КОМЕНТАРІ •

  • @VungaQueen
    @VungaQueen 19 днів тому +19

    Apa nde chakwela akutitola kwambiri mulungu mumve kulilira kwa amalawife mupaka kugilitsa mutchenga uli wachilengendwe ayi zikomo magamuro anu chakwera adutsa muyetso mitsozi yanthu kuvutika kwanthu dzikhare pa panja lanu achakwera 🥲🥲 inu aboni kalindo keep it up kutiuza anthu opepelawa 🔥🔥🔥🔥

    • @FRAVIOKUNSANJA
      @FRAVIOKUNSANJA 19 днів тому

      Koma boma ili lafika posauzana n'chenga umene akulesa wayamba kuvuula lero ameneyu galu kwabasi chakwera atimaliza tonse

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk 19 днів тому +2

    Powerful talking from our beloved president, president for the poor always there for poor Malawian citizens the Dddddd Cccccc!!!!, proud of you always. May the good Lord continue to guide and protect you always 🔥🔥🔥🔥

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana 19 днів тому +3

    Akuti apolice adzisilira mpunga WA Ana school koma ADC inuyo ndi wa wani long live a kalindo anya manyi achakwera achitsiru amenewo , nde bwino akalindo ineso maganizo amenewo nariwo kuti athu asavotere chauzika akalindo inuyo inuyo ambuye akudaritseni ife kwakwataine sitikupanga nawo zopusazo tikulira ife ku Ntcheu😢😢😢 koma God knows chakwera adzafa imfa yowawa

  • @user-hk3hg1to4e
    @user-hk3hg1to4e 19 днів тому +4

    Anatiloza ndi malemu chilima aise pomuchita follow achinyamata ife😢😢

  • @FisherAction
    @FisherAction 19 днів тому +3

    Big mulungu akudaliseni ndipo pitirizani kutiombola kuwachosa amalawi mw agaluwa a mcp

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 18 днів тому

    God bless you Mr DC you always stand for the poor this government of chakwala is useless ever

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 19 днів тому +2

    This two much guyz..koma kuli Mulungu amatha kumuchitsa munthu pa mpando ndikuthamangitsa kukamusiya ku ntchire..koma mmawelenga baibulo????? Inalipo mfumu ina imachita zimenezi koma ngati simusamala Mr president ndi nduna zanu mupalanura mkwiyo wa Yehova....take my note

  • @GoodsonDiwadiwa
    @GoodsonDiwadiwa 18 днів тому +1

    The Dc Bon Kalindo anthileni fire anthu osowa umunthuwa osanyengelera ayi

  • @StevieChikaonda
    @StevieChikaonda 18 днів тому

    Uku nde kung'alulatu 10,000% ayi zikomo ndithu💪💪💪💪💪💪💪

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 19 днів тому +1

    Koma Mulungu ngati kunali kufuna kwanu kuti munthu uyu awulawe u president ayi pafikapa ife anthu anu timveni kulira kwathu 😢, Ife anthu akumuzi kuti tigule sopo timadalira kuvuwula mchenga omwewo kuti tichape, onani pomwe zinthu zafikapa Yehova, ingobwerani muzaweruzepo dziko lanuli Ambuye

  • @EmmanuelMpalagule
    @EmmanuelMpalagule 19 днів тому

    Mr kalindo u are a hero, the opposition the very week, the opposition is in deep slumber,

  • @vitumbikokamanga5869
    @vitumbikokamanga5869 19 днів тому +1

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤go deeper mr kalindo you are the best ❤❤❤❤❤❤

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 19 днів тому

    Mr president the DC we love you and greetings from North London UK

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 19 днів тому +1

    Kalindo we are failing to thank you but only God will thank you

  • @GamaGama-z8p
    @GamaGama-z8p 19 днів тому

    Tell dem the dccccc!!! Never stop fighting for the poor innocent people we vote for purposes Mr born we are on ur side

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN 19 днів тому

    Timanva nanu kukoma nsaname🎉🎉
    ndipo mau anu amatitothoza ifeo,ndiposo pa mpando wa upresident inuo mwafika kale bwana,zolembalemba zangosala tsiku loyikika bas

  • @RidwanAdam-nq6lz
    @RidwanAdam-nq6lz 19 днів тому +2

    Booooon kalindooooo 🔥🔥

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 19 днів тому +1

    Muli bwino koma Anthu Ena sakukhulupilira inuyo boss munatitenga kutisiya ku sewo inuyo munapita kunja nokha mukadya ndalama zatha lero mwabwera 😂😂😂😂😂😂

