Yes ndizotheka kubowoleza Mr Tipa koma vuto lomwe liri mu muzik industry yathuyu kunachuluka Timilungu tofuna kutilambira kuti zako ziyere nde Muthu ukasakha kulambira timilungu timeneto umatchukadi koma kwathawi yochepa kenako fwakalara Koma best musician ndiyemwe amasakha komaso kulora kuti maimbidwe ake afikire ka guru ka anthu ochepawo amene akukwanisa kuwafikira posalambira wina wake
I like this guy for his music, it touches me so hard, I was wondering where about of him but now am happy to hear that he is still doing music big up tipa boy!!!!.
Aliyese amakhala ndichisankho inde iyeyo Ali okhozeka ndithudi chifukwa ndimaloto Ake angathe kukwanilisa inde kmso atafuna kubwelela Ku south kuthekela alinakoso nde let's go sapot fanayu apitilize missions
Waganiza bwino. Coz nalo dziko la south Africa likadayambaso kumusaka kuti lizipindula mwa iyeyu. Zosatila zake zikadakhala ngati za Bushiri. Kuthawa mkusiya chuma dziko laweni. Tipa fire.
Uyuu wabooleza kale Siwe wekha is hit song now is on repeat
Yes ndizotheka kubowoleza Mr Tipa koma vuto lomwe liri mu muzik industry yathuyu kunachuluka
Timilungu tofuna kutilambira kuti zako ziyere nde Muthu ukasakha kulambira timilungu timeneto umatchukadi koma kwathawi yochepa kenako fwakalara
Koma best musician ndiyemwe amasakha komaso kulora kuti maimbidwe ake afikire ka guru ka anthu ochepawo amene akukwanisa kuwafikira posalambira wina wake
Yes he will most famous in Malawi
I like this guy for his music, it touches me so hard, I was wondering where about of him but now am happy to hear that he is still doing music big up tipa boy!!!!.
You are the best ❤
Ndizotheka I love the guy he has a talent
Yes ndizitheka ndi big man ameneyu timakonda kwabasi
May the good Lord almighty be with you @Taimon Tipa🙏🙏❤❤ you may live long and in good health 🙏
Watengako gawo lake ameneyu ❤❤❤❤
Baba,god is great it will be happening
Od mkaveleso nyimbo yake apa tamulandla kale uyu😊
Nice koma wapanga chigabizo chabho moti ineso ndikubwelele kunyumba
Ndpo ku ma show Nd gokonko waiphula amneu good musician taimon
Good luck to you
🎉🎉🎉❤❤❤amatha
Taimoni amaimba bwino and I love him as an artist
Uyuyu NDI shasha ❤❤❤
Ilike this guy ayiphula ndithu ku malawi
Chilichonse ndi chotheka kwa iye ndi mmene akuyimbira abooleza ndithu
According to my suggestion he is very important man in music than others
Kelly Kay you can't compare with Taimon Tipa, Tipa ndi machine owopsa zedi komanso got uncountable fans❤❤❤❤
Abooleza ndithu welcome again taimon tipa to Malawi musicians be free
We are praying for him God will take him there
Zitheka osaopa amatha
Obviously he will make it no doubt
The song siwe wekha
This guy is talented ndipo ndi makina owopsa zedi❤❤❤❤
Aboleza bwana❤
Aliyese amakhala ndichisankho inde iyeyo Ali okhozeka ndithudi chifukwa ndimaloto Ake angathe kukwanilisa inde kmso atafuna kubwelela Ku south kuthekela alinakoso nde let's go sapot fanayu apitilize missions
Ndpo zatheka kale siwe wekha
Mulungu wamwitana ndi cholinga
Is going to be the best 🎉❤
Uyuyu ndi Dolo❤
Mwanayuuu aziimba mmene akuimbilamu asalowee zadzikoo
Aboledza ❤🎉 ndikatundu mwanayo
Welcome back madhala. Uyu amaika music ndipo agwesatu azibambo enawa
Ok kodi nyamatayu anali kuno ku south Africa?
