Atuma apolisi kuti athane ndi opposition & social media

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 17 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 758

  • @mosesphakamisa5406
    @mosesphakamisa5406 2 місяці тому +19

    The Best TV in Malawi 🇲🇼.... BMTV Bringing yout the hidden secrets, Historian 100%

  • @kidaadams
    @kidaadams 2 місяці тому +47

    Koma anthu zinthuzi mumazitengela chibwana, ngati Dziko this is an alarm to wake us up

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 2 місяці тому +1

      Ndipo live zimafunika tikamva chonchi tizichitapo kathu, koma vuto ndi apolice ndi a army coz ndiomwe akugwirisidwa ntchtooo

    • @Mtonga-m9b
      @Mtonga-m9b 2 місяці тому

      You are right.... Koma basi kaya mkutani? Tonse tikumamvera daily koma basi kaya ozindikira ndi ophunzira akutani kaya

    • @SaidyKamala-jj7lo
      @SaidyKamala-jj7lo 2 місяці тому +1

      Kk😂😂 guys mpaka gondolosi ayii chakwela asowe guys bola tivotele bakili muluzi tv 😂

  • @ganizankabango
    @ganizankabango 2 місяці тому +122

    BAKILI MULUZ TV FANS LET'S GATHER HERE

  • @VictorCustom-my1nv
    @VictorCustom-my1nv 2 місяці тому

    Akamuna

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 2 місяці тому +7

    God is using you in our generation to bring light to the blind.
    May good Lord keep protecting you

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 2 місяці тому +42

    Inuyo man ndinu machine mumadziwa zisisi za zitsilu izi 💪💪

    • @jonathanphiri-t2i
      @jonathanphiri-t2i 2 місяці тому

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @JafaliChiwimbi
      @JafaliChiwimbi 2 місяці тому

      Kkkkkkk ❤❤❤

    • @PaulKagona
      @PaulKagona 2 місяці тому

      Osamachemerera zopusa

    • @usherjamson174
      @usherjamson174 2 місяці тому

      @@PaulKagona poti kupusa umakuona iweyo ukakhala opusa oyamba

    • @BlessingsBanda-ih4th
      @BlessingsBanda-ih4th 2 місяці тому

      ​@@PaulKagona zopusa zimeme ukuyankhula iwe zapamutu ziiiiiii😂😂😂😂😂

  • @VINCENTKADZINJA
    @VINCENTKADZINJA 2 місяці тому +20

    Ulemu wanu amwene koma muzihala utali kuti asazakupezeni timakufilani💪💪💪

    • @lovemoremandala7420
      @lovemoremandala7420 2 місяці тому +1

      😂 ndiye mwati anadya gondolosi

    • @StevoZimba
      @StevoZimba 2 місяці тому +1

      😅😅😅😅😂😂😂😂​@@lovemoremandala7420

  • @mustapherallie6448
    @mustapherallie6448 2 місяці тому +28

    Kunena moopa mulungu nkuluyu amalawife akutifela akusakidwa koma akutiuzabe chilungamo guys lets vote mwanzelu

  • @JamesKhudze
    @JamesKhudze 2 місяці тому +23

    Now ndkugona ndimadkra munthu wamkulu ❤❤❤❤

    • @BrianMuleke
      @BrianMuleke 2 місяці тому

      Muzibwera daily umakwana

  • @NtloniphoNodimbaza
    @NtloniphoNodimbaza 2 місяці тому +1

    Abisala mmbatata koma mmtsana ukuoneka osawasiya akubawo We love you Mmtola mkhani wathu nambala wani ku Malawi komanso to the World

  • @JEVICO-MW
    @JEVICO-MW 2 місяці тому +2

    Kuba,kupha ndi kuononga😆🙌 ndilibe lawyer ine

  • @Sleemsteri
    @Sleemsteri 2 місяці тому +5

    A man with a flowery speech without action

    • @AlgentChilanga
      @AlgentChilanga 2 місяці тому

      Yes that's Mr chikangawa Mr chifunga kapena Kain kkkkk

  • @JOELMoyo-m6u
    @JOELMoyo-m6u 2 місяці тому +17

    Kkkkkkkk malume ajatu kuno aing'alura eeee saopa ayiiii

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 2 місяці тому +1

    Bakili Muluzi timangokumbukila nthawi yomwe tinkamvera sewero la John chilembwe pa radio.now panopa ukaiona msanga umakhala number 1 kutumizila azinzako kut naonso amvere news ya bakili muluzi.coz he is real not even the comedy.coz mwatsegula Mitu ya anthu ochulika.May the good Lord protect and comforting you with the blood of Jesus where ever you are ❤

