Evance Meleka... paying last respect to soldier Lucius Banda

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 24

  • @ObvidinhoBalalasJnr
    @ObvidinhoBalalasJnr 2 місяці тому +4

    Receive your flowers when u are live... U r so talented GOAT 💐💐

  • @johnchilima6351
    @johnchilima6351 2 місяці тому +3

    Soldier's soul was smiling kuona how memorable he left
    Ameleka ulemu wanu

  • @justiceziyewe7305
    @justiceziyewe7305 2 місяці тому +2

    Meleka ndi GOAT.. RECEIVE UR FLOWERS WHILE UR ALIVE 🎉

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi 3 місяці тому +2

    Komatu kunabeba mmmm ngati sikumaliro 😂😂😂😂❤❤❤ Lucias wapita akumwetulila

  • @Isaiahbotoman
    @Isaiahbotoman 2 місяці тому +2

    Eeeee meleka ndi goat ❤

  • @tukuramartin1112
    @tukuramartin1112 2 місяці тому +1

    I watched this live, it was really an outstanding performance

  • @LeonardJere-h8s
    @LeonardJere-h8s 3 місяці тому +2

    Congrats Evance Mereka

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli 3 місяці тому +2

    Anthuwa akuimba mene akuimbila ndipo ngat zili zoona boma likumamanga anthu akuimba ndiye kut ngakhale overa nyimbo za lucias azimangidwa chifukwa kwamene sanaphe munthu palibe chifukwa chomangira anthu koma ngat mukuziwa kut munachotsapo zimu wanthu ndiye kut mukungokunbukira zomwe munachita zomwe anthu ambiri sakuziwa mukuziwa ndinu ndinamalenga

  • @pempheroraynnoxmpesi8713
    @pempheroraynnoxmpesi8713 3 місяці тому +1

    Nkasa is a vibe😂

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 3 місяці тому

    Eeeeeee❤❤❤

  • @FredStenala
    @FredStenala 3 місяці тому +1

    Ndiye apachomumangila chikhale chani?

  • @EllieMvoso
    @EllieMvoso 3 місяці тому +1

    Meleka iweyo ndi one

  • @MacEmmanuelMkhamula-sy1ff
    @MacEmmanuelMkhamula-sy1ff 2 місяці тому

    Pumani bwana😢

  • @JosethaundiMateus
    @JosethaundiMateus 3 місяці тому +1

    palibe nkhani yomumangira apa chakwera wazolowera kumanga anthu

  • @wilsonchampopa7408
    @wilsonchampopa7408 3 місяці тому +1

    Eeeee koma evance meleka ndi dolo

  • @siyabongantombela9833
    @siyabongantombela9833 2 місяці тому

    Kumaliro kapena kuchinamwali

  • @kingsleymwitiwa9114
    @kingsleymwitiwa9114 2 місяці тому

    Born rastafarian

  • @LeonardJere-h8s
    @LeonardJere-h8s 3 місяці тому

    Enance ndi Dolo

  • @GetrudeGama-gu5rb
    @GetrudeGama-gu5rb 2 місяці тому

    Acakwera mukundiopsya ayi zikomo😂

  • @jasonbenardosunthenimwale5482
    @jasonbenardosunthenimwale5482 3 місяці тому +1

    Kkkkkk

  • @DrolieDongowa
    @DrolieDongowa 3 місяці тому

    Chomumangira ndichani apaa

    • @paurosi123
      @paurosi123 3 місяці тому

      Ndani wamangidwa?

    • @PeterChilombo-ou2cd
      @PeterChilombo-ou2cd 2 місяці тому

      komaso nyimbo inaimbidwa kalekale chakwela ulisha ng'ombe kwanu iya