Politicians In Malawi Learn to Tell the Truth Mukalephela - Samuel Lwara

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 вер 2024
  • In his latest audio Samuel Lwara pleads with Malawi politicians to learn to tell the truth when they have failed to lead the country.
    M'mawu ake aposachedwa a Samuel Lwara apempha andale ku Malawi kuti aphunzire kunena zoona pomwe alephera kutsogolera dziko.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 32

  • @JamesMalango
    @JamesMalango 2 місяці тому +5

    You're a great man with an idea

  • @LumbaniNeba
    @LumbaniNeba 2 місяці тому +3

    Powerful Mr Lwara

  • @user-fp5qn5ci2v
    @user-fp5qn5ci2v 2 місяці тому +1

    Zikomo munthu wanzeruwe Samuel Lwara I salute you bwana

  • @josephinemisomali6840
    @josephinemisomali6840 2 місяці тому +1

    Eish imfa ya Dr Chilima I kupweteka tsiku ndi tsiku mutu kumachitakupweteka Rlp

  • @chiefmalindi4070
    @chiefmalindi4070 2 місяці тому +2

    Another Born Kalindo's brother from another mom

  • @DavieMaloya
    @DavieMaloya 2 місяці тому

    Powerful massage

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 місяці тому +1

    Powerful talking

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 2 місяці тому +1

    Ndege inali yabwino bwino koma inali plan yoti aphe Chilima thats all!

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 місяці тому

    Powerful,Lwara ,you deserve respect

  • @ruthchikhoswe6028
    @ruthchikhoswe6028 2 місяці тому

    Powerful

  • @victormaluwa6710
    @victormaluwa6710 2 місяці тому

    Powerful indeed 💪

  • @blessingmanda
    @blessingmanda 2 місяці тому

    namuwongani dada chiuta wamutumbikani

  • @MartinMsimuko
    @MartinMsimuko 2 місяці тому

    Tikamanena wisdom ndi izi munthu uzivomereza zikavuta or uli pa position yotani accept ngati walephera

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i 2 місяці тому

    Where is osward jumani

  • @CaptainNyenga
    @CaptainNyenga 2 місяці тому

    Kweni unapamulomo😂😂

  • @sydneyngoma2356
    @sydneyngoma2356 2 місяці тому

    Where is Lyton Mangochi we miss him for his commitment to democracy

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 2 місяці тому

      Don't talk about laytin men!, we don't need to hear anything about dat stupid crocodile, I'm saying dis coz dat guy is a hypocrite and he don't deserve to be a freedom fighter

    • @meganabigail-ye7fw
      @meganabigail-ye7fw 2 місяці тому

      Lyton mangochi zakudya Kaye ndalama ndi azikhale, chambiko nda chikuni anatelo oyimba Ena

  • @emmanuelsoko87
    @emmanuelsoko87 2 місяці тому

    Malawi in not a lawless country,if you break the law,u will face the music.mukati asamange anthu nde likhala dziko? mkwiyo ochotsedwa mnyumba ya housing uwu😂

    • @petertaulo8014
      @petertaulo8014 2 місяці тому

      Yes is not lawless country but Mcp take law in their hands ✋. This is also democratic country Mcp must respect this too and we can not accept this nonsense of arrest innocent people!

  • @ebenezerkamanga6016
    @ebenezerkamanga6016 2 місяці тому

    Iwe lwara wabwera tsopano tikufuna anthu ngat inu

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Obwelesa mvula si azibusa ayu maan inuu, mvula amabwelesa ndi MULUNGU

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Akulu inu, wat's ur point?, ngat munalibe blackbox, chimayeza temperature mumlengalenga mchiyani?, nanga mafon awanthu anafa mundege aja munalibenso?, nanga chilima anakapezeka 200 metres away from the place were the plane wer crushed y?, why chilima anapezeka alibe zovala chikhalirecho anali mu suit, and y anapezeka ndi mabala akuluakulu azikwanje mumiyendo yake😢? , eish!,

    • @LeendaDeborah2005
      @LeendaDeborah2005 2 місяці тому +1

      Hmmm mulungu athandize ndithu. Kuyankhula yankhulaku kukubwera chifukwa cha mabodza omwe president amatiuza zokhudza za ndegezi. He knows the truth but God will expose him

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 2 місяці тому

      @@LeendaDeborah2005 data true , and they know wat they dd on dat day and the truth will review

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 2 місяці тому

    Ndikudabwa adada wachitumbuka uyu akutukwana mafumu anthu komaso zimene akuyankhula onse amene akutukwana pano ali ndi zifikwa zawo iwe ukukakamila kukhala mnyumba yaboma undamange nyumba yako kumzimba uko nyumba zikuntchipa basi mpaka nalelo nyumba mlibe mkatukwane mafumu chikwa cha ndale mbusa uyu nyo ngwakutangwanika chomene ndicho chifukwa wakakangama na mamembazi ake siwosankhidwa ndi mulungu ayi .

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому

    Anthu ena owona patali akusungila serial number ya black box yomwe inali mundege yomwe inapha chilima, nde iwe ukuti munalibe black box, stop confusing the pple

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 2 місяці тому

    Akatolika ndiwozindila not enanu

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h 2 місяці тому

    Adanena kale kuti mudalibe black box

  • @Elvin-dr8tv
    @Elvin-dr8tv 2 місяці тому

    Mtitole Makola 😂😅

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801 2 місяці тому

    Ngamo yonkha yonkha

  • @GoodsonLindani-gf8pn
    @GoodsonLindani-gf8pn 2 місяці тому

    Inuso ndiachitsilu papitapo zaka 4 chakwera akukwela yomweyo, bwanji ndege simagwa.lurwa nanuso point yanu siikuziwika mukuikila kumbuyo boma pena ayi,nde ndinu opepela kwambiri, bola kalindo amanena zomveka.