  • @sahasalanje4786
    @sahasalanje4786 2 місяці тому +5

    Umatiimirira chabwino kumalawi kuno kuli maluzi but tikanvera zomwe umatibweresera timazaona ngati tikupasidwa ndarama usazasiye bro GOD bless you

  • @rightlombe380
    @rightlombe380 2 місяці тому +43

    Anakomoka ndi agness ku room 😂😂😂 chipongwetu

  • @OFG-th3st
    @OFG-th3st 2 місяці тому +18

    Agnes kukomoketsa wapolisi😂😂
    Komatu a Agi mwayaka moto😂😂😢

  • @ShadyDaHustler
    @ShadyDaHustler 2 місяці тому +6

    Much respect bro ❤❤watching from Nigeria, Lagos

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 2 місяці тому +4

    Akulu a kulu apa sipakufunikaso kumusiyira mulungu ayi,,,,, mulungu mbari yake akuchita daily koma tatiyeni monga ife nzika titengepo gawo pochita ziwonesero kusonyeza Kuti tanyasidwa nazo akupangazi osamangoyamikira wa muluzi tv daily achina big up koma ku ma demo ndikuzakhala nde tapanga chani apopo

    • @stevemtambalika
      @stevemtambalika 2 місяці тому

      Zoonadi Mulungu do amathandiza olimbika so ifeyo tangokhala chete mmal

  • @NoohNowa
    @NoohNowa 2 місяці тому +2

    Anakomoka ndi ageeness kubedi ndiye angathane ndi Ife 😂😂😂😂😂❤❤

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 місяці тому +1

    Yomweyo our president of information l salute kudya gondolosi ndikukakomoka achepa nanu bigy sangakupezeni akuzinamiza kwabasi kkk

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 2 місяці тому

    We have been waiting for this continue to give us the best analysis of what is happening around the world

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 2 місяці тому

    Akomoka bwanji ku room atatafuna gondolosi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 yomweyoooo chigangawa, we love bakili muluzi TV ❤

  • @P.Bilali
    @P.Bilali 2 місяці тому

    Bakili Muluzi TV... asazafe.... U keep us updated and mwina zina zimakanika kuti zitike poopa kuti uying'alula

  • @InnocyLee
    @InnocyLee 2 місяці тому +5

    Koma inuyo you are brotherhood best tv in Malawi

  • @SannyChifambi
    @SannyChifambi 2 місяці тому +1

    Keep good work of inspiring the nation

  • @lingsonmitunda293
    @lingsonmitunda293 2 місяці тому +3

    Maso ndi makutu za dziko la Malawi.
    Thank you BMTV.

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 місяці тому +1

    You're the best thank you for Good job

  • @MathewsMafaiti
    @MathewsMafaiti 2 місяці тому

    Keep it up my boss matimilira big man ✊✊

  • @LamieTiger
    @LamieTiger 2 місяці тому +4

    Achoke chakwera we don't want him anymore

  • @Laurent-h9u
    @Laurent-h9u 2 місяці тому

    Thank you so much for updating us as Malawian wake up 😢😢😢

  • @MrBanda-w6o
    @MrBanda-w6o 2 місяці тому +9

    Uncle osaopa mulungu Ali mbali yanu amatetenza anthu ake inuyo ndiwosakhidwa😊❤❤❤

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 2 місяці тому

    Tell us more and more, chakwera ndichitsilu mbolo yamake !!

  • @OusmanDavie
    @OusmanDavie 2 місяці тому +6

    VUTO malawi kugona Hrdc. Pac onse ndi agaru awa anagulidwa

  • @philipoga2401
    @philipoga2401 2 місяці тому

    silute fadah much love asakufuna asiye iwe ndi wathu wathu bakili muluzi tv machine amphepo

  • @PeterMoloko-lr3wq
    @PeterMoloko-lr3wq 2 місяці тому

    Kkkk and I quote 'anadya gondolosi mkukakumana ndi hule ku lodge kumenya round imodzi mkukomoka'.......

  • @Benson-cf6qd
    @Benson-cf6qd 2 місяці тому

    😅....mpaka kukomoka chifukwa cha Agnes 😊😊

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 місяці тому

    😂😂😂😂 koma big inuyo mumatha❤❤❤ just stay alert please

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds 2 місяці тому +1

    Iponden fadah , kukomoka ku room ndi Agnes Sha😮

  • @MadaBuleya
    @MadaBuleya 2 місяці тому

    Chilima may your soul continue resting in peace.dziko pano ndimasanje

  • @MohammadShek-u4k
    @MohammadShek-u4k 2 місяці тому +8

    Akuluwa amakamba chilungamo chifukwa sikanakala zonama bwesi asqkusakidwa komano kusakidwako akuwaulula somwe akupa zonama bwesi akuti ndiwamisala komano sangamukwanise ndipo tikumufunira wabwino sonse

    • @watchman731
      @watchman731 2 місяці тому

      Exactly....sangakhale busy kumamusaka had it been kuti sakunena chilungamo , ndekuti chilipo...

