UTM KU MANGOCHI 17 August 2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 26

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 25 днів тому +4

    Hard to believe that you have gone for good my president 😢😢 you have made me to vote in 2019 your manifesto like magnet attracted me to a voting station 😢😢May your soul rest in peace💔

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 25 днів тому +3

    Chilima wanga , palibe yemwe azakwanilitse kupanga zomwe iyu amaganiza 😭😭😭

  • @OliverChimsewu
    @OliverChimsewu 25 днів тому +2

    Imphi BIYEN you have left the youth with many questions where by it needs answers.we will still remembering you for ever

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 25 днів тому +1

    You were a light to this nation now my president...Darkness has fallen into our nation 😢😢

  • @EnerstBanda-m4s
    @EnerstBanda-m4s 25 днів тому +3

    More fire Fredokiss mzimu wa Biyeni walowadi mwana iweyo osaopa osatopa osafooka UTM boma 2025

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 21 день тому

      Ndipo koopysatu..,akulu akulu akuopa koma mntchana uyu sakupanga nao zoopazo.,, keep up bro

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o 25 днів тому +2

    Utm my votes SKC forever in our hearts ❤❤❤❤❤❤

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 24 дні тому +1

    He was the dream of our forefathers. When will we see such leadership and passion for Country🇲🇼

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh 25 днів тому +2

    This guy was amazing guy in history as yoy can see chidwi chomwe anali nacho povetsera

  • @user-ln5hw7dn9g
    @user-ln5hw7dn9g 25 днів тому +2

    Ka mwana kolimba mtima continue ❤❤❤❤❤

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 25 днів тому +1

    Zoonadi ABWINO Samankhalitsa kunena Zoonadi this gentleman amalifunira dziko la Malawi Zabwino ( Continue rest in Well Imphi BIYENI💔)

  • @SoftwareSolutioz
    @SoftwareSolutioz 25 днів тому

    Usani muntendere weni weni waYehova aChilima ndi anzanu onse amene mudamwalira nawo pangozi yandege kuChikangawa pa 10 June 2024

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 24 дні тому

    Ndilekelenji ine kuvotera Utm ,,,SKC zowona munaferadi Malawi,,,,Tsoka kwa Iye anatenga mbali pa imfa yanu

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 25 днів тому

    Mulungu wathu kumwambako ife tilibe chonena zonse mukudziwa ndinu rest in peace BIYEN. Koma dzikoli abale inu ngati maloto ndithu munthu anapita ngati boza😭😭

  • @BenAbraham-z5u
    @BenAbraham-z5u 25 днів тому +1

    Munthu uyu adali oganiza bwino zomwe zidapangitsa anthu kuganiza mwakuya nowadays

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 25 днів тому

    Mzimu wanu Biyeni uwutse mu mtendere. Chikangawa ija imva nyunyunyu.

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli 25 днів тому

    Inalillah wainah illayihi ryajuuna mau anu bwana anali uthenga wabwino

  • @JamesMjathu-dg4ep
    @JamesMjathu-dg4ep 25 днів тому

    Mulungu akukhululukire iwe yemwe unatengapo gawo pa imfa ya Biyeni

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli 25 днів тому

    Chakwera iweyo mulungu akulipile zomwe unachita

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 25 днів тому

    Amalikonda dziko lino ndi anthu ake.

  • @user-di8hq3dl9o
    @user-di8hq3dl9o 25 днів тому

    My vote

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 25 днів тому +1

    ❤❤❤

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli 25 днів тому

    Machine ayine

  • @NorahMangasanja
    @NorahMangasanja 25 днів тому

    utm my vote

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 25 днів тому

    Utm anthu timayikonda koma atamwalira asog akaliyati angagulise chipani ku dpp aife tiwakonda achilima osati pang ono ayi

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o 24 дні тому

      @@VictoriaKumwenda-k6o wakuuza ndani zonwe ukuyankhula zo unamuvako Kaliati pa interview ija kuti wapanga chibale ndi chipani ifetu sitikupanga nawo ngati ndikuluza tiluze basi koma sitikupanga nawo za team nkhalamba utm my votes SKC forever in our hearts ❤️❤️❤️❤️