Times Exclusive with Kondwani Nankhumwa - 14 January 2023

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 сер 2024
  • Times Exclusive with Kondwani Nankhumwa - 14 January 2023

КОМЕНТАРІ • 43

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Рік тому +5

    Not all countries inu a Nankhumwa... Just pa Kenya they don't have this.... Kumatsata zithu. But keep the good work up

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 Рік тому +5

    Zoona ndi awa omwe kufuna kukhala president wa dziko la malawi 🇲🇼 koma malawi ndi dziko lonvetsa chisoni kwambiri mbuzi bulutu wa munthu ngati uyu alamulile dziko la malawi, upresident kumpatsa uyu ndiye palibwino kuvotela chule frog 🐸 kuti akhale president wa dziko la malawi 🇲🇼

  • @giftbanda4518
    @giftbanda4518 Рік тому +1

    He answered all questions very well without ducking. Well done sir

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 Рік тому +2

    Uyu sangatsogolere dziko uyu zeru alibe. Ku kenya, Zambia South Africa anthu akudandaula ndikukwera kwazinthu

  • @cassimmeleka40
    @cassimmeleka40 10 місяців тому +1

    Oky Nankhumwa kugona zedi asiye kudya ndalama za boma kamba chomwe Ali msogoleri wa opposition sichikuziwika, Ndipo sakuziwa komwe akupita iyeyu mulibe usogoleri

  • @patumakassim2974
    @patumakassim2974 Рік тому +3

    Awa ndiye opanda nfundo kumangogona ku parliament basi

  • @Kamwachale
    @Kamwachale Рік тому +1

    My views is that leader of opposition is elected through election. The party that has become second on presidential election automatically he or she becomes leader of opposition. In case where that person is not a member of parliament, there must be a provision in a law (if it is not there) to allow that the one who came second on presidential election to choose a member oof the party who can be a leader of opposition on his behalf not that the leader of opposition be elected in parliament.

  • @petermkandawire1994
    @petermkandawire1994 Рік тому +2

    Nankhumwa ali bho

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Рік тому

    Greetings from London UK 🇬🇧.

  • @evancebetha1656
    @evancebetha1656 Рік тому +1

    Uyu ndiye mayazi ku convention ndi kabambe bas what we need is economics ndye kabambe osati nankhumwa adxagulitsa chipani ku utm uyu

  • @stevemataka
    @stevemataka Рік тому

    Let's wait & see

  • @marvinmulinga1015
    @marvinmulinga1015 10 місяців тому

    Impressive

  • @justainnchambalinja4328
    @justainnchambalinja4328 Рік тому

    Powerful words

  • @harryulaya9791
    @harryulaya9791 Рік тому

    😊😊

  • @thiagosbotha2015
    @thiagosbotha2015 Рік тому +4

    Mukuti peter muthalika mzimu wake uuse mu mtendereso???? Kkkkk

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Рік тому

    Tulo ta opostion leader
    U cant lead my friend

  • @patumakassim2974
    @patumakassim2974 Рік тому +2

    Uyu amadya bansi kumbali uyu palibe anganame

  • @jasonnamainja7403
    @jasonnamainja7403 Рік тому +1

    Ati a Brian ali ndi akazi awiri 😂😂😂🙌

  • @angelicajoseph3080
    @angelicajoseph3080 Рік тому +1

    Wowwwwwh! Mwana wamulomwe kuyankhula!

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e 6 місяців тому

    Nakhumwa ndi wamcp usatinamidze iweyo

  • @Skasompha2016
    @Skasompha2016 Рік тому

    Nde Mukuti you can make a good Presiden?

  • @emmanuellemson705
    @emmanuellemson705 Рік тому

    Ndakonda kondwa

  • @carinazecamariozecamario1662
    @carinazecamariozecamario1662 Рік тому +1

    Mayankhulidwe ake amenewo mungamake inu kkkkkkkk

  • @fedson2050
    @fedson2050 Рік тому +1

    Mulomwe uyu aaaaaa MTHERA KUWIRI m'mutu mulibe NZERU Bhobho

  • @zaidimussa
    @zaidimussa 7 місяців тому

    Athu ambili akasapota team player akasiya kumenya mpila athu amasiya kusapota popanda apm ife tibeledwa

  • @cassimmeleka40
    @cassimmeleka40 10 місяців тому

    Nankhumwa yu sakuziona yekha kut ndi osakwanira?

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Рік тому

    Simunga wineinuyo anankhumwa

  • @kennethmakweya3561
    @kennethmakweya3561 Рік тому +2

    Kabambe will carry the day no matter how tough it's going to be

  • @zaidimussa
    @zaidimussa 7 місяців тому

    Kodi ufuna kuseweletsa amalawi poti enaakamalila ena amakodwa kodi malawi wake uti amakunamiza iweyo

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Рік тому

    This means members of Parliament are enjoying paid leave for free. Another way of wasting government money. Sorry waya

  • @nkhwalamkwala6483
    @nkhwalamkwala6483 Рік тому

    Chilima ndi nankhumwa antha kukoza ziko

  • @lukainnocent5380
    @lukainnocent5380 Рік тому

    Awa ndbuluzi weniweni akuti kuzakhala president eish amalawi mavuto okhaokha kkkkkk

  • @mzeewandembonyirongo2972
    @mzeewandembonyirongo2972 Рік тому

    Kkkkk a UTM ndi 4 kkkkkk koma a Leader of Opposition kkkk u don't even know kuti ma MPs all bwanji...

  • @mikemulobwa9814
    @mikemulobwa9814 Рік тому

    1a13g

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Рік тому +1

    Koma FDH bank sinagulitsidwe mwa ndondomeko, ikuyenera kulandidwa. Panalowa chinyengo chochuluka pamenepa.

  • @kelvinkapachika6975
    @kelvinkapachika6975 Рік тому

    Uyu watikwana uyu🤣🤣🤣

    • @jomochirwa
      @jomochirwa Рік тому

      Esh akuwopa adad lol,adad ndi akamunatu ,nalikukutu uja kkk

    • @jomochirwa
      @jomochirwa Рік тому

      Brian mavuto ali konse konse kuno ku john katundu wakwela mtengo zeedi ,anthu sakulembedwa ntchito,magetsi 12 hours sakuyaka,panoso magetsi awonjezela mtengo ndi 13.5 percent en ramaphosa is under so much presure komano beside that kumalawi ndizovuta kuti tivomeleze kamba kodi akuluakulu aboma akubaso kwambili.

    • @kelvinkapachika6975
      @kelvinkapachika6975 Рік тому +1

      @@jomochirwa komanso so called adad wo would have paved the way to fresh minds ah ah ah. His age is supposed to be at resting 🤣🤣🤣