  • @user-or7ng3fj8f
    @user-or7ng3fj8f 19 днів тому

    Mr Bonnnnnnnnnnn kalindo DC big up kodi bwanji osayambisa madem bwanji kumalawiko galu ameneyo ife kuno atikwana kwambiri ndithu tiye nazo Mr bonnnnnn kalindo the DC

  • @limbanimtitima9170
    @limbanimtitima9170 19 днів тому +1

    Kung'alula big man,ife Angoni kuntcheu ndife oganiza kkkkk😂

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon 18 днів тому

    Born kalindo more 🔥

  • @pacharokoloviko1694
    @pacharokoloviko1694 14 днів тому

    😂😂😂😂 ati kufuna kumangidwa!! Komadi ndiwe DC

  • @kelvinmphande3754
    @kelvinmphande3754 19 днів тому +1

    It's the sikusinja Gwenembe song for me

  • @user-wu4tl2yn9e
    @user-wu4tl2yn9e 18 днів тому

    Khaaaaaa wafika the DC

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju 19 днів тому

    Make mbuuu mwana mbuuuuu long live the DC

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t 19 днів тому +1

    The dc our poor president in Malawi

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 19 днів тому

    The DC 🔥🔥💕 Chakwera atule pansi udindo..., Palibe zoti asintheso ai.., tikumunyengelela uyuh.. _

  • @chimwemwemasamba2880
    @chimwemwemasamba2880 18 днів тому

    Allowance ya manebbtatenga koma ndiyochepa kobasi....polingalira ndi mmene zinthu zakweleramu

  • @user-ko1lk3br4r
    @user-ko1lk3br4r 19 днів тому +1

    Mafuta ayamba kuchoka ku Mozambique kukafika ku area 50 ku Lilongwe kudzela pa njanje ai zikomo

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge 19 днів тому

    ULEMU WANU MR, THE DC..... BON KALINDO 💪✊✊✊📡🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @PempheroKasimongwa
    @PempheroKasimongwa 18 днів тому

    Kalindo 🎉🎉 iweyo ndi 1,,,ku Egypt kuja timadya kwabasi ❤❤

  • @JabesAlfaiate-t4v
    @JabesAlfaiate-t4v 19 днів тому

    A kalindo tiyankhulileni ife tili nanu mcp ndi yoipadi ifeyo a malawi amenetili kuno ku Mozambique tili o khuzika ndi zomwe likuchita boma la a chakwela , ku vuula mchenga mpaka laicence zinachitikako kuti ? Keep it up a kalindo.

  • @AudettaYohanie-fl3oc
    @AudettaYohanie-fl3oc 19 днів тому +1

    Aaaah koma izizi ndiye chakwera wationjedza zedi ,koma chifukwa chani kweni kweni?

  • @user-vh9uk1jy7w
    @user-vh9uk1jy7w 19 днів тому

    Our president more fire 🔥 Booooon kalindoooo 🔥 🙌

  • @KnowledgecGodwin-xo4pw
    @KnowledgecGodwin-xo4pw 19 днів тому +2

    Chakwera nkongo wamako ,mboli Yako ,machende ako ,alipwisi alitongo.

  • @LovelyJapaneseMaples-xc2bc
    @LovelyJapaneseMaples-xc2bc 18 днів тому

    Kuswakuswa big osaopa😊

  • @RafickRaj
    @RafickRaj 19 днів тому

    Mmatha madhala madhala inu mungoyimila koma zikhala bwino

  • @RashidSaid-lk6bb
    @RashidSaid-lk6bb 18 днів тому

    MCP ikufuna kuzabela ma vote chifukwa sizidachitikepo ku voter without ID ngakhale kuno ku South Africa

  • @OmegaNjati
    @OmegaNjati 18 днів тому

    Ambuye nditengeni

  • @mbewemisoyaanenenji1908
    @mbewemisoyaanenenji1908 18 днів тому

    Boooon Kalindo , Pangolin mwana womvuta kwambiri

  • @RashidSaid-lk6bb
    @RashidSaid-lk6bb 18 днів тому

    Uchitsilu ndiye umeneo
    Sizidachitikepo

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 18 днів тому

    Kkkk Boma amalawi kutifinya tiwona zinthu shop chaine chasala ndi maepute katoni okhaokha ndatawira kunnjenga ndiyemukulesa mukufuna kundipha chani mukandiphera kuzenje komweko 😮😮😮😮

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 19 днів тому +1

    Koma mpaka chenga mmmm mawonjeza

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x 18 днів тому

    Ife dzuro timadikira mademo, agalu amenewa atitopesa

  • @HawardStainly
    @HawardStainly 18 днів тому

    Akubwila fodya wamagogo wakuzino uja,(maganga).

