Video iyi ndaipeleka kwainuyo Amalawi Kut muiwone! Athu nonse a MCP ndinu zinsilu makamaka IWE chakw

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 11 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 68

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 7 днів тому +1

    ❤❤❤❤

  • @ReubenMwanza-w5s
    @ReubenMwanza-w5s 8 днів тому +1

    Every Government hss it's so was D.PP. Not because M C. P is in controlling the Affairs of Government zokamba mbweeee. Let mcp do its part yours will come..U also have your own shortfalls that is democracy.

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 10 днів тому +3

    Fertilizer akamupezera Kuti ana a Njoka Ndalama anazitafuna . Chomwe amadziwa kugawa ndi ZIKWANJE .
    Kuzolowera Mkhamza, Tsankho ndi Kupha

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 10 днів тому +3

    Ndipo afika po chikangawa 🙌🙌

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 10 днів тому +3

    Pantumbopawo amcp mbava owonangati dzikoli layambila paiwowa

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 10 днів тому +1

    Exactly munthu umazilemekeza wekha ndiye chikangawa ali ngati manganya amazipepusa okha chifukwa alibe nzeru

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 10 днів тому +2

    Zoonad munya nane nkhumba izi zichoke bas

  • @Achina-warrior_Mw
    @Achina-warrior_Mw 10 днів тому +2

    Chakweradi ndikape

  • @MonjeziShaban
    @MonjeziShaban 10 днів тому +2

    Munthu Uyu akutenga dzikoli ngati lakunyumba kwao

  • @MartinKapito
    @MartinKapito 10 днів тому +1

    Chakwera ndi wadzibwana akuona Ngati amalawi ndife opepera kt tidzinglo ombera manja pasala pangono chikangawa udzayakha l

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 10 днів тому +1

    Munyanane awuze makape a mcp, dzisilu zimenezi awuze big apapa ukutilankhulira ndizomwe tikunena panopazi kuti akuitenga ngati ya mawo. Koma manganya kobili wagulira iye 40teleza si za mcp ndi zake zija amafuna kulipila ku kovesion zija.

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 10 днів тому +2

    Ya Allah dalisani dziko lathu dalisani mitundi yonse tonse ndfe akapolo anu ndpo Allah ndnu nokha oyenera kukupembedzani AMEEN🤲🤲❤❤

    • @NyasaPulseofMalawi-g3m
      @NyasaPulseofMalawi-g3m  10 днів тому

      @@ShamimuBisani Ameen allah bless you my brother

    • @noahkalima5294
      @noahkalima5294 9 днів тому

      Allah fano lakufa lingadalise ndani,,kulemekeza chibwana Inu eti,, Allah fano ndmuhamad. Chigawenga,,

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 9 днів тому

      @noahkalima5294 may .Allah almighty bless u and ur famiry

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 9 днів тому

      @@noahkalima5294 may good Lord almighty bless u and protect u and ur famiry Mulungu modzi akudalisen lero mpk siku lachiweruzo

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 9 днів тому

      @@noahkalima5294 zikom poyankha mene mwayankhiramo wakulu kumwamba kulemekezek ininso Mulungu akusogoleren zikom kwambri siku lopambana zikom🤲🤲

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 10 днів тому +1

    CHAKWERA SPERCH YAKO KUPPSYA NGATI NJOKA MMUNDA WA EDEN

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 10 днів тому +1

    Alomwe ndamene akulowa boma mufune musafune 😂😂😂😂

  • @LameckGamah
    @LameckGamah 10 днів тому +1

    Ati kumaophyeza Aaaa, zopusa bas ☹️

  • @BrightonChidzalo
    @BrightonChidzalo 2 дні тому +1

    Auzeni

  • @JafaliTenda
    @JafaliTenda 10 днів тому +1

    😂😂❤❤ munya nane

  • @EnochSamuel-o5e
    @EnochSamuel-o5e 9 днів тому +1

    Chakwera, bola akanangokhala osayankhulaso. Palibe icho chingapindulire ife koma iye amangofuna kutisamzika kuti akutiberaso ndalama zopasidwa zija kupitira ku Dubai

  • @JamesYusufu-m4r
    @JamesYusufu-m4r 10 днів тому +1

    tinasiya. zopusazo. zimenezo azivela. anachikwanje kwaoko simavela zopusazo

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 9 днів тому +1

    Agalu kkkkkkk, abusa asanduka galu, koma Mulungu ndi Mulungu, amaziwa ndani kuti Chakwela azasanduka galu atakhala M'busa zaka zambiri.

