Nkhani zikuchitika ku Congo

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 11 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 217

  • @marianamwanje8968
    @marianamwanje8968 День тому +10

    Akukumana ndi mavuto ndi a Ku Congo anthu akhale chete ineyo am happy, Ana opha anthu si Ana amadziwa zomwe akupanga, minister wachinyamata koma wanzeru🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥Akagwira ena asasiye ayete ndithu mbeeee

  • @ChimwemweJuwao
    @ChimwemweJuwao День тому +3

    Ndankhala ndikuyitsata nkhaniyi koma sindimayimvesesa koma ndimangowaona anyamatawa kuti moyo wawo uli pa chiopwezo mumakwana jack tayimvesesa musazafe❤❤

    • @ussimasi2458
      @ussimasi2458 10 годин тому

      Nkhaniyo yovuta kwambiri komaso yachisoni

  • @GeraldGomati
    @GeraldGomati 5 годин тому

    Ineyo ndi truck driver ndimayenda ku Congo but to say the truth this Congress they don't value life ma driver anzanthu aphudwa ku Congo ndi magulu amenewa, thumbs up to the youthful minister for coming up with the decision

  • @vitumbikogondwe5095
    @vitumbikogondwe5095 3 години тому

    We need this practiced in MALAWI. Anthu ataililanso kuno milandunyophana,yogwililila,kuba ndalama za BOMA all these azinyongedwa

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 День тому +3

    Kunoso azikwanje a mu Lilongwe anja azaphedweso

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 День тому +4

    Life sentence in prison , kumakhala kuonongesa zokudya zaboma ,
    Bola death sentence yomweyo akawononge zokudya za mulungu kumwamba .
    😂😂😂

    • @Blessings-s3g
      @Blessings-s3g День тому

      😂😂😂😂😂😂😂

    • @AUDIRIABWANALIKHWERE
      @AUDIRIABWANALIKHWERE 6 годин тому +1

      Ndikudabwa kwambiri kuwona munthu WA kupha akulira kuchonderela chosecho iyeyo analibe kuva kuchonderela Kwa amene adawapha mopandaso kuwavera chifundo oloso kuwapatsa mpata kumene Oti achonderele ndi kuva mbari yawo ngati Iwo samadziwa ngati Iwo samawona kuti moyo ndiwofunikira Kwa azawo nde akufuna adziwire pa Iwo?Kudzikonda Kwa mtumdu kwanji kumeneku.Basi akaphedwa si malamulo akutero kumeneko aliyese amakolora zomwe wafesa akulu Amati ukafuna kufa mumayamba ndi mu khutu kugotha tawonani Iwo amachenjezedwa koma osava nde bansi kwawo kwatha.

  • @Vava-up5dc
    @Vava-up5dc 18 годин тому +3

    Ana achani aaaah aphedwe Mesa amapha anzawo

  • @PatrickChalimba
    @PatrickChalimba День тому +3

    Nice aphedwe kumene

  • @ShahidaMada-zv9no
    @ShahidaMada-zv9no День тому +2

    Mon ndine jack❤❤q

  • @LukeMapukusa
    @LukeMapukusa День тому +5

    Zingawenga ziphedwe bas ana asatana

  • @JoshuaNgosi
    @JoshuaNgosi 17 годин тому +1

    Jack, u are the one. And boma la congo landisangalasa pachingamulo chawo.

  • @Hendersonspoon
    @Hendersonspoon 10 годин тому

    I have understood the story create from you and government have done a great job ordinary people must have their rights brave DRC minister

  • @bridgetmubisa3420
    @bridgetmubisa3420 День тому

    Iyiyi timweredi eee... thanks jack

  • @MonicaThocco
    @MonicaThocco 7 годин тому

    Ok ndakumvani Mama ,😢 ana kulibe moyo uno ,ndi khadwe pakati pa anthu ,akudziwa ndi chauta ndi momwe kuthere

  • @DigleDafter
    @DigleDafter День тому

    Nice aphedwe kumene dziko kumakhala akuopa tiana ngati itii kwasala ku mpanje azikwanje tizaphaso tikasitha boma 😂😂