Zabwino zonse nyamata oyimba modekha usasunthike koma pita chitsogolo ili ndi luso lochokera kwa yehova
tonse timankonda❤❤❤
Rashley ameneyo tinamutuluka
ndi sha sha amene unja
Uyu ndi dolo,,tili pambuyo pake
inu mukumuyika malire?
Yes
Awa ndimachine osakaika
Ndimmene akuimbila zitheka
Ndi zotheka taimon abooleza ndthu
Don't hate him....uyu amayimba bwino 🎉🎉
Dolo kwambiri taimon tipa ❤❤❤😊😊
eeee taimon ndi oyimba wachabe
Yes abooleza Ali ndi lunso
Tipa amatha ndipo asaope
Ndipo ndizotheka akumaimba nyimbo zolimbikisa kwambili
That's true
Zitheka palibe so ataaa
Mwana amatha uyu akwani sye yekha inanso akusaka zomwezo
Eya ndizotheka chifukwa athu akumukonda kale
Taimon will make it and mpata anaupeza kale,,,space mu music industry yake ilipo kale
Yah he can also make it,because talent is an unique
Uyu wapeza kale mpata
Ku Malawi ufiti basi😢😢
Taimon is the best
Uyuyu waboleza kale!!!!
Ndiponso mwin ali pa 1poyerekeza mdi enawoaka enefe timazisatira bwino
Abooleza ameneyu muli mfundo za bho mu nyimbo zake ziti wina aliyese angathe kuzikonda and nabora atsogoze mulungu
He's going to make it
Uyu wabooleza kare amwene
Kukaika ndi chimo. Zitheka bora faith
Bola asalowere Ku mipingo ya chionongekoyi ili dziko munoyi
tamuchosenipo Lashley malo akewo muikepo afanawa
Inu Adawo Amaswa havy kulibe kunong`ononeza bodo ai Chifukwa Amaswa kwambiri nyimbo zake ximatiwaza havy
sam ndiwe kape
Zitheka kwambiliso ubwn wake sanachoke atanyoza amfumu
Taimon ndidolo akuyimba mwachikoka
Ndpo musakaike Tippa ndi dolo than Dreimo
Uyu waboleza kale
he is better
Amaimba bwino tipa love more
Aaaa iwe Mesa waboleza kale ameneyi
koma ase umaimba bho iweyo umatimilira ngakhale wamveka pompano komabe aliyese akuziwa ndithu....koma osavomela zolambila milungu chifukwa ukumasowa usanadyelele mapeto ake
Ine ku moçambique 🇲🇿 taimon tipa amatha apeza malo chifukwa amatha kuimba za tathauzo
I like this guy
Tips nidolo osati zinazo
Mesa zikakamuvuta akabwelera ku South Africa
Sasafulika kkkkkkkk
kkkk
Ayi nachita kugwidwa ndi yifeyo wotsati anangochita chigano ayi aaaa chonwelela kumqlqyiko ayi kunama aaaaa
Sanalakwise kuzayesa mwayi kumudzi mulungu akafuna kutukula Muthu sasamala kuti kuli ndani amachotsa kapena kuyika amene wafuna
Taimon Tipa ndi Dolo angofunika support ya mphavu
Ndizotheka abowoleza basi
Ndzotheka ndthu
Aaaa inu mwanayu aboolez ndpo osakaik mix mafuso enawo nd otsitsilan pas
Kuimba kuli maimbidwe imbidwe tizimukonda malingana ndi Chamba chomwe amayimba komaso fundo zomwe zikumapezeka mu nyimbozo mwanayu fundo zilimo
Ada awa amaimba
Akwanisa
Taimon ndimunthu amene amayimba bwino kwambili ndipo kubooleza sikuvuta chifukwa ndiwoyimba yemwe amayimba waukadaulo
Waganiza bwino. Coz nalo dziko la south Africa likadayambaso kumusaka kuti lizipindula mwa iyeyu. Zosatila zake zikadakhala ngati za Bushiri. Kuthawa mkusiya chuma dziko laweni. Tipa fire.
Iwe onesimus siwa international?
I love you tipha
Aboleza
Dolo
Ali kale mu line ndi katundu taimon