Mr. Banda job well done...Ministers are public servants, where ever they serve, they shall be held to account. We the people have the right to Answers... personal attacks and defensiveness will not solve our problems.
A daus mukuoneka ngati ndinu ochenjera pomanamiza amalawi ndi A P Mutharika wakoyo nonse machende anu ine president wangatu ndi chilima ndipo nthawi zonse ndimavoteta chipani chowina
Dausi uzipusitsa ana adad wanva? Out of ten thousand houses u promised zoona kungomanga 200 zokha bas!!! Ndine wa police vote yanga mwailuza futsek dpp
Anyone watching it in 2024😂😂😂😂
This interview is the greatest comedy you will ever watch! 😂 from Zambia 🇿🇲
Mr. Banda job well done...Ministers are public servants, where ever they serve, they shall be held to account. We the people have the right to Answers... personal attacks and defensiveness will not solve our problems.
BRIAN BANDA katundu omanga ndimawaya tikanakhala nao otere 50 Malawi thinking mentality tilipatali👏🏼👏🏼👏🏼👏🏼👏🏼👏🏼👏🏼👏🏼👏🏼👏🏼🇲🇼 kuwavundula akavuwevuwe odedeluka ngatii awaaaa DAAUUSSII
Brian ndi more from times keep moving Mr. Banda good work
This is such a chaotic yet funny interview looooool
Brian Banda kumalawi kulibeso ntolankhani ngati inu timakupasani ulemu ndipo mumaimilira ntolankhani onse ku malawi, mr Dausi kufika ponena kuti mukafuna kumapanga interview amakhala nanu nkhawa ndipakedi chifukwa simuopa kufunsa zomwe zikulakwika keep up mr Banda
Best interview in Malawian history
This interview made my day 😁😁😁😁😁😁 Greetings from your neighbor MOZAMBIQUE 🙂
What is the minister saying in 31;12 and 32:00
That makes the interviewer laugh hysterically
Brian Banda GOD bless you
Amen
Who is watching this in 2022????
Best interview 💥
Wish you could interview now when he's at home 🙈
May you feature him back as a follow up to this program
Very wise when he is respond
Inu si judge iyai, ndi judge? Kkkkk enjoying it from Zambia.
following
koma braun banda i love you kumafuso anu koposa.mumaphaphalutsa
Brian Banda, tsiku lina udzatikokere Atupele Muluzi. Nudzamuphaphalitsa ndi mafunso.. za ubebe ife timadana nazo.
Wawww good news
Utm ndibomaaaaaaaaaa 2019 kuti buuuuuuuuuuuuu
Brian adangofika pozolowerana ndi mdalayu ndi majoker basi
P
BRIAN WOYEEEE!!!!
Classic 💯
Shaa koma mr Dausi ndionama kwambiri. Akusewelesa amey ndi police
These guys eeeh amatengetsana
Dausi ndi guru la China Ntaba maboza okhaokha
Daus....It's hard to hate him. He is very funny.
"Honorable minister, you can do better than this " 🤣😂
Kkkkkk Brian ndi Dausi muzibwerabwera
17:40 "Wabwela bwanji, Wadzatani, wathawa kwanu chifukwa chani, kuno nkwambuyako"😂
I'm loving it ha ha ha ha ha ha
18:30 barbershop?
Atambwali akumana
Kaa mcp I'm apha anthu nkozi wake ndi Dausi
Dausi palibenso shaa
Usaopse I we dausi asa
Dausi Ali ndi certificate ya Standard 8
Kodi adausi mudzapuma liti kubela amalawi ?ngati peter ali oyipa mchifukwa cha iwe galuwe
Makani adausi
Brian ndiye mdalayo wamukutumulamo kapena kumphaphalitsa ndi mafunso naye waziwa ndiye palibe mayanko womwe apereka Dautsi wonveka bwino😂😂😂
...nonsenu mmakwana...