  • @ENE_MANUJA
    @ENE_MANUJA 2 години тому

    Nice

  • @MaggieKachepaNkhoma
    @MaggieKachepaNkhoma 4 години тому

    Now I understand the story,,,,

  • @blessmax5148
    @blessmax5148 День тому +1

    Iweyo ndiye walakhula zoveka bwino chifukwa me konda you enawa mene akuyifotokozera eeeeee akutisokoneza mutu iweyo ndi number 1

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie День тому

    Bravo congo government mwachita bwino muonetsetse kuti onse 700 chakutiowo aphedwe ndithu ndithu ndagwira miyendo yanu aboma

  • @PatrickChalimba
    @PatrickChalimba День тому +1

    Ku Malawiso ziyambe akubawa aziphwdwa zanyanya

  • @CharityKaponda
    @CharityKaponda День тому +1

    😢😢😢😢😢 aphedweee amenewo azawo omwe ankaphedwawo samafuna moyo 😢😢😢

    • @MacloudSalima
      @MacloudSalima День тому

      Ndipo zobhowa aphedwe kumene eeee anthu oipa

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole День тому +1

    Ana oyipa ngati anyamata azikwanje mu Lilongwe achita bwino asamvetse chisoni anzawo adawapha .

  • @BenBanda-z4d
    @BenBanda-z4d День тому +5

    Nkhani iyi ndimaidikila thanks Sister Jaki

    • @denndavie6041
      @denndavie6041 День тому

      I congratulate the judgment. Dear GOD? Thank YOU.

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete День тому +1

    Awachita bwino ukupha naye aphedwe basi

  • @GeorgeMatewere
    @GeorgeMatewere День тому +1

    Aphedwe onsewo then ena atengerepo phunzilo sazakhalanso Ndi maganizo oyipa ofuna kuyambisanso zauchifwambazo

  • @DalitsoAlufeyo
    @DalitsoAlufeyo 10 годин тому

    Basi tikakumana ku mwamba singavere chisoni amenewa

  • @ROBERTMasonga
    @ROBERTMasonga 13 годин тому

    Jack you are the 1️⃣ but anayenela kuwapha asogoleriwo anawawo ndikuwa siya ku ndende chifukwa choti achinyamatawo amapangila chimbulimbuli ndi tindalama tomwe. Amapasidwato

  • @AfracaTyre.s
    @AfracaTyre.s 9 годин тому

    Atsikana kuthilidwa ma battery 😂😂

  • @EllenPhiri-g7t
    @EllenPhiri-g7t День тому

    More love, tamva nawo

  • @Justin_Nano
    @Justin_Nano День тому

    Nde kwanthu 😂😂😂🇨🇩👋

  • @janeangella2774
    @janeangella2774 День тому +1

    Umatha Jakilini wangaaaaa

  • @PatriciaBibu-nk1fu
    @PatriciaBibu-nk1fu День тому

    Ndipo nkhani iyiyi ndimayifuna inuyo ndi dolo mamie 🤗

  • @RosinaWakuthera
    @RosinaWakuthera День тому +1

    Manager wa tv station amulakwira mmm 😢 munthu oti wangokwatira kumene kuphedwa choncho zoona?

  • @hamdanmasuku
    @hamdanmasuku День тому +2

    Uku kukufunika Ibrahim Traore

  • @RuthMpambalika
    @RuthMpambalika 9 годин тому

    How there goverment asured this young men are the one who bulutaring the oldinary people

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k День тому

    Well done...panopo otsalawo adziopa

  • @SeleSelebati
    @SeleSelebati 8 годин тому

    Best explanation 😢

  • @HectorMkiss-s8e
    @HectorMkiss-s8e 10 годин тому

    Akanawaphera pagulu pompo
    Iyaa

  • @amosbenson6383
    @amosbenson6383 День тому +1

    Awachita bho, awaphe onse

  • @PeterMakaika
    @PeterMakaika День тому +1

    Awaphe basi...iwo amapha azawo...mulingo omwe ukumuyesela nzako iweso uzayesedwa ndi omwewo

  • @AmoslazaroManuel-kb4uh
    @AmoslazaroManuel-kb4uh День тому

    Moni ndine jaki khaniyi Apa Nde ndavetsetsa😊😊😊

  • @MauryFombe
    @MauryFombe День тому

    Ndipo no mercy aphedwe amenewo....a amnesty wo asalowelere sakupanga zikuti justice iwoneke bwanj pankhani zankhondo zo

