Vuto malamuro omwe anakonzedwa ndiwolakwika onena kt president azisankha mkulu wa MEC , lamulo limeneli akulu akulu lizatiphetsa ndithu likuyenera kuzatsitha please azisankhidwa ndi nyumba ya malamuro,cipanda apo ndithu tizakhla tikulira mpaka kale
Nanunso mapwala okwakwazawo first sukunva zomwe akukambazo pamenepo tikut anabel sangayendese zisankho ndi mwana Wa munthu Wa mcp sukunva pat mwana wahuleiwe pankholopako
Wa Lilongwe amadziwika,,,osati wa central region ayi,,,sitoseyi enafe ndiye tikunva kuwawa,,,,enanu mwina kwanuko ku Kukasiyako mchinji ,Dowa mwina zanu zilibwino
Koma inuwo ndiye amzelu,,,,koma Malawi eeee sinditha kumuvetsa ndithu,,,,anthu mukukhala ndi mwk10000,,,koma ntchito yake ngati ya mwk25000,,,,koma kakaka akuti poti akulamulawo ndi achigawo chawo,,,,,komandiye enafetu mulibemo,,,,zipangani Mu lilongwenu enafe ndiye tikusiyanitsako ndim'mbuyomu zinthu zinalibwino
Munthu ali ndi zaka 55 ati akupangisa chaunzika choyamba aaa anali kuti?mukumawatenga ku Mozambique uku mma lole mwanu inu ma mp akumulanje mukhaulatu.
Agalu amenewa atikwana kwambr...mademo achitike basi DPP my vote❤❤❤
Good message mec ikozedwe salibwino
Chiganizo chabwino kwambiri keep it up
Love this ❤
Nonse amene mukuma commenter kubackira mcp ndinu zitsiru agaru nyani. Joint opposition more fire
Sindingachite kuvotera dpp wansanje uyu
zili bwino asatinamize tione chilungamo asabele😂😂kkkkkkkk 🙏🙏🙏🙏Amen
Good l dear more fire Dj nyimbo ikhale apita abentcha loyal 🎉🎉🎉🎉💯💯💯
MCP nzeru mulibe munazolowera kupha anthu kuwaponya ma Dam angona
Apa nde Malawi anasintha ❤❤❤❤
Mfundo zabwino tilli pambuyopo timasowa otiilankhulira ❤❤
That means NRB is sided with the MCP the same with MEC
a chakwera akapume tione zina mwtizuza kapumeni ibweleso Dpp basi
Congratulations timafuna zimezo
Apa ndiye yagwilana osalola satana akuloweni plz amalawi akudalila inu kubangamoyo kwatopetsa kwambili
Tell them the truth they must step down before Dem Stretton
Zimenezo ndizomwe tikufuna ife km muzitenge serious
Mwati amatha kupha😂😂😂 ndiyomweyi
Mukungo yaya nthawi tiyeni pansewo ngati muja adapangila iwowo
Point number 1 good
More fire opposition osalola zopoyila ayi akakanika Pempho limenelo chisankho chilephereke basi ali ku mpani pano
Agalu a mcp pamodzi ndi chikangawa akufuna azabele mavoti
Km NRB ndi MEC chikuvuta ndi chani kungotsatira za Ku court komaso maganizo a Malawi
Komatu muzijambula zinthu zomveka bwino,zinazi zikuduka
Dpp Aford Udf Utm chonde musalole agalu awa amcp akufuna abele chisango chonde musalole amalawi akuvutika kwambili 😭😭😭😭😭😭😭
Mcp ikufuna za nkhondo Mulungu lowereraniponi ndithu mutithandize kumenya nkhondoyi patokha sitingathe
Ndipo chonde achakwera sitikufuna smart Matic machine wobera zisakho tikufuna zisakho zikhale mumene zimachitikira nthawi zonse tatopa ndi inu achakwera
Mukungopepha daily wosangopanga action
Misonkhani iyi, imafunika kufotokoza zomwe mzachite mukazawina, nkungotaya nthawi ndikusutsa zili zonse, Ngati tawona kuti a Malawi akuvutika tiyeni tipange fundo kuti anthu akuvotereni, zinazi zikukhala ngati ma plan anatha. Anthu tikuyembekezera omwe angabwere zonthandiza osati izi.