  • @DavieNhlane
    @DavieNhlane 2 місяці тому

    Koma man inuyo mmmm .unadziwa bwanj zot akuluwa anakomoka atamenya round imodzi 😂😂😂😂😂.thats why i always say that you are speaking from heaven

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому

    Agness, chonde chepetsa kunyekhulira mbolo. Usaphe apolisi ambiri. Chepetsa kunyekhulira mbolo agi.

  • @GiftMlinde
    @GiftMlinde 2 місяці тому

    Iweee ndikatunduuu GOD protecttt u

  • @AyandaPhungula-bg9ql
    @AyandaPhungula-bg9ql 2 місяці тому

    The best and truth TV ❣️ mumatiyimilira big

  • @MussahNamalomba-e3p
    @MussahNamalomba-e3p 2 місяці тому

    Ndiye mwati anakomoka ndiimozdi😂 eeee koma Agnes 😊😂

  • @REECEMw-o9s
    @REECEMw-o9s 2 місяці тому

    ❤❤❤❤❤ bakili muluzi TV ndiozindikila kuposa chewa ameneyi

  • @user-Grant260
    @user-Grant260 2 місяці тому +1

    Much respect elder ❤❤watching from Venezuela in Caracas

  • @manzyhetekele8697
    @manzyhetekele8697 2 місяці тому

    Keep it up brother 💪 we love your work 👏 😊

  • @gifahumphrex2454
    @gifahumphrex2454 2 місяці тому

    Our best Chanel ❤

  • @MilitaryYusuf
    @MilitaryYusuf 2 місяці тому

    Respect to u .history is a best teacher

  • @KassoCompany
    @KassoCompany 2 місяці тому +1

    Being first to watch!!!!❤❤ Ndipaseni udindo bwana bakili muluzi tv😂😂

  • @JacksonMoyo-tm8dv
    @JacksonMoyo-tm8dv 2 місяці тому

    Father of history like herodotus, you are the one

  • @khambisan
    @khambisan 2 місяці тому

    Kkkkkk now its time to open a eyes thi is true massage 💪💪💪💪💪

  • @DimoraMvalo
    @DimoraMvalo 2 місяці тому

    Koma inuyo big ndi number 1 ❤❤ ndimakunyadilani heavy

  • @JasperKaleni-dx6nn
    @JasperKaleni-dx6nn 2 місяці тому

    Ife sitingakusiye wekha ❤❤best tv

  • @MichaelJannah-hn9qv
    @MichaelJannah-hn9qv 2 місяці тому

    God bless you Bakili muludzi tv

  • @livinesspasseli5044
    @livinesspasseli5044 2 місяці тому

    Kkkkkkk apa ndye mamalidza machedza bosss
    Mpaka kukomoka ndi gondolosss for 3 days kkkk

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 2 місяці тому

    Iweyo umaziwa history ndithu ndikuhala Khani bwino aaaa maulemu ako basi Allah guide u

  • @emmanuelkampira6950
    @emmanuelkampira6950 2 місяці тому +1

    ❤❤❤ it's our prayer for you to be safe always. 👑

  • @jonathanphiri-t2i
    @jonathanphiri-t2i 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂😂Anakomoka ndi Agness koma Agnes ai zikomo kkkkkkkkk 🤣🤣

  • @JosephSamson-g1h
    @JosephSamson-g1h 2 місяці тому

    Popanda inu ife tili m'mazi bro kept up🙏🙏

  • @idrisshtambala
    @idrisshtambala 2 місяці тому

    Koma iweyo umakwana ❤❤❤ndiwewachikondi chodzadza usazasiye timakhala ndithawi yokuvetsela ndipo timakudalilakwambili

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 2 місяці тому +10

    Malawi Chikangawa Party out in the name of Jesus. Ndipo mademo mwezi unowo tinyetetsa zedi pa 31

  • @PeterLemani-jk3mw
    @PeterLemani-jk3mw 2 місяці тому +2

    You're the best tv in the world

  • @AustinYusuf-do4vz
    @AustinYusuf-do4vz 2 місяці тому

    😅😅😅😅😅 ati ngati anakumoka ndi agines kuli bwanji Bakili mulunzi TV Kkkkk kkkkk 😂😂

  • @mayesoedisonmatama86
    @mayesoedisonmatama86 2 місяці тому +1

    Inuyo big ulemu wanu, mumasata zinsisi zonse za dziko lathuli, may God protect you always, boma la mcp ndi la nkhanza koopsa

