Church changa chija maiwe mmmmh mpaka kumalowa mu Church ndi Wig ma wiv meshi make up aaaaaaa SDA inali dzana osati lero ai mmm zikomo Satana wakutengani basi ndimakumbuka ulaliki wa A Twaibu ndithu 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
A SDA anzanga mwayamba kutaya chikhulupiliro pa maso pa mulungu mungamulole zowona Michael Usi munthu okuphayo mkubephezera kachisi wake wayehova zowona? Mzimu WA Chilima umukhanthe Michael Usi asatiipisile SDA
God bless Mr Usi to do your will.
Koma uyuyu uyu, Wayamba bwino Izizi bcoz this can be true definition of working hard.
Kukukopani kumeneko Kut azadyeso ndalama zanu
Iii akutumidwatu uyu akufuna akufoiliseni
Akufunadi kufoilisa anthu
God bless you all Amen
Thank you mr VP
A Chilima komwe muliko rest in peace. Simmalengezetsa mkamapita Ku church ndipo zoti Pena mmakolopa taziona mtamwalira keep on resting former VP
😂😂😂😂Zoona zake amati pothandiza pangani zoti dzala la manzere lisaone
This is very good
Km zoona mwana wangono kuyimba nyimbo komaso kupempela pakuluakulu😅
Happy Sabbath day a VP
I can see my grandmother Nyamalopa and her daughter from Hewe. Miss them
Happy sabathday my vice president all the best
Nice one VIP
This is gud VIP. Malawi needs a true Godly leader.
Usi pitiliza kugwira ntchito ya malemu Chilima ause muntendele ena abesa chipani chathu kamba kakusapilila
😂😂😂Koma ndiye akuyenda 😅😅😅😅😅guys vp whats going on
Church changa chija maiwe mmmmh mpaka kumalowa mu Church ndi Wig ma wiv meshi make up aaaaaaa SDA inali dzana osati lero ai mmm zikomo Satana wakutengani basi ndimakumbuka ulaliki wa A Twaibu ndithu 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
😂😂😂 inu paja ndamene mukalowatu kumwamba matelo aSDA enafe tutsala 😂😂😂 tikaonana komko osunga sabata mawingi alikumutu
Musaweruze kuopa mungazaweruzidwe,Tisaipise mpingo,Anthu tmapanga tokha chisankho ngakhale choenera kucita Baibulo imatiuza.
But anzake aja bwana SKC samalengezesa amapita every Sunday ku Lilongwe pa 18 parish osayitanisa a media mwakachete chete
Mwati mupeze chifukwa basi vuto chani pamenepa
Mwana kusogolera nyimbo ( Chikondi Chikondesa) zamanyazi koma Michael Usi ngat Ali ndichikondi munthu okuphayo alibe manyadzi Michael Usi koma
Koma kuyenda kumeneko misonkho yathu ilimbaa???
Koam ndipo waonjeza bwanji?
😂😂😂😂Koma ndiye akuyenda eeeeee abwana😅
Paja mau a Mulungu amati chimene nkono wamanja uchita nkono wa mazere usawone mmmmm Usi mwachita chani apa Ambuye akukhlulukireni ndithu
A usi tavonani ngati momwe mumavinira muja mumandiwaza
Amen
Miko usi sayenda ndi akaziake bwanji ndionyasa kodi
Ambiriwa ndi nsanje koma vip mukuyesesa kwambiri
Convoy yoseyi aaaaaaaa koma zinazi eti mukutiwonongera ndalama ndithu
Eeeesh no madam ndiku church komwe
Good
Kodi leronso a boma amagwira tchito or izi ndi za mpingo?
Kodi chomwe akuyendera choncho ndi chani? Zayamba kuonjezatu
Please musamsike sound yomwe imamveka pansiyo
❤
Mulungu atitsogolere mipesa tonse.
A SDA anzanga mwayamba kutaya chikhulupiliro pa maso pa mulungu mungamulole zowona Michael Usi munthu okuphayo mkubephezera kachisi wake wayehova zowona? Mzimu WA Chilima umukhanthe Michael Usi asatiipisile SDA
😂😂😂😂koma usi iwe umuziwe yesu ni ophuziraake
Muzitenge bwino ausi
Asilikali alikuti sthu ena samukufunilsn zabwino
Chifukwa chiyani anthu mukupembedza mafano? Kodi mulibe maso kuti mungawone fano? Munthu amene amayenda ndi Mulungu amadziwa chilungamo
Masiku omwewa avp anenepatu mpandou ngonona eti
😂koma mukuyenda
Eti dairy panseu ngati ndivenda mzathusotu kk allowance
Km zilibhoo
Kanyimbo/ instrumental kapansipo irritating kachotsedwe
Kojambula comedy 😂😂
The guy is trying
Amalawi khalidwe lasowa ndipo ndikuganiza boma lizimanga anthu omwe akutukwana m'ma social media.
Munthu aziweruze
Paja achakwelaso anali munthu wamulungutu
Kkkkl 😅
Amen
Amen