Mr twaibu my God continue to bless you ndine wa ccap koma ulalikiwanu umandiphuzisa chinachake keep it up mulungu oziwakuteteza nkhosazake akutetezeleni.
go deeper the man of God..zamveka ndinthu...ndipo inuyo mimatiwunza chilungamo..tikudziwa zobisika ..zakumidima chifukwa cha inuyo ..kulandra Ambuye kukhala ambuye ndi mpumutsi wanu ifenso tapulumitsidwa..tadziwa zambiri..tamphuzila zambiri
Ine ndinkakonda channel ya TB Joshua koma tsiku Lina ndinakhumudwa ndinalota TB Joshua akundiuza kuti sindizapeza mtendere mpaka kalekale ine mau omwe ndinamuyankha anali oti Mulungu wake uri basi ndinadzidzimuka pomwepo ndipo ndinayamba kuipidwa ndi Emmanuel TV
The world behind the scenes. Zinsinsi nzake za Yehova koma zovumbulukazo nza ana a anthu. Ayamikike Yehova Mulungu wamkulukulu ndipo apitirize kukutetezerani
Uyu simutumiki WA yehova,ngati akurimbana ndi TB Joshua,uyu atha ngati Garu,twaibuyu Alibe wa satanic,apeleka bwanchi wumboni wasatanic atatuluka... judgement belongs to God..we will see him if he will last anymore...
Masiku omaliza awa chowonadi chizakhala choipa. TB joshua was really man of God. Satana sangadziulure yekha. Inuyo mukufunika muphunzire mphamvu ya mzimu woyera mmene imachitira.
@@NicholasKwajama paliso kuumitsa mtima apa akulu...zinazi tamangomvelani ndkupanga kafukufuku..this guy sinamukhululupilepo since from beginning..he just use ma theories omwe tinkawamva tidakali ana...I think ndiwe mpesa thats why...lol
Wayandika olengayo. Nthawi yomvuta yakumapeto. Koma zosangalasa kuti Olenga dzuwa sanatimale mulozo wa mawu ake baibulo. Keep it up Twaibu.
I thank God for what you are reviewing to us through your vessel Mr Twaibu.May Mr Twaibu live long life.
Mr twaibu my God continue to bless you ndine wa ccap koma ulalikiwanu umandiphuzisa chinachake keep it up mulungu oziwakuteteza nkhosazake akutetezeleni.
🎉Ineso wa ccap koma zoona zotsakula maso kuona komwe tikupita Mulungu apitilize ukutetezerani
go deeper the man of God..zamveka ndinthu...ndipo inuyo mimatiwunza chilungamo..tikudziwa zobisika ..zakumidima chifukwa cha inuyo ..kulandra Ambuye kukhala ambuye ndi mpumutsi wanu ifenso tapulumitsidwa..tadziwa zambiri..tamphuzila zambiri
Akane akane omvera amvere. Dzikoli Lili paulendo. God bless you brother Twaibu
Very true, my brother, anthu asiya kulambira mulungu koma kulambira anthu otumikira.
May God bless you and protect you wherever you are.🙏
Different Branches of satanism
Am always praying for you for protection papa
More years of grace brother.
Amen mtumiki Twaibu
Mumatidalitsa kwambiri
Thanks for detailed information and you have widely open my eyes
Ambuye akutetezeni bro Twaibu
Thank you Mr twaibu
Informative, God bless you
God bless you Mr twaibo
Ine ndinkakonda channel ya TB Joshua koma tsiku Lina ndinakhumudwa ndinalota TB Joshua akundiuza kuti sindizapeza mtendere mpaka kalekale ine mau omwe ndinamuyankha anali oti Mulungu wake uri basi ndinadzidzimuka pomwepo ndipo ndinayamba kuipidwa ndi Emmanuel TV
Lovely
God will protect you!
😢chipembezo chilichonse choyamba ndiye munthu chili mmanja mwa mdierekezi
God protect you
Timverenso bbc documentary on TB Joshua pa you tube. Mwina tiona ma umboni ena. Am not here to judge also
God is with you my brother
Ngati nkotheka tilowetseni mu group la Whatsap tili ndi mafunso komanso zambiri zofuna kudziwa
Ambuye odziwa kuteteza akutetezeni amen
The world behind the scenes. Zinsinsi nzake za Yehova koma zovumbulukazo nza ana a anthu. Ayamikike Yehova Mulungu wamkulukulu ndipo apitirize kukutetezerani
GOD bless you MAN of GOD MR TWAIBU
Mupitilize musaope akusamalilani amene anapulumunsa danielo
Mulungu akutetezeni mr twainu
Payelepayele, ma satanic pastors, prophet atchulidwe Mr Twaibu!!!! Anthu aziwe chooonadi
Uyu simutumiki WA yehova,ngati akurimbana ndi TB Joshua,uyu atha ngati Garu,twaibuyu Alibe wa satanic,apeleka bwanchi wumboni wasatanic atatuluka... judgement belongs to God..we will see him if he will last anymore...
