He's real UTM....sakulimbana ndikuzinamiza kumagula nsalu za DPP or za UTM nkumaveka zigoba...iyeyu ndi mfundo zake zokweza Malawi 🇲🇼 typically SKC thinking....akuchita kuonetsa kuti SKC amamukonda ngakhale anali ku Blue camp! Kusiyana ndi enawa ochita kudzidzimuka kunamizila, kuzinamiza, komaso kuwanamuza abwana 😂😂😂😮😮
A😂😂😂 ongofuna kugwiritsidwa ntchito ndi chikangawa awa ndale zaku Malawi zomvetsa chisonitu zolankhula ndijungoti mpulumutsi uja wafika Soasidwe mpata 7 out of 100% Kufuna kusokonedza mitu a Malawi basi
Well done Kathy appreciate the questions in both interviews. Love the suit too. Keep it up. You inspire our young girls.
I like the way how Cathy is reporting
Genius of economy and presidential tactics giant.
Ndi UTM yokha yimakhala ndi manifesto yothandizira Malawi uyu. UTM more fire
Aunt Cathy u are a gud reporter, keep on pushing cc
The guy is feet to carry on chilimas legacy ❤ please! UTm delegates tiyeni tikamusankhe namandwa wazachuma ameneyu
My vote Kabambe ❤
That's very true maphunziro ndi ofunika ❤❤❤❤
Nfundo zake nzabwino close to chilima uyu akunela
Kabambe anali best friend wa Dr Chilima zikanavuta bwanji anali obwerabwera ku UTM Peter atangonena kuti aimaso anayamba kukambirana ndi Dr Chilima
I just love this guy Kabambe (he knows his staff)
Catherine maulidi ndiwe dhilu Banda akukusuladi
We are gone for age,, for Kabambe, you seem like SKC legacy
Kabambe he deserve to be a president of Malawi
He's real UTM....sakulimbana ndikuzinamiza kumagula nsalu za DPP or za UTM nkumaveka zigoba...iyeyu ndi mfundo zake zokweza Malawi 🇲🇼 typically SKC thinking....akuchita kuonetsa kuti SKC amamukonda ngakhale anali ku Blue camp! Kusiyana ndi enawa ochita kudzidzimuka kunamizila, kuzinamiza, komaso kuwanamuza abwana 😂😂😂😮😮
Fact man
Ndayamba kumukonda kabambe hvy
Big up Dr kabambe
My vote Kabambe=my president , G-d bless you
Paground lets hope is helpful , tchereni did the same
My vote Doctor Kabambe
I like the reporter how she do the lecturing
Khang.a my vote
UTM IS ONLY HOPE FOR MALAWI .
Komano choti mziwe palibe chipani chomwe chizawine nkulowa boma kumbali yosusa boma, kumbukilani zisankho zambuyomu analipo ena amazifila kuti aichotsa dpp chinachitika ndichani sanapambane zinatengela re election pomwe zipani 9 zinakhala pamodzi ndipo boma analigonjesa, ndiye strategy yopanga gwilizano that's the way to go komano zoti ine ndine surely mcp ikhoza kuzawinaso
Kambambe president next
Let's go for kasambe for next president
Malawi needs change now.
Work hard mayi upuzireko china chake kwa Brian Banda
Ilove the Guy Kabambe
Kabambe sangapange kalikonse wachepa, mufuseni bakili afotokoze mwemwe anamusankhira bingu
Let's forget about those old politians
He's looks like he can take Malawi
Kabambe ñdi ozitsata kwambiri ndipo akudziwa zomwe akunena komaso akuchita
Koman tamufusan kabambe ,at ndizoona kut mcp ikumunyengerera kt achoke ku utm?
Yeah akumunyengerera ndi dollar
Koma sangamuthe
A😂😂😂 ongofuna kugwiritsidwa ntchito ndi chikangawa awa ndale zaku Malawi zomvetsa chisonitu zolankhula ndijungoti mpulumutsi uja wafika
Soasidwe mpata 7 out of 100%
Kufuna kusokonedza mitu a Malawi basi
Asaiwaretu kuti iwowo Tati awina atha kukhala Pule ndiye asamayankhule ngati sadzakhala ndi anthu owazungulila .kuyendesa dziko lilingati limu lanjinga. Zomwe akabambe akumalankhulazo ndi history yawo imeneyo Koma kuyendesa dziko simasewera
Ndale zikufunika panopa ndi izizi za reform osati zakale zothana ndi atsamunda.
Awa amatha
❤
Aaaa akutitayitsa nthawi ameneyu
Akutaisa nthawi iweo
Nigalu kabambe palibe zazelu ukunena
Kodi kabambe yi akanakhala kuti chilima ali moyo akanalowa utm?
Kuli bwino asankhe mtsogleri yemwe wakhala mu utm ndi chilima awa akhale member
Anthu Asankhe anthu oti kuthekera koyendetsa kuyendesq dziko, economy etc chifukwa choti anali ku utm wirh chilima instead of kusankha munthu wothandiza dziko chifukwa sanali ku utmost chilima chilipo??
Aaaa akutitayitsa nthawi ameneyu