Joe Gwaladi - Chipepeso N'dyeretu
Вставка
- Опубліковано 2 бер 2013
- Enjoy! Send requests by commenting! Are you a musician and do you want to be published on this channel or do you have songs that should be on this UA-cam Channel? Send a message on our Facebook page which can be found here:
/ chichewaonlinemusic
Our email address can be found there too!
😂😂😂😂Koma Gwaladi ndioyimba wabwino zedi amakhala ndiuthenga komanso amavita bwino komanso ali ndi beat yake yake malawi yonse❤❤❤❤❤❤❤
Gwaladi, Duster namakwa, Nkassa, lucius, chimoto, katelele, chimoto, and..., Thanks very much
Joe Gwaladi umandiwaza kwambiri kuno ku Botswana ndingokumbukira kumudzi more fire you are original.
My fav song back in the days
Gwarad mukuyimba bho
big man Gwaladi kukamba nzeru zokhazokha 😂❤
Powerful message
Legendary Gwaladi inu ndi big
Nice Professor Joe Gwaladi❤❤❤
Keep up
Those days when I use to hustle in Lilongwe area 25
Am here coz of tiktok 😂
Aaaaaa🎉🎉🎉🎉
Gwaladi akufuna galimoto
Joe Gwaladi tsopano!! ndimaku3la zedi!!!ndine Harrison Moyenda kuno Ku Mphedzu..
You inspire me with all you songs ,am Solomon in Zambia
Pamaliro aine mukudya nyama kma ine ndamwalira ndi therere ,jo ukunena zoona
😂😂😂😂😂Ndizoonaditu Koma brother 😂😂
Professor joh gwaladi umantha
Your onlyone Joe
How to make sex
Kuyimba kwabwino wawawawawawawawa
malawi mwachoka kutali
Nthawi imeneyo asanamugulure mano😂😂
Hahahha yafika bwanji uku 🤣🤣🤣
that is true jo.
Substance! Muli uthenga umu
Polofesa 😂😂 A.K.A Tupac 😆😆
Koma ichi man😅😂😂😂😂
Gwaradi asala pang'ono kumulesa kuimba mumalawi
Iribho umandisagarasa kuno ku South Africa
Its true gwaladi
gwaladi wawawawaw
awuze gwaladi amenewo asiye zimeno
umaitha gwaladi
beston namala Joe ndimaku3la heavy undipase wtsp # yako
Aunthetic music
Gwaladi muyitaneni ku SouthBend 😂
I don't know if it's just the malawian beat which is difficult to dance to or they just fail to dance. I love the music
Kkkkkkk
Fail to dance
😂😂😂😂😂They didn't fail they tried 😂😂
Yes gwaladi Auze assaaaaaa!!!! lol
kkkkkk fact!!!
hie guys our videos are very poor we need to do something
If you are rich promote him
Kikkkk koma uyu
Gwalad mbamba
kulira maso ali pamphika wanyama ayi ndithu ...
madala gwaladi
wamisala iwe tapondyaso inu
Gwaradi ndi Gwaradi iye samanama kkkkk
help people when he'n she is arrive than buying expensive things when is died that true
Fact brother
aaaaaa joe
Mimu Weta blv
mbebe ...... eya
wamisala iwe zuziwa kuomba
kkkkkkk nice
Zoonadi 😂😂😂😂😂
AMAITHA
hahahahahah that's true tell them
Munthu wamkulu uyu hahahaha malingizo alipo apo
kkkkkkkkkkkkkk,koma yaa.
hajison yohane lawaaikamp
Tempos
Kkkkkkkkk
Nthaw imeney GIBO PEARSON Al kut??
apo ndafika kumlakho tikuiponda dansi