Comrade Ntanyiwa Pa Limpopo Fm Lelo Pa 2 Feb 2025 "Akufuna Ayambe Kugulitsa Ma ARV Muzipatala"

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 1 лют 2025

КОМЕНТАРІ • 41

  • @YamikaniYamikani
    @YamikaniYamikani 46 хвилин тому

    munasowa comrande ife tili bwino ndizoona simankhumudwitsa inuyo mr comrande🔥🔥💃💃💯

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 2 години тому +1

    Munasowatu a comrade ntanyiwa ine ndimadandaula kuti bwanji ,zakhala bwanji,Ambuye alemekezek ndava mau, anu, kuti muli safe. a ntanyiwa. History is best teacher ❤❤❤we love you comrade ntanyiwa

  • @GraceChikosa
    @GraceChikosa 5 годин тому +7

    Praise the Lord kuti Don't trust watuluka mchipatala Ndipo Mulungu apitilizekumukhudzandi dzanja lakela machilitso ..... Ndipo timakusowanidi boss comrade Mtanyiwa

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 6 годин тому +4

    Tinakusowani comrade kaya akupez. Bwanj don't trust?

  • @olivemkumba
    @olivemkumba 3 години тому

    Kwachaaaaa!eee kwachadi😅😅😅😅😅 Comrade Ntanyiwa of the most high🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 28 хвилин тому

    Ntanyiwa nnakusowani ine ndipo ndinadwara posamva mau Anu masiku anenewa

  • @JumaEriya
    @JumaEriya 59 хвилин тому

    Kuyambira Kare paribe tsiku rimodzi rimene athu anabwerera kuchipatara kuti ma maravi kuti atha paribe.ngati inzi nzayamba chonchi ndibwino kuti amene anene kuti bwererani ma Aravi kuribe ameneyoyo gwirani menyani.

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 2 години тому

    Welcome brother ntanyiwa

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 5 годин тому +1

    ❤❤❤❤

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 5 годин тому +2

    Osamasowa choncho mr ntanyiwa

  • @MariaMnkhondya
    @MariaMnkhondya 39 хвилин тому

    Hy

  • @AnnieZungu01
    @AnnieZungu01 2 години тому

    More fire brooo

  • @NdalamaDique
    @NdalamaDique 2 години тому

    Apule ufumu wanu wayesedwa ndipo mwalephera...
    Mwalephera muchilichonse.

  • @wayafrank2405
    @wayafrank2405 5 годин тому +1

    Koma ntanyiwa..😅😅😅😅😅 akuti kwachaaaaaaa

  • @ABRAHAMFRIGHTON
    @ABRAHAMFRIGHTON 5 годин тому +2

    Mulungu ndi wamkulu

  • @RuthChaola
    @RuthChaola 2 години тому

    Atanyiwa chipatala chimene mwatchulacho ku nsanje kuno kulibe gaga kapena ngabu koma ndi ku ck

  • @staindulamanja1218
    @staindulamanja1218 Годину тому

    Com mkudzafika

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 3 години тому

    Mtanyiwa woyeeeeeeeeee 🤣🤣🤣🤣🤣

  • @MisheckKamwendo-w9n
    @MisheckKamwendo-w9n 2 години тому

    Boma silomwelo akunama likuchoka limenero

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w Годину тому

    Mumatiyimilira.ntanyiwa

  • @AnthonyGondwe-b1t
    @AnthonyGondwe-b1t 5 годин тому +1

    Koma nkhangazi mpaka kusuzumila pafupi,! 😅😅😅

  • @MariaMnkhondya
    @MariaMnkhondya 37 хвилин тому

    Mumakwana amtanyiwa

  • @AbdullahMatolah
    @AbdullahMatolah 6 годин тому +3

    Musamasowe

  • @Alexchinangwa-k2q
    @Alexchinangwa-k2q 2 години тому

    mulungu ndi wankulu amakonda aliyes

  • @AllunaBenjamin
    @AllunaBenjamin 3 години тому

    Atenga ndalama imene akufunakungula mashin aukazitape akangule makhwala arv

  • @MaxwellChaminju
    @MaxwellChaminju 3 години тому

    Kma ndekukhala bzmes yotethatu 😂😂😂Tnx Kuti watuluka uyo ambuye apitilize kumuchiza padenipo

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 6 годин тому

    Yomweyo galu iwe Chikangawa party 😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂

  • @williamsobilika6255
    @williamsobilika6255 6 годин тому

    Amayi koto...!😢 Ili ndi Boma lobalalika zeeedi.

  • @AlicePondani
    @AlicePondani 6 годин тому

    PA ARV ndiye awonjeza kuiputa khondo plus black box jeee tiphanapono,,zaulere azigulisaso

  • @Rasheedissa-f3q
    @Rasheedissa-f3q 5 годин тому

    Abg munasowa nkwambilli mulungu asikupasan moyyo wabwinno ndawi yonse

  • @WilsonNedi-s6t
    @WilsonNedi-s6t 2 години тому

    Kwachera nyasi , zamanyazi

  • @BwanaliLabson
    @BwanaliLabson 3 години тому

    𝓬𝓱𝓲𝓴𝓪𝓷𝓰𝓪𝔀𝓪 𝓰𝓪𝓵𝓾 𝔂𝓪𝓶𝓾𝓽𝓱𝓾

  • @ChiefJustin-l5p
    @ChiefJustin-l5p 5 годин тому

    Akamati kwacha kwacha kwa zigololo😂

  • @GeofreyRhonard
    @GeofreyRhonard 5 годин тому

    Beansnes ndye ikuyendatu 😂😂😂

  • @SmartMailos
    @SmartMailos 2 години тому

    Mumaitha

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 3 години тому

    Ndinakusowa ntanyiwa

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o 6 годин тому

    😂😂😂😂 chigololo😂palipoze kkkkk

  • @AlicePondani
    @AlicePondani 6 годин тому

    Tinakusowani comrade

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d 4 години тому

    Wado wadooKkkkkkk

  • @Momweekly
    @Momweekly 3 години тому

    Achita bwino