BON KALINDO LERO PA 18 September 2024🙌🙌🙌

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 58

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i День тому +1

    The DC be strong 💪 my guy 👦 one day is one day mr president bon kalindo

  • @BamboAnura
    @BamboAnura День тому +2

    Mtsoleri. Opanda Chisoni 😢 at mpang'ono ndi anthu sangasinthe dziko komaso Moyo ya a Malawi all he cares { is his well being and that of his commorades🥸🥸🥸 }
    Long live the DC Kalindoo For Sure ndiwe Chilembwe wathu walero. I can't wait to see you ruling Malawi and change Malawi for Better

    • @AmoTiamo
      @AmoTiamo 16 годин тому

      Inenso kunena zoona za president uyu eeeeish sizinthu

  • @OmarBmphaya
    @OmarBmphaya День тому +3

    Ndikupepha amalawi muli kumudziko chonde pokavota kavoteni bwino chifukwa zomwe akupangachakwelazi siziphula kathu

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri День тому +1

    The DC woyeeeeeee ❤❤❤❤❤

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma День тому +3

    Walitenga zikoli ngati dimba laamake ndinthu

  • @DennisKalima
    @DennisKalima День тому +2

    Chakwela walepheleletu achoke sitikunufuna munthu okupha okuba

  • @bonfacemoyo5171
    @bonfacemoyo5171 День тому +1

    Tell our chiefs to say no such trips tell the president to say you are taking me out but my people are in trouble

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza День тому

    God bless you true story tha DC❤❤❤❤

  • @ALLIEDAUDI
    @ALLIEDAUDI 23 години тому

    The DC ❤❤🎉🎉🎉

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242 День тому

    Kodi ndege akwelayo siingagwe KT alondole achilima achakwelawa ife atikwana crc

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko День тому

    koma marawi ndiye chakwera akuthawa chirungamo ameneyo uyoyo sakukhazikika chifukwa chamagazi a anthu amene wampha ndimanyazitu amenewo pazimene anapanga akuthawa mafuso koma ambuye rowereranipo

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma День тому

    Ndipo rive uyu ayende bwino uyu chakwela watikwana

  • @EbrahimMmadi
    @EbrahimMmadi 14 годин тому

    Mcp party they will never change no matter what,if u think they will change ask ur forfather .what they do to them.

  • @patsonmdwazika3108
    @patsonmdwazika3108 День тому

    Mr nama drama inu musalimbane ndipa central pangani za kwanuko minda inatengedwa ndi azungu mukukanika kutenga pa central kulibe kubweleketsa minda usaname

  • @BistonMacheso
    @BistonMacheso День тому

    Kodi akuti chani anthu onsewo akupita kunjawo koma ziko lamalawi mulungu aliphulumuse ndinthu muthu kuyenda kuposa azibusa chifukwa amayendatu anthu amulungu kukatumikira

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c День тому

    A opposition onse ndiombwambwana akuopa kumangidwa azalamulidwaso ndi mcp

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 17 годин тому

    ndipo msogoleri uyu ayi ndithu wandigomesa mmm

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma День тому

    Ndipo zikolidi walitenga ngati dimba laaamakedi

  • @HarlodLemwe
    @HarlodLemwe 21 годину тому

    Ndipo simunat ndichiambi chabe chimene kkkkkkkkkk kumwera ndikomwe anthu akuzuzika

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 17 годин тому

    Agwa nayo denge imeneyo😂😂😂😂

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e День тому

    Ndi chifukwa chake aliyense akufuna upulezident muno mu Malawi chifukwa upulezident muno ndiodyera anthu

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 18 годин тому

    Kodi sizingatheke akamabwera kumeneko Amalawi kukwiya mkukachita nkhondo pa airport? akaone nyekhwe? munthu wanji wopanda chisoni ???
    mmene zavutilam mdzikoli, iye mkuononga ndalama zankhani nkhani Koma popanda phindu. mmalo mopulumusa miyoyo ya Amalawi powapasa mtengo wabwino wachimanga,mankhwala nzipatala
    Ambuye kumwambako timveleni mapemphero athu chonde Ambuye chonde

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 17 годин тому

    Kumvetsa chisoni Malawi 😢

  • @ElmajorForeign
    @ElmajorForeign День тому

    Kodi a katolika akupanga chani kwenikweni osatulusa pastrol letter ✉ amatulusa ija bwanjiii

  • @Chancy-ry4tw
    @Chancy-ry4tw День тому

    The Diciiiiiiiiiiiiiiiiiiiii

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w День тому

    Malawi ndi prison kaletu, anthu samamva akakhala mu boma.

