Munanyamula mbendera ya chilungamo ndi chifukwa mwapulumuka mulungu ali ku mbali yanu ankanakhala chimwendo zikhale kunkuyu ataoloka chifukwa alibe chisoni ndi dziko lathu akuvutika mulungu si Lazarus
EYA A GAMECHANGER MWAAKHULUKIRA AMANGAWA ANU.KOMA ,ZIPSYERA ZIKUONEKABE .NDIPO YEHOVAH ANATI REFER MATHEW 11 VS 14 AND TO END "" GIVE ALL YOUR BURDENS UNTO ME..AND I WILL GIVE YOU CARRY MY YOKE OF LOVE. HUMBLENESS AND PATIENCE FOR MY YOKE IS LIGHT AND I HAVE COMFORT TO YOU AND GENUINE LIFE AND I SHALL FIGHT YOUR BATTLES UNTIL YOUR ENEMIES ARE TOTALLY BANISHED AND DISAPPEARED FOREVER REFER EXODUS 14 VS 14 TO END GLORY BE TO GOD IN JESUS NAME. MR GAME CHANGER HAND YOUR ENEMIES TO JESUS CHRIST OUR LORD AND SAVIOUR REFER JÒHN 6 VS 1 TO END AND HIM WÌLL AVENGE YOUR ENEMIES TOTALLY
KUCHILOBWE KULIBE OLEMBETSA MAVOTI A MEC NDI A NRB .NDIYE ANTHU TITANI ? KOMA A MCP AKUNGOPEREKA MATUMBA CHIMANGA MA 50KGS NKUSINTHANITSA NDI MA ID A ANTHU. KUNO ZACHITIKA KU NTONDAKU KU CHILOBWE LAST WEEK
Mulungu ali nanu cholinga Mr muthoro ndipo apitiliza kukutetezerani kuli konse mutadzapite❤❤
Mulungu anali nanu cholinga..titetezeni ife
Munanyamula mbendera ya chilungamo ndi chifukwa mwapulumuka mulungu ali ku mbali yanu ankanakhala chimwendo zikhale kunkuyu ataoloka chifukwa alibe chisoni ndi dziko lathu akuvutika mulungu si Lazarus
Thanks so much God bless you
Mulungu alinanu ndipo sakusiyani inuyo apa tipite pasewu tiyeni guys osasiyira osutsa bomawa ife ndamene rikuyenera kuyenda nawo amalawi tiyeni
iwe born kalindo mtanyiwa nonse komzani ma demo ma oudio tatopa nao
Koma inu kumakuyanjani nkulalikila not zinazi chifukwa mawu akuchita kumveke
Ambuye apitilize kukutetezani ndipo ambuye atiweluze
Chakwela chimunthu choyipa ntima
EYA A GAMECHANGER MWAAKHULUKIRA AMANGAWA ANU.KOMA ,ZIPSYERA ZIKUONEKABE .NDIPO YEHOVAH ANATI REFER MATHEW 11 VS 14 AND TO END "" GIVE ALL YOUR BURDENS UNTO ME..AND I WILL GIVE YOU CARRY MY YOKE OF LOVE. HUMBLENESS AND PATIENCE FOR MY YOKE IS LIGHT AND I HAVE COMFORT TO YOU AND GENUINE LIFE AND I SHALL FIGHT YOUR BATTLES UNTIL YOUR ENEMIES ARE TOTALLY BANISHED AND DISAPPEARED FOREVER REFER EXODUS 14 VS 14 TO END GLORY BE TO GOD IN JESUS NAME. MR GAME CHANGER HAND YOUR ENEMIES TO JESUS CHRIST OUR LORD AND SAVIOUR REFER JÒHN 6 VS 1 TO END AND HIM WÌLL AVENGE YOUR ENEMIES TOTALLY
Kod awa samene anathandizira kut a mcp alowe boma
KUCHILOBWE KULIBE OLEMBETSA MAVOTI A MEC NDI A NRB .NDIYE ANTHU TITANI ? KOMA A MCP AKUNGOPEREKA MATUMBA CHIMANGA MA 50KGS NKUSINTHANITSA NDI MA ID A ANTHU. KUNO ZACHITIKA KU NTONDAKU KU CHILOBWE LAST WEEK
Allah alinanu comrade osaopa osatopa osafooka
Osamaopa munthu zoonadi awuseni