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 2 місяці тому +1

    You and Kalindo are the only heros we have in Malawi

  • @mikemakamo7360
    @mikemakamo7360 2 місяці тому

    One round fent 😂😂😂 sangamake ndimafana amenewa.
    Big up BM TV 📺

  • @Anthonymendos
    @Anthonymendos 2 місяці тому

    Ilove you bakili muluzi TV, you is One

  • @PatriceKaomba
    @PatriceKaomba 2 місяці тому

    God bless you mulungu akupatseni zosowazanu mudzina la yesu

  • @thokoayami6934
    @thokoayami6934 2 місяці тому

    Ife tizapanga ma demo akazakugwirani, much respect to you brother

  • @Gorilla-k8e
    @Gorilla-k8e 2 місяці тому

    Munthu wa mkulu kwambili bakili muludzi tv big up big bro

  • @EmmanuelZiba-qz6ug
    @EmmanuelZiba-qz6ug 2 місяці тому

    l love you from Lusaka Zambia 🇿🇲🇿🇲 kucharo

  • @Addih_calyx_music
    @Addih_calyx_music 2 місяці тому

    😂😂😂TELL DEM .FIRE BURNING #bakili TV to di world

  • @Justin_Nano
    @Justin_Nano 2 місяці тому

    Best TV❤❤much love

  • @matembamadadada8291
    @matembamadadada8291 2 місяці тому +3

    Respect captain love you to much 🎉🎉🎉

  • @ulemuchisale
    @ulemuchisale 2 місяці тому

    History is the best teacher

  • @uzaleuzale8603
    @uzaleuzale8603 2 місяці тому +1

    Pakufunika game kuyiwonera patali mapeto ake bomali kuti lidzalamulireso tidzakukuta mano that's why I love bakili muluzi tv every day

  • @MuhammadInack
    @MuhammadInack 2 місяці тому

    Kkkkkkkk Agnes ayi zikomo🙌🙌🙌🙌

  • @FisherAction
    @FisherAction 2 місяці тому

    God bless you big man keep it up

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 2 місяці тому

    We love you our own brother be safe wherever you are,

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 місяці тому

    The only number 1 TV station ❤❤❤❤

  • @giftjamali8204
    @giftjamali8204 2 місяці тому

    Kkkkkk inuyo ndi katundu boss eee tataya kantengooo boss mwawiba basiiii

  • @Dee-h7c
    @Dee-h7c 2 місяці тому

    LONG LIVE BAKILI MULUZI TV 🎉🎉🎉🎉

  • @Deajay-jn8cf
    @Deajay-jn8cf 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂Koma adah iweyo aaaah kayaa😂😂😂😂😅😅

  • @AnnaPhiri-b8t
    @AnnaPhiri-b8t 2 місяці тому +1

    Mr chikangawa akuzimvera

  • @JoshuaNamauti-py4up
    @JoshuaNamauti-py4up 2 місяці тому

    Kwambil big man inuy ndinuyo bc mumakwanila guy's tiyen tivote bwino bwino good night timadikila imeneyi❤❤

  • @joshuamasulani1190
    @joshuamasulani1190 2 місяці тому

    Am just thinking during voting period muzinanena komwe akubera

  • @OZIELBLESSINGS
    @OZIELBLESSINGS 2 місяці тому

    much proud of you sir🎉❤

  • @stevemtambalika
    @stevemtambalika 2 місяці тому

    Koma chikangawayu eshhh see you 2025,bakili TV morefire and be strong

  • @jerryl.chadziwika8527
    @jerryl.chadziwika8527 2 місяці тому

    Following from Libya

  • @hopembendela
    @hopembendela 2 місяці тому

    You are are the number one bro

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 місяці тому

    Anthu wa kuasekerera ationongera dziko li ndithutu mmm zomvesa chisoni kwambiri esh

  • @JOELMoyo-m6u
    @JOELMoyo-m6u 2 місяці тому +4

    Mumankhala malume you are number one

  • @innocentmabedi3850
    @innocentmabedi3850 2 місяці тому

    Apapa ndigonano, bravo BM tv

  • @johnkatapeh7182
    @johnkatapeh7182 2 місяці тому

    Tilibe chisisi pa dziko lapansi........❤❤❤❤❤❤bakili tv

  • @AffickChaona
    @AffickChaona 2 місяці тому

    Best TV in Malawi bakiri Muluzi TV ❤❤

  • @Prodbysix40
    @Prodbysix40 2 місяці тому

    2:59 u killed me 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉

  • @StevoZimba
    @StevoZimba 2 місяці тому

    Voice to the voiceless😊