NTANYIWA PA LIMPOPO FM, MCP NDI MEC ANAKUMANA KUKAMBILANA NJIRA ZOBELA MA VOTE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 13

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 2 години тому

    Umakwana comrade keep it up

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x Годину тому

    Uwauze amcp kuti mulungu si James akuona ali ndi angelo omwe anawatuma kugwira ntchito keep on going

  • @FrankNdelemani
    @FrankNdelemani 2 години тому +1

    Mumatiyimilila bwana mtanyiwa mulungu azikudalitsani

  • @samsonbanda3470
    @samsonbanda3470 3 години тому

    Ntanyiwa more 🔥 we do follow u brother keep letting us know we tired of these people

  • @LacksonKasongo-x7o
    @LacksonKasongo-x7o 2 години тому

    Ana achepa tanyiwa ndi 1 chiyembekezo cha amalawi onse chili pa inu Mr kp it more

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 3 години тому

    Tiyamike mulungu wakumwamba potidziwitsa

  • @SalomeManda-c1i
    @SalomeManda-c1i 3 години тому

    Mumakwana a ntanyiwa kp it up

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 28 хвилин тому

    Mtanyiwa ndi dolo

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 3 години тому

    More fire comrade ntanyita mukuyimirila pano dziko rathu osati crocodile mbuzi yamuthu ndi team yake yonse

  • @BashiruPendapenda
    @BashiruPendapenda 2 години тому

    Wow

  • @KondwaniChauluma-v4x
    @KondwaniChauluma-v4x 2 години тому

    Mumaitha antanyiwa koma palibe chilungamo pa zokonzekera zisankho kodi sizingatheke kuti zisankho zikanike?

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 3 години тому

    Asaopa osatopa osafooka Allah alipo
    Mcp ikunama
    Mcp ikukakamira koma palibe chimene mukuchita muziko mwangosaukisa dziko basi mulibe nzeru kodi mukufuna kuti dziko mulimarize iwe crocodile ndi team yako yonse muzipita athu a nzelu zawo ayendese dziko warephera kuyendesa dziko iwe chakwera ukungoba kupha athu basi chimenecho ndi chimene umadziwa iwe ndi team yako yonse suku wina basi ufune usafune

  • @smartchamkuwa-l3g
    @smartchamkuwa-l3g 2 години тому

    Za