Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Dziko lathu likufunikira utsogoleli waukadziotche coz zinthu pomwe zafikapa ana athu sazapeza pogwira 😢😢😢
Exactly i like your statement mr chunga ndizothekadi dziko la Malawi sungalimvetse
Muzisiyanitsa ngozi ya normal ndiyopanga guys , and musamnamizile woyendetsa poti sangayankhe anapita , ngati inali ngozi bwanji anthuwa anamwedwa magaz???
Thank you your malangizo ndithu, zimenezi zidzadzetse ziwawa tsiku lina ndithu
Hot current please telling about You can know witiness about crush history is best teacher
Black box
Koma boma la Malawi analilodzayo 2025 atimasule 😢 ndipo zikungoonetselatu kt ma president athu ndiosamva ndipo zindivuta kudzakhulupiliranso andale. Inu a Chunga mumatha ndipo respect ❤❤ timafunako nkhani yanyanja abale 😢 RIP Saulos Chilima 😢😢💔💔😭😭
1:37
Mmmm akulu akulu or kutabwela ndege 50 komabe biyeni sazabwelanso...or ili ya new one ngati a wonder muli pa program yoti musowe ndi ndegeyo anthu ake awa sungalimbe ...zitayeni basi chiona chipande poomola
Amalawi ndi ife olephera pachilichonse Makamaka ndi kusadziwa kwa apule aaaa zomvetsa chisoni
How are you discussing the report in the most recent hot currents?It seems you are missing the point
They are addressing Negligence at its best
Ndiye inu a times muli sure kuti inalidi ngozi yachilengedwe pa ngozi imeneyija muli ma mistake ambilimbili omwe akuonesa kuti anachita kukhonza ndege inagwa 4.5 meters ingaphe anthu onse
These guys are playing safe the report missed a lot of points
Vuto ndiloti amalawi tipusa kwambili
Malawi government ndiyosava chomwe amaziwa ndi kusolora bas
This hot current is focusing on that report but that was a bulllshit one..... Munalibe chilungamo
Penatu ukapepetulidwa sumamva😅😅😅 umazazindikila ilim'mutu......Ujeni yake siimeneyitu....Owhoo!
Takambiranani za nyanja zikumveka Zi please zandegezi panopa sizimveka bwino tizapitiliza kufufuzabe
We have airwings not airports
There is no accountability of government funds
Should we say our country should learn from you guys? Come on Malawi we can do better