  • @IsaacMwale-hu9kg
    @IsaacMwale-hu9kg 23 години тому

    Ndye ena akuti afunika kukhululuka ayi Apte ana asatana achita bwino that's stupid thanks Jack for information

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs День тому

    Inuyo ulemu wanu mumatifikisa koti sidafikeko❤

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 9 годин тому

    Nkhaniyi ndaivesa kwambiri sopano

  • @shabbanpaul
    @shabbanpaul 16 годин тому

    Jack we love you here in Australia

  • @FutureChiyo-mt4yy
    @FutureChiyo-mt4yy День тому

    Proudly Malawian 🇲🇼

  • @Nkhani-nkhani
    @Nkhani-nkhani 13 годин тому

    Olo nkhopezo kuchita kuopsa eee

  • @emmanuelkapelula6142
    @emmanuelkapelula6142 День тому

    Mmmh mbola tu km shaaa

  • @MissTasnim-n1t
    @MissTasnim-n1t 18 годин тому

    Thanks aunt jaki we didn't know the story we just so the story in tik Tok the did not explain the just post 🙏🙏

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt День тому +1

    Byee byeee

  • @ZahirMatiya
    @ZahirMatiya День тому

    Kodi Jaki ndi ndani? And amakhala kutiko ? Let us know then will start to follow

  • @AishaAbasi-o6u
    @AishaAbasi-o6u День тому

    Thanks Jack apa nde ndavetsetsa chomwe chikuchitika

  • @ApatsaAnderson
    @ApatsaAnderson День тому

    Good job 🔥🔥🔥

  • @wellingtongodwillkapande
    @wellingtongodwillkapande День тому

    Point of correction. DRC isn't in direct war with Rwanda. DRC is fighting against rebel groups, one of which is M23 from Rwanda. Of course, DRC government claims M23 is being supported by Rwanda

  • @Shadreck-n7z
    @Shadreck-n7z 9 годин тому

    Izizi ndizabho coz anyamatawa anyanya asala akwasundwe oyenda ndi zikwanje

  • @blessingsmimu5236
    @blessingsmimu5236 9 годин тому

    Asala achikwanje aku lilongwe plus ndi otuma ujq 1 day is 1 day

  • @noelcheonga8247
    @noelcheonga8247 14 годин тому

    Awachita bwino ndipo aphedwe ndithu zigawenga zosowetsa mtendere

  • @AnniePwere
    @AnniePwere День тому +1

    Anthu asamasowe mtendele dziko lawo lomwe zophedwazo ndilibe nazo vuto ena atengelepo phuzilo

  • @ThokozaniSayendaa
    @ThokozaniSayendaa День тому +1

    Aphedwe sakulakwaaaa

  • @dorafaartsigns6188
    @dorafaartsigns6188 День тому +1

    Ngati amaphadi nawonso aphedwe basi

  • @GeorgeNkhata-x1o
    @GeorgeNkhata-x1o День тому

    Zikomo jack chiyamkhulo sizimamveka apopo watisegula mmaso

  • @LandiraniFidesi
    @LandiraniFidesi День тому +1

    Awaphe ka 10niso pat

  • @FINNAHSMART
    @FINNAHSMART День тому

    Ya khani iyi simadikilira thanks sister ❤❤

  • @NomsaLali
    @NomsaLali День тому

    Oooh that means the predent siolakwa et aaa tavesano

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie День тому

    Kunonso ku malawi kuli anthu azikwanje akusowetsa ntendere a peter muthalika mujalowa mu boma pa 17 September anthu amenewa azaphedwe

  • @KasusuDamiano
    @KasusuDamiano День тому

    Very interesting story but sad

  • @IbrahimChiputula
    @IbrahimChiputula День тому +1

    Zibwana akafe mesa amampha azawo

  • @DhakaJr-pm5kn
    @DhakaJr-pm5kn 17 годин тому

    Engonga again

  • @TemwananiHojane
    @TemwananiHojane День тому

    Jaki you are star ❤🌟

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 23 години тому

    Ana angono angono 😢😢

  • @manuelnamapita6281
    @manuelnamapita6281 День тому

    Mphoto ya uchimo ndi infa,basi palibe kuchitila mwina,mbava zikafika pakhomo zilibe ulemu