Ine ndikufuna chimene China chinachitika concerning grace chinga Moffat
My eyes is open now
Go deeper man of God
Tingokumbutsana kuti nkhumba siyolakwika kudya. Nkhumba inali yokanidwa inde ku old testament koma ku new testament nyama iliyose inayeretsedwa ndipo palibe verse ku new testament akuti nkhumba ndiyolakwika. Bible likuti ufumu wakumwamba siwa zakudya, tsiku lopembedza kapena zakumwa koma chikhulupiriro chako. Nde ndisadzamveso mawu onyoza nkhumba. Muwerenge Acts 10v9, Roma 14v14-20, 1stTimothy 4v2-6, Col 2v16 pomaliza Hebrew 8v6-10. Twaibu uwerenge ma versewo. Za TB Joshua ndingoti mulungu ndamene akudziwa choonadi ndipo oweruza ndiyekha osati ine or inu a Twayibu. Funso langa ndiloti; Tb joshua adakali moyo simunkayankhula zimenezi bwanji? BBC ndi devil's advocates nde ngati TBj anali wa satanic zikutheka bwanji akulimbana okhaokha? Satana kugawanitsa ufumu wake? Mateyu 12v26. Oweruza ndimwini tidzaziwa choonadi patsikulo.
MULUNGU akutetezen amene.
Tatipangani joine gulu limenelli kuti tivere nawo
Amen!!!!!!!!!!
No hiden secrets under the earth
Amen 🙏🙏
Masiku omaliza awa chowonadi chizakhala choipa. TB joshua was really man of God. Satana sangadziulure yekha. Inuyo mukufunika muphunzire mphamvu ya mzimu woyera mmene imachitira.
Zimenezo nzoona kwambiri
Za TB Joshua zo zamveka koma za Elen g.white ndiye hmmmm!!!
Sabata si tsiku ndimunthu(Jesus)
Amen..
Ndipo ndizoona chifuka u profit umadabwitsa
Wakava ave
mutiyikeko mu WhatsApp group utenga wabwino brother twaibu tikuikeni mumapempelo kuti mutetezeke
Mukalimbana ndi tb joshua mukulimbana ndi mzimu woyera. Inu ngati mumapemphera zenizeni bible limati iyezeni mizimu. Ambuye akutseguleni maso ndipo mudzale ndi mzimu woyera.
Munasintha moyo wanga atwaibu
Nanenso
Ndilinao ine group link yawo
Amen brother twaibu
Ati mpingo suyambitsidwa ndi munthu as if seventh day sinabadwe kamba ka great disappointment 😂😂😂😂
Iwe upange zomwe ungapange Mr twaibu Ali pachimene akuziwa
@@SaraihKambatata religious ignorance
Nkhaniyo ndiyowonad anthu tikhala pa mpando woweluza kod mulungu adzatani great disappointment 😂😂 ay zikomo
Amen
Sometimes whenever you are listening to this guy tamapangani some researches...i am not here to judge😂😂😂
Inu inu mwaumisilanji mtima achimwene
@@NicholasKwajama paliso kuumitsa mtima apa akulu...zinazi tamangomvelani ndkupanga kafukufuku..this guy sinamukhululupilepo since from beginning..he just use ma theories omwe tinkawamva tidakali ana...I think ndiwe mpesa thats why...lol
Tibigosa
SDA pple very funny , they claim to know much and yet knowing nothing . Mr don't judge , leave room for God
About what
Ameni ameni 😊
Twaibu wat zii bwanji alipo km
mateyo: 23vs9 ndipo musamachutchule aliense pansi pano kuti States...
My is open now
🎉😂🎉😂❤😢
Zoona zokhazokha
Mukutisegura mu mzimu
Xx
May God protect you man of God.i want whats up group number if its possible thanks
Mutigaileko whatsApp group link Mr
Ndipange hi ndikugaileko link
@@DuncanDestinybare tipangen
Ndicufuna number wanu mu WatsApp,ndili cu Moçambique
Ineso ndikufuna whatsapp group
Amen
Amen