Our last hope,,,, His exllence professor Peter muthalika The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2025 general election . Let's vote wisely before it's too late , This is our and only country of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 let's build a better MALAWl by uniting togeder
Kumbuseni chakwera yo munthu wabodza uyu chakwera anane yekha kuti akazakanika, azatula president kom leo, akulilira kuti tipasenso 5 years ina yachani maka maka munthu walephera uyu chimene wapanga cha nzelu ndi chikangwawa basi kuba, nkaza , muuzeni chilungamo cho , chakwera wasankho,
This is more than powerful message bro timakunyadila koopsa mulungu adzikudalitsa
Big up to suleman
Osamanyoza zipan zina kodi ukudana ndi udf chifukwa chan dont do that
@AkbarAllih-ln6ky I don't hate UDF anymore but MCP crocodile party
Comrade bones amandiwaza ndi voice bravo bravo.
You are the hero and you are the best of the best and you are the only one who makes people understand very strong message
Kuti Munthu umapelekapo ndemanga apa bwezi ine ndili oyamba. Gud shot Comrade. Chakwera chitsiru uyu
Powerful message my brother God protect and bless u
🙏🙏🙏🙏 mumatiyimilira malume.
I salute you captain Bones,,yu speak with wisdom,,keep it up n God bless yu more 👏
Zowonandi mkuluwanga ❤
Ameen mau mau popanda chigamba chilungamo munthu wamkulu ulemu wanu
Powerful massage
❤❤❤❤❤❤❤❤ chilungamo chomveka ngat mwano
Mau opanda chigamba
Mmmm China ndichina koma mkulu uyu amayankhula mwanzeru kwambili
Awa azipita alephela 😂😂😂
Khokhokhokho kuyankhula Mau amphamvu .....izi ndizoona zokhazokha
Powerful words ❤❤
Comrade chilungamo ngati mwala apangadi campaign ya dpp
Mumayankhula chilungamo achimwene
Ati qkuioncha chipani chaos pompano a Usi ,hmmmm tiaonera
Zoona zache udf and mcpyo aiiiiiiiii koma Atupele angapite ku mcpko apitako yekha
😂😂😂 Mkulu uyu ndi dolo
Auzeni malume akhutukuve anthuwa
Our last hope,,,,
His exllence professor Peter muthalika
The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2025 general election .
Let's vote wisely before it's too late ,
This is our and only country of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 let's build a better MALAWl by uniting togeder
Kkkkk kkkkkk Awuzeni achitsiruwo😂
goood
Game on Captain Bones 😍
Ulenu wanu bwana
Zoona zokha zokha basi kunena kosanyengelera
Purinzi mtima ukutiwawa amarawi.mugorremba nambara yachakwera ndimuyimbire 4n akangoyakha wapita ameneyu purinzi nambara
Nice one my brother ur tolking the truth ❤
Kayin mwazi ukulilila ku ntaka yehova wakwiya
Mau koma awa mcp inasakha nduna za uchitsilu zokha zokha chaka chino chikangawa party yapakila
Akuru inu musamasowe please
Kumbuseni chakwera yo munthu wabodza uyu chakwera anane yekha kuti akazakanika, azatula president kom leo, akulilira kuti tipasenso 5 years ina yachani maka maka munthu walephera uyu chimene wapanga cha nzelu ndi chikangwawa basi kuba, nkaza , muuzeni chilungamo cho , chakwera wasankho,
Strongest words 💪💪💪💪
Sulute
Eeeeeee😅 ayi guys 🙌 chikangawa akapuma kumwamba bas 😂😂
Chalakweee 😂😂😂😂 manyaka amunthu , mbudzi yeni yeni yamunthu, chisilu cheni cheni
Awuze amanama chakwelayo moto kuti buuuuuuuu
Big ulemu wanu
Musatelo chondee kumbukirani kt munali mbusa ndiye mbusa sakhala wa upandu chondee lapani tembenukani mtima kut mukalowe
Uyu anabadwila kudabwe oil anakwana
Kuyakhula kwake chakwerayi akut zaka zapitazi anali pachiphinjo zofunya zithupswa boma la Dpp linawonga zithu zambir ndiye zaka 5 zikubwelazi zizakhala bwino akuwuza mwana Mesa bwez atayesesa kuchita bwino zaka zoyambililazi kut akope anthu azoteleso koma apa waga nayo😅😅😅😅
Ulemu wanu bwana kuyankhula mosapsatira,tiuzeni zowona zokhazokha
Zamuphwikira😂😂😂😂😂
Mbambande bwana 😂
Chilungamo tonse tikudzunzika
Zoona zokha zokha basi kunena kosanyengelera