Alibe choyakhula Nena chani akhala muboma kuyamba 2004 ndiye munthu amunamiza chani palibe chimene angabwelese awa sindikuziwa kupanda ndege kugwa sindikuziwa akanakhala akunena anthuwa
Mulira simunati kotsutsa kumaliza umayakhura koma zosamveka,pamene muthere 26 years mukutsutsa mulira mutopa boma sasintha chifukwa chokuverani chisoni kumumayakhura mukamfuse Jen ansa akuwuzani chifukwa chimene adakakamirira undindo mulira simunati
Inu tizingomenyana basi ,kodi mukuwaopa MCP tiyeni nazoni.
Vuto malamuro omwe anakonzedwa ndiwolakwika onena kt president azisankha mkulu wa MEC , lamulo limeneli akulu akulu lizatiphetsa ndithu likuyenera kuzatsitha please azisankhidwa ndi nyumba ya malamuro,cipanda apo ndithu tizakhla tikulira mpaka kale
Zoonadi comrade
Uku ndiye kubwela uku namalomba ndi 1
Koseku kufuna kukakamiza kuti nkhalamba ilowe? Ngati simukuopa auzeni anthu kuti akalembetse
Ine kuno Neno ndalembetsa just within 5 minits tha tha tha zatheka kaya mwina ine ndi wa mwayi koma ku neno ambiri zikutheka
Kod mesa iwo anapa mademo tiyeni tikapange mademo akuluakulu musachedwe tiyeni pasewu
Peter Mathanyula sakutuluka
Namalomba, Chisale
Kodi anthuwo sakuva zomwe mukunena bwanji osapanga action
Zoonadi achoke aku siziwona munthu WA MCP kukhara mukulu wameki
Mmalo moti mziuza anthu azikalembesa nthawi yino mkusokoneza anthu mmaganizo sakulembesa
Kumozambiq machini amanewa akuphesa athu atasokoneza chisakho pana sikulibwino kumalawi zisachitike aimiked asiye pakhale dongosolo labwino
Kulila kosatha a oposition ndipo mulila zenizeni
💙💙
adpp ndinu openga inu munali ndi jane ansa mayi okuba anakubelani kwambili pano mkudandaula chiyani tinatopa nanu kale
Namalomba galu wachabechabe
Mantha kunjenjemera
Kuba kumene amaba iwo akuchita mantha
Ndinu ndani inu kut mukanize kulembesa mavoti
achitsilu inu mutichani Pita akuimaso zanu zada mbava zanya😂😂😂😂😂
Boma ndi machine
Ubwino wake malamulo mupanga nokha mp vuto mukhala mu boma mumawona ngati simuzakhara opposition nchifukwa chani mumamupasa president mphamvu kusakha ma chair Pali anthu 80pervent zipani Zina anthu 10 ngati limana zosekesa bwanji anthu akulembesa mwakathiti chimene mukudaula chani
Zoona ndipo achotsedwe a wankulu wa mec ameneyu sitikumufunaayi
A dpp munazolowera kuba pano mwasauka mukufuna mxikabaso
❤
Namalomba ukhaula sulowa m boma
Kuopa chisankho
Mcp your time is over!!! Chonsechonso mukungogona ndi njala mmakwalalamu
Muyetsetse ma plan achakwera asatheke
Mukodza kumina kuphwisa simunati
Nawoni akuzolowera agaluwo ndi chim'busa chawocho
Anabell mtalimanja sapita kuwina kuli konse chifukwa ndi Malawi Ali ndi zomuyeneleza kukhala pa udindo wina uliwonse palibe chomweungachite
Nanunso mapwala okwakwazawo first sukunva zomwe akukambazo pamenepo tikut anabel sangayendese zisankho ndi mwana Wa munthu Wa mcp sukunva pat mwana wahuleiwe pankholopako
Kodi soprano akamalesa anthu kulembesa azazivotera okha Kodi? Anthu amenewa andikwana osati masewera
Wuzikhala ndi makutu wokumva zomwe zikulankhulidwa osati kumangokomenta chilichonse chifukwa ndiwe wachipani chakupha
Inu tipex uja sikunali kubela
Awaso uchitsilu wakeso, inu tipex munangomunvela mukuthanga ntchito zake , tipex even 2020 anagwilaso ntchito ..