  • @MavutoFodya-p1u
    @MavutoFodya-p1u 10 днів тому +1

    Munya nane fire fire 🔥🔥🔥🔥 auze amve akasongowa

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 9 днів тому +1

    Ali mitu ngati zigumu pamenepo kkkk

  • @GeorgePatels-go7wj
    @GeorgePatels-go7wj 9 днів тому

    Kunali anthu omwe amadzitenga ovuta mu dziko lapansi Koma onsewo anapita ndipo taona kwati ziii,

  • @Amina-gg5gr
    @Amina-gg5gr 9 днів тому +1

    Chakwera ndi okupha

  • @HusseinMofatt
    @HusseinMofatt 9 днів тому +1

    Unasowatu aise ndimakunyadila aise

    • @NyasaPulseofMalawi-g3m
      @NyasaPulseofMalawi-g3m  9 днів тому

      @@HusseinMofatt ndilipo KKK ndipo simukunama ndunasiwadi Koma pano ndipamene ndizipezekera auzeninsoni azibalewo Kuti tili pano tipangeni subscribe

  • @AnnnesBango
    @AnnnesBango 10 днів тому +1

    Wakulu ndi wakulu

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 10 днів тому +1

    Mr crocodile not chakwera but Mr crocodile kapena Mr chikangawa

  • @courageouslondo1986
    @courageouslondo1986 10 днів тому +1

    Auzeni mana

  • @PatiHasan-u1l
    @PatiHasan-u1l 7 днів тому

    DPP woyeeeee

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi 10 днів тому +1

    Kodi manga akupangila kampeni ndani kkkkkkk Koma misala inayi

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 10 днів тому +1

    That's all?

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 10 днів тому

    Aaaaaaa DJ Munyanane kodi mulipo ayi musamasowe

    • @NyasaPulseofMalawi-g3m
      @NyasaPulseofMalawi-g3m  10 днів тому

      @@OssmanAbubaker-v7t ndilipo tiope inu basi pakeathu ndiponpano tipangeni subscribe

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 9 днів тому +1

    Munyanane yemweyo 😂😂😂 kma ndasekamo mu audio yi😂😂😂

  • @Costance-nf7ue
    @Costance-nf7ue 10 днів тому +1

    Chakwera akutenga. dzikoli ngati labambo ake mbuzi ya president ngati imeneyi kkkkkkk

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 10 днів тому

    Kkkkkkkk mafuta akagula yekha zafikapo ndithu Malawi okomera tonse ayi zikomo zibani ndalamazo basi

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 10 днів тому +1

    Alomwe muli pachintchito simuzabwerelanso boma munali ndi mwayi pangono chifukwa munawabera a udf boma koma pano simuzabwereranso kaya mupange kampeni mwantundu wanji kwanu kunatha

    • @NyasaPulseofMalawi-g3m
      @NyasaPulseofMalawi-g3m  10 днів тому

      @@GeshoMwakitwile kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk angoti kakasi kusowa chochita

    • @EDGARMPIKAMEZO
      @EDGARMPIKAMEZO 10 днів тому +1

      Zisapite polozana mitundu. Ine ndine mchewa koma sindimasapota abulutu Ali m'bomamu a MCP. I support Dr Dalitso Kabambe Mlomwe ndi UTM 🔥🔥🔥. Afisi awa ndiye afika ponunkha 🤮🤮

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 10 днів тому

      Mulungu akudalisen maganiz anu tonse ndfe amodzi ndne muyao koma Malawi aliyense ndimamulemkeza ​@@EDGARMPIKAMEZO

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 10 днів тому

      Moopa Mulungu ndne wachiyawo koma ndikaganiza zasiku lomaliza siku laimfa yanga aaaaaa ndimalemekeza mtundu ulionse Mulungu atidalise tonse olamula ndi osusa omwe

    • @courageouslondo1986
      @courageouslondo1986 10 днів тому +1

      Kape unaona president akagula mafuta kkk

  • @ODESHOBO
    @ODESHOBO 9 днів тому +1

    Kkkkkkkkkkkkkkkk bas koma chakwera akanakhala bola mbudzi ndikanayigulisa

    • @NyasaPulseofMalawi-g3m
      @NyasaPulseofMalawi-g3m  9 днів тому

      @@ODESHOBO kkkkkk tikanagula ndikuipha

    • @ODESHOBO
      @ODESHOBO 9 днів тому +1

      @@NyasaPulseofMalawi-g3m ndipo ogulawo akaithile laja wabwino tomato otsaola koma akhale wakupsya bwino

  • @NyasaPulseofMalawi-g3m
    @NyasaPulseofMalawi-g3m  9 днів тому +2

    ua-cam.com/video/wsoR7qsfP9I/v-deo.htmlsi=cS9dIdk6KWBheXdS

  • @ChisomoNthembanji
    @ChisomoNthembanji 10 днів тому

    😅 respectfully 2

    • @ChisomoNthembanji
      @ChisomoNthembanji 10 днів тому

      Dxko akuona ngat lamake cakwelayo. Akupanga zasete