Uyu ndiye pumbwa weni-weni.... We are tired of you old leaders
Fyanta! LOL
this is political appeasement ....dausi is very dangerous
Akatolica akhumudwitsa Yehova samalani
Bulaan banda ndi muthu wolimba nazo upitilile ewee
Ukudzikola Dausi kusonyeza kuti ukunama
mother mery
Mfuso? Mwamanga manyumba angati mr.dausi
Kodi m'menemo ndi my office mwa nduna zisekozo azipake vanish komadi a pumbwawa angodya ndalama
A daus mukuoneka ngati ndinu ochenjera pomanamiza amalawi ndi A P Mutharika wakoyo nonse machende anu ine president wangatu ndi chilima ndipo nthawi zonse ndimavoteta chipani chowina
Dausi udzanya unamenyedwa pang'ono uonatu khala phee
Hahaaaaaa koma awa azathawa Dausi olwez amaganiza kuti azakhala amuyaya but never ever
Za anthu obwerazo zofunika kuziona bwinobwino chonde ationongera dziko
Kkkkkk Brian basi asiyeni anduna za wavuta aDPP
Dzoona zake ngwirani obwera awoneni bwino kuti akudzatani mdziko.
Iwenso Brian usaope kuti akumanga uthakunkhala kundendeko kwa miyezi 6 yokha basi koz chilima akubwera adzakutulutsa w ar following on ur back bra
Kikkkkkk hahahahahahahahaa Mr Dausi! 20, 20, 2013 ,2011920 hahahahaha!
Shame on you Dausi
Very funny
😂🤣😂 Brian ndi fire kwambiri amamubalalitsa munthu ndi mafunso owoneka a simple
Hahaha
K Mwale muyakhule naye...otherwise Mr Minister you will achieve nothing
Comedy!!!!
if times group will lose this guy am telling you, people will suffer for sure 😂😂😂🤣
Koma ma guys awawa amaipatsa moto 😂😂😂😂😂😂😂
Bodza Dausi
kodi madala Adausi atakhala mphunzitsi ana sangakhonze chizungu chawo chopotoka kkkkkkkkkk Mr Dausi zabwino zonse
ADausi mudziyankha funso limene akufunsani,bwanji kumazemba zemba mmmmmm
Kkkkkkkkkkk Dausi ndi wanthabwala ndi Brian
This Dausi he take Malawians like stupid, why political level ya ku Malawi nthawi zoonse mumafuna mudzinama?
Brian utsazafe uzangosowa
🤣🙌ichichi aah
Kkkkkkkkk koma Daus uuuuuuuuuuuu
Dausi uzipusitsa ana adad wanva? Out of ten thousand houses u promised zoona kungomanga 200 zokha bas!!! Ndine wa police vote yanga mwailuza futsek dpp
kkkkkkkkkkkkkk awuze awuze opusa amenewo
Daus ndi moree ndimankonda
Nkuluyi palibenso
The minister got the job because of his arrogance 😂😂😂
Iyi iyi inali mbambande😂😂😂
Chakwera will win the elections
Stop talk nonsense plz mn
You were right
Ooií
Promises and lies DPP government
Tikanakhala ndi a Brian 5 ku Malawi, zikanakhala bwino.
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Really? Pitala samayankha?
Dausi sikape 😂
Taona kuti ansankha mbuli, Malawi singapite patsogolo tikufuna anthu ophunzira azigwira ntchito
Kkkkkkk koma dausi palibe chazelu apa chomwe akuyankhula mbava yeniyeni iyi.
zoonadi iyiyi ndi mbava
Kkkkkkk
Mdala iwe dausi pena pake umasangalasa malakhulidwe koma problem ndi DPP
kkkkkkkkkkk
kunena zoona adausi mmmmm ndimunthu waziwa kuthawa mafunso kkkkkk koma mzamanyazi ingovomelezani kuti zakuvutani apatseni anzanu alamulilebasi.
Koma Dausi ....inu si mmagawana ndrama aja kusowa zochita nazo....nde uzitinamiza apa kuti kunali mavuto ambiri
Adausi mukuyankhuka bwino uladi mussa mumutengele Ku khoti chifukwa adapeleka zitupa mwachinyengo kwa mzika za mayiko ena
Democratic culture 😂😂😂😂🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