@@symoldicky😂😂😂😂😂😂vutotu longonva koma osazidziwa ndilimeneli,,,,Zoti Tipex amagwilitsidwa tchito pachosankho nthawi zose sakudziwayi,,,,,end zoti tipex ndichiyani sakudziwa
Ndinu onvesa chisoni achitsiru Inu kasambani.
Gulumucha uyu kape wamunthu kanyau
Kkkk mbuli za ANTHU ndithu 😂😂
Chakwela ndi ndiofoila
Nkhani ili apa anthuwa ndiyakuti iwowa ankabera zisankho mmbuyo mosemu nde mpoti amaba akuganiza kuti azawowa awaberaso za ziii
Inu a dpp mwango khala anthu asanje chabe zindikilani anthu ondetsa bungwe lachisankho ndamalawi nawoso Alindi ufulu komaso vuto ndilakt inuyo mukumbukila momwe inu mumabela zisankho zomwe inumukufuna ziwawa siyani kuwononga malawi
Kuwopa nonsenu zisankho Eeee
Namalomba ndi chitsiru
Ndiye pita iweyo ukapange press briefing conference yako
@@IbrahimJackson-i8h😂😂😂😂😂😂komandiyetu iwowo akuwona kuti zawo zilibwino,,,,ndiye awasiye omwe sakuziwona bwinowo basitu,,,,
Tili pambuyo panu , mulimbikile pamfundo zanuzo
Akut muvale zilimbe kuchosa mcp I doudt
Agalu nonse osusa plus ma supporters anu
Tawasumileni anrb wo
Kuno ku thyolo palibe chichitika amecwaaa
😂😂😂😂😂Zimutu zikuluzikulu ndi mimba
Zokambirana zake za ziii anthu akuluakulu ngati awa
Iwe ndiye usanditukwanise wanva
Wa Lilongwe amadziwika,,,osati wa central region ayi,,,sitoseyi enafe ndiye tikunva kuwawa,,,,enanu mwina kwanuko ku Kukasiyako mchinji ,Dowa mwina zanu zilibwino
Eya zoona
Mwati amitu ikulu ikulu 😅
Inu ndi zitsiludi bas zeru mulibe 😂😂😂
Iweyo nde uchitsilu ngwa ma level nchifukwa or udzilubwa zankutu sudziwansyi
Koma inuwo ndiye amzelu,,,,koma Malawi eeee sinditha kumuvetsa ndithu,,,,anthu mukukhala ndi mwk10000,,,koma ntchito yake ngati ya mwk25000,,,,koma kakaka akuti poti akulamulawo ndi achigawo chawo,,,,,komandiye enafetu mulibemo,,,,zipangani Mu lilongwenu enafe ndiye tikusiyanitsako ndim'mbuyomu zinthu zinalibwino
Inuvomerezan kut simuwina tafokozan fundo kt athu adzakuvoteren osat zimenezo zomañgot mukuba mwanji
za ziiiii zopanda mutu
Komaso zoti mkharamba idzabweraso pampando kufuna bokosi muyiware
Komano ndikudabwananutu Anthu 20million muli sure kuti onse akavotela mcp kuti mupeze 50+1%that is true???guys in which way
😂😂😂😂kma iwe panopa kumatinso boola 😅😅😅😅thawi yakhalambayo opusa iwe
Zoonadi
Zianthu zopanda nzelu zili apa zangovala mabuluku wopanda kanthu ndizisilu zinapanga zokha malamulo lelo akuti chani adpp mkuwona ngati mmene mnabela inu anzanuso akubelani ndinu zisilu kwabasi nanga jeni asa sanali wadpp zisilu zaanthu
Zaziii munazolowera kubera masankho kuzera mwa a Mec ndiye mukungoopa palibe zobera apa,mwangozazana opusa okhaokha ku opposition ko,jane Ansa analola bwanji kuti Dpp izipita ulemerero onse uli mnyumba mwake?mungofuna anzanu asamagwire ntchito.muzavomere basi simungawine.
Munthu ali ndi zaka 55 ati akupangisa chaunzika choyamba aaa anali kuti?mukumawatenga ku Mozambique uku mma lole mwanu inu ma mp akumulanje mukhaulatu.
Mbabva ndizomwezi ankadya bwino m,boma nde pano zawavuta akufunaso axidzaba a dpp nkhawa yawapeza mcp sikuchoka mboma