  • @Felix-j3f7y
    @Felix-j3f7y День тому

    Koma chakwera angokhalira kukwera ndege bwanji?

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 День тому

    Akudya. Bwino. 😢😢😢😢

  • @abelkalulu2904
    @abelkalulu2904 День тому

    Zaziii

  • @LindaKapeta-u6d
    @LindaKapeta-u6d 22 години тому

    😂😂😂😂😂 Osamva

  • @MauriceMukona
    @MauriceMukona День тому

    🌽🌽🌽🌽✍️💙🤝

  • @mathewsnachuma8086
    @mathewsnachuma8086 День тому

    THE DCCCCC

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h День тому

    Galu iwe panyopo, Peter wakoyo samatenga gulu kupita Ku Unga? Panyopo Kalindo

    • @jumbradoone4164
      @jumbradoone4164 День тому

      Kutukwana mupinda chani?

    • @munashemoyo4190
      @munashemoyo4190 День тому

      Gwape iwe opusa opanda kanthu kudalira kulandila 2pin ya chakwera chimutu

    • @VictoriaWilliam-ms2ft
      @VictoriaWilliam-ms2ft День тому

      Kutukwana konseko 2000 Yomwe mukupatsidwayo basi? Ndiwe omvetsa chisoni eti kalindo watchulapo Peter apa? U mbuli sizinthu sure

    • @peterthawi
      @peterthawi День тому

      umbuli basi...KALINDO akunena zoona..nde mukutukwana chani ?

    • @stevenfrancism3638
      @stevenfrancism3638 День тому

      Pali zotukwanila APA?

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 День тому

    Kkkkkkk😂😂😂

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h День тому

    This is trip is very important for our country, wait muona ndalama zimene abwlele nazo

    • @razackrashid1668
      @razackrashid1668 День тому

      Zopephazo

    • @jumbradoone4164
      @jumbradoone4164 День тому

      Aaaahhh iweso ndiwabodza eti?

    • @VictoriaWilliam-ms2ft
      @VictoriaWilliam-ms2ft День тому +1

      Ndiye akabweretsa ndalamazo mesa ndizache akupanga nazo chani chothandiza amalawi? Anthu onse omwe wawatenga iyewo akukatenga ndalama? Pls tiyeni tisanalankhule tiziganiza kaye malawi ali pamoto uyu

    • @peterthawi
      @peterthawi День тому +1

      kupemphetsapemphetsa kwa president wanuyi...nkumene kukulowetsa dzikoli pansi.nxeru mulibe ...

  • @OlayjerempondahMponda
    @OlayjerempondahMponda День тому

    😂

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h День тому

    Akukwera ndege anapita Ku school Ka. Iwe ndi umbuli wakowo uzikwera wheelbarrow kkkkk

    • @nabphiri2627
      @nabphiri2627 День тому

      Iwe ndiwe omvetsa chisoni kwambiri, anakuuza ndani kuti okwera ndege ndamene anapita ku school kokha?

    • @JoyceLiwonde
      @JoyceLiwonde 17 годин тому

      Ndiwe galu kwambili

  • @LmmskKambale
    @LmmskKambale День тому

    Not good for our culture

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma День тому

    Ndipo zikolidi walitenga ngati dimba laaamakedi

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 18 годин тому

    Kodi sizingatheke akamabwera kumeneko Amalawi kukwiya mkukachita nkhondo pa airport? akaone nyekhwe? munthu wanji wopanda chisoni ???
    mmene zavutilam mdzikoli, iye mkuononga ndalama zankhani nkhani Koma popanda phindu. mmalo mopulumusa miyoyo ya Amalawi powapasa mtengo wabwino wachimanga,mankhwala nzipatala
    Ambuye kumwambako timveleni mapemphero athu chonde Ambuye chonde

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma День тому

    Ndipo zikolidi walitenga ngati dimba laaamakedi

  • @IdrisahChuma
    @IdrisahChuma День тому

    Ndipo zikolidi walitenga ngati dimba laaamakedi