  • @user-hb1ll8lj3v
    @user-hb1ll8lj3v 18 днів тому

    Gwenembe ND sikisinje yemweyo 😂😂😂😂

  • @OsmanBakali-s5x
    @OsmanBakali-s5x 19 днів тому

    Where are we going to make our hustle now😭😭😭 mpakana nchenga omweu tkatenge chilolezo? 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @MarkinaJohn
    @MarkinaJohn 19 днів тому

    Kkkkkkk koma DC kkkkk gwenembe

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 18 днів тому

    Ndizisilu zaathu zathu ananyerapo chenga iyewo chakwera

  • @MouriceChimkondo
    @MouriceChimkondo 18 днів тому

    Following boss

  • @loycemmadi9303
    @loycemmadi9303 19 днів тому

    And it's the song for me😂😂😂😂Winiko Ayi ndithu

  • @texonkautera
    @texonkautera 18 днів тому

    Anthu amene amabweresa Mbatata Ku nsika wa Limbe Ku chokers Ku Mulanje akuzunzidwa kwambiri akafika kuti asise a Police akuchosa misonkho akuti alakwa akalipire. K20 Pamene anthu akupangira mavuto mafuta anadula Palibe chomwe akupindula

  • @LamseyChimah
    @LamseyChimah 19 днів тому

  • @LoveBanda-sw1nu
    @LoveBanda-sw1nu 19 днів тому

    😅😅😅😅kumalawi mkokoma ndithu bwanawa akutiposa zochita

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 18 днів тому

    Koma funso nkumati kuti,
    Kodi Chakwela ndi Zikhale wacheyo, samachita manyazi konse akamamva izi? kapena umunthu wanu unatha??
    The DC tell them shit

  • @happychimwemwe-1805
    @happychimwemwe-1805 19 днів тому +1

    Umakwana booooon kalindo

  • @mlimolubanda6348
    @mlimolubanda6348 18 днів тому

    The DC .....

  • @TutuAlfred-y2l
    @TutuAlfred-y2l 18 днів тому

    😂😂😂😂😂. Zosatheka sizidzatheka nanga chenga ndichani uyo wasala pang'no kt amfe ameneyo chisilu chamunthuyo muuze ambere Ku muloza border kuno aone kt angatile ife kuvuula chenga.

  • @annamazingashaibuh6276
    @annamazingashaibuh6276 19 днів тому

    Uyu ndi nyoooo kwa nyooo ulemu wanu aaaa mchenga athu anayambira kale za mchenga athu amadyera momo abale eishh sambi

  • @BatsonKadzuwa-tl3rp
    @BatsonKadzuwa-tl3rp 18 днів тому

    Zoonadi mboni ndineyo nditachita ngoz ku Queens ndinalipira kut andithandize

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa 19 днів тому

    A born kalindo mukadikira opposition kuti itisogolere tichedwa inuo tayambisani ife tili mbuyomo

  • @JaxyKumwenda
    @JaxyKumwenda 18 днів тому

    Tikufuna mademo bwana osamunyengerera Chakwera

  • @InnocentBanda-g6i
    @InnocentBanda-g6i 18 днів тому

    ❤❤

  • @Vascomw
    @Vascomw 18 днів тому

    Ndipo live eeee a police eeee akuwo jeza

  • @Sugerman-tw4do
    @Sugerman-tw4do 17 днів тому

    Big Bos DC mumakwa

  • @IvieMwabile
    @IvieMwabile 18 днів тому

    Akufuna kutimpha agalu amenewa.go deeper

  • @loycemmadi9303
    @loycemmadi9303 19 днів тому

    Mr kalindo munafika aaaah kukanapezeka ambiri ngati inu bwezi dzikoli titaona zina aaaah

  • @dinahmunthali5324
    @dinahmunthali5324 18 днів тому

    Ine nyimbo ndi zomwe zimandi waza koophya ati Sikusinja ndi Gwenembe amkaimba agogo awake DC popita ku Mzuzu akudutsa mu chikangawa 😂😂😂😂😂 DC makina 😂😂

