    @AmosBook 6 днів тому

    Pitilizan antanyuwa

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 9 місяців тому

    Our malawian government will not going to do anything , because leaders are busy with corruption ,may be another government to come .

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n 9 місяців тому

    Boma la malawi ndi lindera kale zikungofanana

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 9 місяців тому +1

    Apa nde MCP yaonjezatu

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 9 місяців тому

    Komaso ukakhala kuti unapalamula mulandu,khaya unagwilira,unaba Galimoto...ukaseva Jere mwina kwa 5yrs amakutulutsa kukutumiza ku LINDELA REPATRIATION CENTER,komwe umalandilidwa ndi AZibambo ABOSASA,ndieno umatha kukhala 120days,ukamaliza kuseva 120days,,,ufuneusafune iweyo Deportation ukasevele Jere ku Mpanje....Baba muliapa ndikuzeni...ukamachita zofuntha ku LINDELA, Bosasa imakuswa mpaka kumalira mchilankhulo chakwanu...!!..

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr 9 місяців тому

    Inu madgage 5 mavuto akuchitukawa kufa chiwawa anthu kubedwa ndalama zaanthu zabwera chifukwa chanu komanso ndiinu nomwe muchite kuti lusifala chakwera achoke ndipo mukapanda kutero minyama ndiyanu moyo wanu onse😂😂😂😂😂

  • @MaggieGondwe-vn2wx
    @MaggieGondwe-vn2wx 9 місяців тому

    Mulungu alowelelepo ndithu

  • @user-nz8mq4ff3e
    @user-nz8mq4ff3e 9 місяців тому

    Nkhangaaaaaaaàaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaasaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaàaaaaaaaaaaassssaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaàaaaaaaazaoooooooooooooooooooooooo oooooooooooooooooooooona mulibwanji a Malawi anzaga kulikonse kumene muli Lelo pa 2th October Mr tanyiwa

  • @user-dt8nr1zx6e
    @user-dt8nr1zx6e 9 місяців тому +1

    😢😢😢😢😢

  • @user-vv9xu1gv3k
    @user-vv9xu1gv3k 9 місяців тому

    Boma limene ukunenalo boma lake liti ? Asiye Kuba ndi ziphuphu

  • @anniephiri7273
    @anniephiri7273 9 місяців тому

    Tikaonetsetsa anthu amene akubvutika kwambiri ndi amene anali pa tsogolo kuti boma lisintthe ooo sory

  • @user-pn7ek7wb7n
    @user-pn7ek7wb7n 9 місяців тому

    Zaziii kawatulutse iweyo

  • @DuncanChilole
    @DuncanChilole 9 місяців тому

    Sad

  • @paulgodfrey3361
    @paulgodfrey3361 9 місяців тому

    Heeeeeeeeeee zovuta

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 9 місяців тому

    Zaziiiii how many Times Malawi ikutumiza transport Kuti azibwela koma kumabisala mapeto ake akakugwilani kuyamba kulira

    • @amabhohlela.3492
      @amabhohlela.3492 9 місяців тому +1

      Inenso 2016 ndinalikomweko,,ndinakhalako 120days...Ku Lindela Repatriation Center ku makhala ndewu zoopsya,kusongola ma mswachi kumabailana..ndie kumakhala aZibambo aBosasa Security,ndie kumakhala kuphulitsa ma tear gass,ma Rabber bullet...yeah zimakhala choncho ngati ulindindalama umatuluka ngati ulibe Ndalamayo umaseva 120 days kenako kuzakutulutsa. Ndie osadandaula ai!!

  • @user-ws2er8ty5d
    @user-ws2er8ty5d 9 місяців тому

    Lindela it's not a prison why are you showing prisoners pictures lindela it's a waiting place to be deported but now their not deporting anymore

  • @user-zk5nu5fh6l
    @user-zk5nu5fh6l 9 місяців тому +1

    Watha chakayo mwina ndi mbava ameneyo anzake akutuluka konko