Mima ikhile _Uyuyu (Official Video)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 лют 2025
  • Mima ikhile #newmusic #uyuyu
    Lyrics
    A know you struggling
    You tired
    Funa kusiya ma addictions
    You got no power
    No matter how you try
    Umapezeka pompaja
    Now you frustrated
    You thinking zogiva
    Tamverano
    Nane nnagweramo
    Ndipo zimawoneka za normal
    Koma at the end of the day
    Umazimvabe opelewera
    Kuyesa kusiya komano ayi
    Nde ukuvutikilanji
    Wayesa anthuwa
    Pawekha suli sure
    Kodi umamudziwa yesu nnazareni?
    Oh zosatheka
    Palibe amabwera kwa yesu
    Kubwera kwa yesu
    Ndikukhala the same
    Zomwe ndidziwa ine ndidziwa ine
    Ndi Uyuyu
    Ndunena Uyuyu
    Yesu wake Uyuyu
    Ndunena Uyuyu
    Ndiwa moyo Uyuyu
    Ndunena Uyuyu
    Amamasura Uyuyu uyuyu
    Azakutulutsa nsinga zako wamva
    Depression nkachani
    Ma stress za chani
    Wankati kumkhudza
    Kumukonza-koza
    Kumpatsa za nyowani
    Chiyambi cha moyo wina
    Bwerani bwerani kwa iye
    Invitation
    Olema ndi othodwa
    Azakupatsani ntendere
    Oposa omwe musaka mdzikoli
    Tangoziyiwala wekha
    Musiyile mbuye dekha
    Oh zosatheka
    Palibe amabwera kwa yesu
    Kubwera kwa yesu
    Ndikukhala the same
    Zomwe ndidziwa ine ndidziwa ine
    Ndi Uyuyu
    Ndunena Uyuyu
    Yesu wake Uyuyu
    Ndunena Uyuyu
    Ndiwa moyo Uyuyu
    Ndunena Uyuyu
    Amamasura Uyuyu uyuyu.
    Stream Download And Share.
    Audio Produced By King Duda
    Video Shot By Middle
    #malawi #afrobeat #africa
    UYUYU

КОМЕНТАРІ • 23