  • @ChikumbutsoTsalangu
    @ChikumbutsoTsalangu 19 днів тому +1

    Ati pedza madzi mu tikuvula chenga tikhapanamo

  • @jameskamanga628
    @jameskamanga628 17 днів тому

    Koma mkulu uyu kkkkkkkk sikusinja sikusinja kkk

  • @densonchiwaya8439
    @densonchiwaya8439 18 днів тому

    Mau awaa sikalindoo

  • @duncainjimmy
    @duncainjimmy 19 днів тому

    Mulungu adalenda dothi osati Chakwera ai

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w 18 днів тому

    We only need solutions not only kulalika

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 19 днів тому

    Mafumu aku ntcheu mtima wawo ukuwawa alibe dyera ndi mafumu odziwa kulira moyo wa munthu sizocheza

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 19 днів тому

    Ng'alula DC

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni 18 днів тому

    Njira ya ld pokavota sitikavota nkhondo ichitike ichitike

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 19 днів тому

    Kodi a Pule alibe olo foni ya mmanja kuti azitha kuona zomwe anthu akukamba online incase samadziwa zomwe nduna zake zikugwilira ntchito.What kind of leadership is this.

  • @ChondezVick
    @ChondezVick 19 днів тому

    The DC himself 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @azunguauskay4903
    @azunguauskay4903 18 днів тому

    😂😂 Akalindo nyimboyo ndayikonda

  • @MartinsKhumalo
    @MartinsKhumalo 19 днів тому

    ❤❤❤ ndimakunyadilani 👏👏

  • @ErnestAllex
    @ErnestAllex 19 днів тому

    Ku opposition kuli mbuzi zokhazokha ,munthu anali yemwe uja atiphela uja bas😢😢

  • @LinoMatchado
    @LinoMatchado 19 днів тому

    Iyayi na ya mchenga yokhayo boma likunena zoona chifukwa mchenga is in the group of minerals and any mineral is a government property which is minored through the government permission. Everywhere in the world illegal mining is prohibited citizens are allowed to collect sand ndi wilibala basi not with a thipa truck then you have to go face the law which is in the constitution every country.

  • @JamesKambale-s2c
    @JamesKambale-s2c 18 днів тому

    Koditu uku mcp kwangokula mbuzi za anthu

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t 19 днів тому

    Zoona aliyense akavote opanda cha unzika basi nanga izizo nchilungamo

  • @user-qc7qg4cy6k
    @user-qc7qg4cy6k 19 днів тому

    Totally agree the dc

  • @user-sv5yi9gt4u
    @user-sv5yi9gt4u 19 днів тому

    Zoona Born Kalindo auzeni ife tikuvutika kwambirii pa msewu kuno ku Kasungu chamama

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 19 днів тому

    Ndiye zaonjedzatu mpaka kuletsa mchenga????

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 19 днів тому

    Osakhala presdent bwanji abon kalindo
    Tayambitsani chipani cha amphawi

  • @PatronChanza
    @PatronChanza 19 днів тому

    The DC 😂😂😂
    😂😂😂

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 18 днів тому

    Koma inuu!! Ayi zikomo.

  • @christophermukaka7403
    @christophermukaka7403 19 днів тому

    Kalindo ndisaname mukuwatsegula anthu koma bvuto opposition ili weak

  • @KnowledgecGodwin-xo4pw
    @KnowledgecGodwin-xo4pw 19 днів тому

    Mumatimilira mr president

  • @BillyMhone-jp3kn
    @BillyMhone-jp3kn 19 днів тому

    We are in a Failed State and Chakwera uyuu achoke

  • @IsraelMtawali
    @IsraelMtawali 18 днів тому

    Chakwera is apus must go

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 19 днів тому

    The DC boooooon kalindoooooooo

  • @ZainuluNsalule
    @ZainuluNsalule 18 днів тому

    Good

  • @chipilirokalison1334
    @chipilirokalison1334 19 днів тому

    Denkha Born mulungu azikudalisani koma opposition yadekha ndicholinga usadande iwe mulungu azikudalisa

  • @KnowledgecGodwin-xo4pw
    @KnowledgecGodwin-xo4pw 19 днів тому

    Mulungu wanthu ndiwamoyo
    Sagona ndipo saodzela
    Ndithu chakwela alandila mphoto yake monga mwa ntchito zake zokupha wanthu osalakwa.

  • @stanfordnsona
    @stanfordnsona 18 днів тому

    Kalindo umatitsekula maso

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 19 днів тому

    Ndipo zoonadi chonsecho sanapangile anthuwo chochita