Amalawi angofika pozolowera kuti Forex yawo ikuthera maulendo a president

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 13 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 134

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 Рік тому +6

    😂😂😂😂😂😂😂dziko lili mmanja mwakapolo ali busy kudziwa mayiko bas akut economic engineer pogwetsa kwacha kut amalawi azisauka, koma abale

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 Рік тому +1

    Akamuchemerera amadziwa kuti ndi mburi,Professor Peter Muthalika sangalore zimenezo that's why My fellow Malawian are suffering 😢 💔 😫 because sleeping of the Leadership.

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Рік тому +3

    😂😂😂😂😅😅😅😅 koma ndafwa kkkkkk

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 Рік тому +1

    You're the best man!! Big up!!

  • @johnman4619
    @johnman4619 Рік тому

    Zoona mpaka kupita ku johnnn zinthu zisali zawo mpaka kukhara no 1 kufika mmm mulibe manyazi mr kamwendo munjira

  • @EphraimNaveya-fc4iu
    @EphraimNaveya-fc4iu Рік тому

    Chakwera ndi president ochitisa manyazi pa dziko lonse lapansi,angoyenda mawulendo opepera osapindulira a Malawi 😢😢😢

  • @jamesjealous-p4v
    @jamesjealous-p4v Рік тому +1

    Chakwela sakulakwitsa kuyendayenda ndi tchito yake kupepha mayiko olemela vuto a malawi nsanje ndi kaduka zimatipweteka 😂😂😂

    • @farmupmalawi
      @farmupmalawi Рік тому

      Aaaah ulendo wa chakwela ukudziwa kuti ndi ndalama zambiri zimaonengeka iweyo sukudziwa ukukamba

    • @jamesjealous-p4v
      @jamesjealous-p4v Рік тому

      The more you win the more you spend

  • @stanleykaludzu-bm4pm
    @stanleykaludzu-bm4pm Рік тому

    Ka instrumental ako kamandiwaza heavy

  • @jackmambo2638
    @jackmambo2638 Рік тому

    Mwatisiya mmalele biggy

  • @tingo3155
    @tingo3155 Рік тому

    Sadziwa kanthu mbuzi yachabechabe

  • @MathewsPhiri-y3v
    @MathewsPhiri-y3v Рік тому

    Carry on brother, good job , tell people the truth

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Рік тому +1

    BIG 👍

  • @AshrafuBwanali-qi3my
    @AshrafuBwanali-qi3my Рік тому +1

    President of history in the world

  • @josephkarengera5895
    @josephkarengera5895 Рік тому

    Tiwuzeni President Ibrahim Traore

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 Рік тому +1

    Ife tamfa basi ma ulendo onsewo akumanwela ndichani 😢😢

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 Рік тому +2

    Almost every day amayenda konseku kusakaza chuma chaboma

  • @SuFa2050
    @SuFa2050 Рік тому

    Tikamati ndnu One musamakane taonan mwawerengesa ma Ulendo onse amene Chakwera wayenda olo iye mwini sakukumbuka

  • @hanifuyahaya9064
    @hanifuyahaya9064 Рік тому

    Nde america imeneyo imachemelera ma president akwafrica akamapala ati kuopa angafanane nawo. Koma chakwela ndidolodi poyenda yenda ndamutaila kamtengo

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 Рік тому

    Kom ndye di iyeyo si member wa bricks wa zatani di nanga kom malawi eshiiii dyera.

  • @davidlinerevelation3427
    @davidlinerevelation3427 Рік тому

    Chilima and atupele one should be given a chance

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Рік тому

    Eish

  • @FahadifalajiFalaji
    @FahadifalajiFalaji Рік тому +1

    True king

  • @WisdomMwitha
    @WisdomMwitha Рік тому

    Ife chakunda chanatuluma big man tsoka lobadwanalo ili minyama mavuto ama president kaya adzapezeka opulumatsa Malawi

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du Рік тому

    Mbuzi iyi mavuto Alitho chakwera sazatheka

  • @richwilly681
    @richwilly681 Рік тому

    Amwene Ku malawi kooo musawelengele kuti wayenda ngakhale kuno ku south Africa ramamposa amayenda daily

  • @shupikayintuwaluwa-5899
    @shupikayintuwaluwa-5899 Рік тому

    Pulpit wa Imf. Kupeperaa

  • @SalvationMumba-rl2fk
    @SalvationMumba-rl2fk Рік тому

    General

  • @kantionsankhulani
    @kantionsankhulani Рік тому

    m'makwana

  • @francistonysanena5349
    @francistonysanena5349 Рік тому +1

    Mwa manyazi he was the first head of state to arrive in SA the whole world ku bricks summit...