  • @GeoffreyMgundo-s5k
    @GeoffreyMgundo-s5k День тому +1

    Aphe onse bas

  • @ZahirMatiya
    @ZahirMatiya День тому +1

    Akaphedwe basi

  • @14102010kia
    @14102010kia День тому

    We visit Congo now

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d День тому +1

    Ompa zake ampedwe

  • @LandiraniFidesi
    @LandiraniFidesi День тому +1

    Aphedwe bas 😢

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p День тому

    Nkhani nga ndiimeneyo achita bwino

  • @EvanceBonjesi-n2z
    @EvanceBonjesi-n2z День тому

    Good job ndazikonda

  • @JawardBenard
    @JawardBenard 17 годин тому

    a Boma la Congo apanga chiganizo cha bwino

  • @GraceGwazaJere-ox2tz
    @GraceGwazaJere-ox2tz 19 годин тому

    Nkhani inayo muyikambeso

  • @InnocentKavalo
    @InnocentKavalo 14 годин тому

    Iweyo jack umakwana maina ajack ndi anthu anzelu

  • @tesfachinomba4901
    @tesfachinomba4901 День тому

    Zikomo jaki❤❤❤

  • @HappinessMainala
    @HappinessMainala День тому

    Now u have clear my doubt but we are also waiting to hear about Marcel malanga ,is he dead or people are talking

  • @AlexanderMphalasa635
    @AlexanderMphalasa635 День тому

    Aphedwe Aaaaaaa anthu osamva

  • @HashirJames-d5n
    @HashirJames-d5n 11 годин тому

    Asawanyengelele awaphe bas amazimba udolo kumapha azizao

  • @chawanangwamkandawire5850
    @chawanangwamkandawire5850 День тому

    Musawone kuchepa misinkhuko, umunthu umukhala kuti unachoka anthu oterewa, zimakhala zinyama zongolabada za moyo wawo okha, moyo wa munthu wina kwa iwo umakhakhala ngati wa mphevu.
    Kubwezeretsa umunthu mu anthu oterewa imakhala process yolema ndithu which requires very tight scheduled psychological reformation programs nde dziko la nkhondo zosatha ndakayika if they have such resources to waste.

  • @christinamkota2919
    @christinamkota2919 13 годин тому

    Palibe zokhululukidwa amayenera phedwe kumene

  • @GraceGwazaJere-ox2tz
    @GraceGwazaJere-ox2tz 19 годин тому

    Thanks Jaki ❤

  • @dajmussa2331
    @dajmussa2331 День тому +1

    Awachita bwino akee

  • @AngelaChavula
    @AngelaChavula День тому

    Zikomo taziwa nawo😊

  • @RoseJere-t9x
    @RoseJere-t9x 5 годин тому

    Achitabwino kuwampha zigawenga

  • @AmakaBAbie
    @AmakaBAbie День тому

    Apachikidwe anyongedwe hiyaaaa kusiya amzawo pa umasiye basi

  • @northbusymw
    @northbusymw День тому

    Mutiuzenso za Marcel Malanga with his friends, zikuti bwanji Kodi

  • @RaheemBondwe
    @RaheemBondwe День тому

    Moni ndine jaki 🌹

  • @AlinafeKasinja-g6q
    @AlinafeKasinja-g6q День тому

    Zikomo jaki apapa ndavetsetsa nane nali madzi ophatikiza nkhani yakulunao ndiya Marcel malanga

  • @FrancisMwafulirwa
    @FrancisMwafulirwa День тому +1

    Moni ndine Jack

  • @WezzMeaah-ns7xc
    @WezzMeaah-ns7xc День тому

    Ndilupanga lako lizakuphe akuyenera kuphedwa kumene amenewo 😏😏😏😏

  • @HalietyKasawalawapha
    @HalietyKasawalawapha День тому

    Ine ndipo simayivetsetsa cz amayankhula chiyankhuro chakwawo apa ndavetsetsa Jack mmmm km mayiko azathuwa mmmm eshiiii so sad zigawenga chomcho za live live eshiiii 🙌

  • @nyakamayuni5074
    @nyakamayuni5074 День тому

    Ndamvesesano jaki thanks