TCHUTCHUTCHU - 28 JUN 2018 - PATRICIA KALIATI
Вставка
- Опубліковано 3 жов 2024
- Hon Patricia Kaliati MP. Popularly known as 'akweni' by her peers and her constituents. She' s been member of parliament for Mulanje North constituency since 1999. She has been a staunch supporter of the ruling Democratic Progressive Party in Malawi earning her ministerial appointments on several occassions. In 2012 together with other 5 DPP loyalists she was arrested by the PP regime for allegedly plotting to usurp power from Joyce Banda, then President of Malawi. In a dramatic turn of events Patricia Kaliati has now switched allegiance, drumming up support for Malawi's Vice President Saulos Chilima and his Chilima movement. What went wrong?
My role model 🥰❤️
True Malawian woman
Akweni, following👏👏👏
With you all the way.. for a better Malawi
Ndakunva kweni
koma kaliati
DR. PATRICIA KALIATI. Asafuna akhale.
Kweni umatha iweyo kodi u MP udakapitirirabe?
sindine wa kwa mai kaliyati koma ndimanva kwambiri zoti zithu zake amachita bwino ndipo zoti akhodza kuwinaso ndi zithu zosakaikisa coz she is doing well
Kkkkkk akweni ati mkamwa mukuwalemera kuti anene Dr kweni kkkkk
Akweni kkkkkkk,mwati life mp????? Pano ndiye mukuti bwanji mene mwaluzamu? Ndi abambo omwe kugwa chagadwa!!!!!
Mayi Patricia othekela ndimakunyadilani
Kweni tsopano, mai olimba mtima komaso okonda anthu ake
Akweni mumakwana kwabasi
Koma akweni mukuitha
Kodi oyang'anira ndi mai maria,kapena mulungu?Tiphunzitseni chonde
Zazathuwatu simungazinvesesw
kunena zoona mai uyu amakonda anthu
chilima sakufuna ndichifukwa sakuyankhulapo kanthu akuchita kukakamizidwa aaaaa sangawinetu koma coz mwachitawu ndiupandu
zikukanikani ngati momwe zinawakanikila amayi joyce banda mwapupuluma
Kkkkkkkkkk ati anthu akumetesa Ku barber iye akumetabe ndi lazer
Hahahaha wandisekesa bwanji 32:21 ati atambala amasiku ano analowa fake, akumalira eight bar
ofunikadi kumangowakhoma nkhongo zawoza....kkkkkk ...koma A KWENI...
Kkkkk koma kaliat
Achedwepo heti kkkkk
2019 waluza chagadaaaaaa iwe chikwwni iwe walapa kkkkkkkkkkkkkkkk
Mulipobe pano mukuti bwanji akuru 😂😂😂😂😂
Kkkk kweni
wathuwathu Akweni
Akweni. Tilipambuyo. Panu
Kunama kokhakokha munali ku UDf kenako ku dpp pano ku movement. mungofuna ndalama not kuthandiza anthu
zikuvutani chilima sangawine sereus
It's clear she's disgruntled,sorry with your drama group