  • @AlexKaunda-ir6rz
    @AlexKaunda-ir6rz Рік тому

    Mai achakwera anali hule ndi chifukwa Ali ndi mtima oyendayenda

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure Рік тому

    Iweyo ndiwe mfiti ndithu chakwera mmmm chisoni mulibe

  • @andersonbenmwema3916
    @andersonbenmwema3916 Рік тому

    galu ya president

  • @davenchimadzi6529
    @davenchimadzi6529 Рік тому +1

    Boma anatengela zimenezo bas kufuna kuziwa mayiko ena 🤭 munthu ameneyi akundibowa kod Kumalawi afiti anatha eti😂😂😂

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Рік тому

    Thanks

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 Рік тому

    Alibe zochita mu office mkulu ameneyu. Kuyenda nde amatha zedi. Munavotera nokha

  • @EmmanuelKamsale-ph1nr
    @EmmanuelKamsale-ph1nr Рік тому

    inuyo mmazitsata bg man

  • @chrismakhela7133
    @chrismakhela7133 Рік тому

    Mumatha boss

  • @hopembendela
    @hopembendela Рік тому

    Chakwela maulendo onsewo zausilu zopanda ntchito zausatana basi

  • @luqayyayaseenmjojo4944
    @luqayyayaseenmjojo4944 Рік тому

    Vuto la amalawi sitiziwa chomwe timafuna, Kunali achina Muntharika samkayenda , mummkalankhula chipongwe kuti president wanji osayenda kuona anthu, lero wabwera uyu akuenda mukudandaula kut folex eeee ayi ndithu

  • @ShaqMeyer-qu2hs
    @ShaqMeyer-qu2hs Рік тому +1

    Malawi kkkk kuzamva

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Рік тому

    Ndi mubusa ndiye akumapita na lalikila uthenga wabwino ngati paulo

    • @simongondwe4280
      @simongondwe4280 Рік тому

      Exactly no matter what Mr Chakwela is my president ilove .nothing else tobe loved only DR Chakwela bass from West to south, from north to east only wise president is only DR Chakwela ❤❤ 👈💔

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Рік тому

    Chakwera ndi venda osaka ma allowance. Mbava yeniyeni.

  • @kantionsankhulani
    @kantionsankhulani Рік тому

    Koma sizathuzi mmm zingowononga ndalama

  • @ishmaelmkuluma2013
    @ishmaelmkuluma2013 Рік тому

    Iwe izingomaliza ndalama zaboma

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Рік тому

    Mbuzi yamunthu chakwera

  • @dartweedzmdawali5063
    @dartweedzmdawali5063 Рік тому

    Maputo sazatithela ife

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242 Рік тому

    Waonjeza nkuruyu kwambili

  • @OwenChitalo
    @OwenChitalo Рік тому

    Ithadi ndi galuyu mwati tionapo chanzeru ngat

  • @rajabadam2426
    @rajabadam2426 Рік тому

    Messa mumafuna nyamata woganiza bho ndiameneyo mukhaula muona l'm ndili kuno ku Namibia

  • @marthacassam
    @marthacassam Рік тому

    Koma ndiyetu azao akuyenda kusaka ndalama osati kuyenda kopanda phindu

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363

    Kodi Khondowe anamwalira?

  • @emanuellbanda4028
    @emanuellbanda4028 Рік тому

    Zikumveka boss

  • @lloydlongwe426
    @lloydlongwe426 Рік тому +2

    Chakwera only came yesterday to attend bricks summit not 5 days ago as you are saying

    • @yusufusaidi5374
      @yusufusaidi5374 Рік тому

      Chakwera wayenda mokwa sopano ayambe kugwiritsa ntchito ndalama zake

    • @tingo3155
      @tingo3155 Рік тому

      Ndi mbuzi Chakwera koma alira

  • @hannahmazizwa7054
    @hannahmazizwa7054 Рік тому

    Ine chimene chikundidabwitsa ndi choti a first lady akuzatani ku Brics summit?? all other Presidents ayenda okha opanda azikazi awo nde awa afirst lady wa akuzatani kuno, kodi alibe zochita ku Malawi ko , summit yi ndi ya ma President okhaokha chomwe Mayi Chakwera wabwera nawo ku summit ndi chani ??

  • @ChembeSolomon
    @ChembeSolomon Рік тому

    Never give up ❤

  • @FahadifalajiFalaji
    @FahadifalajiFalaji Рік тому

    Meneo pathako pake

  • @caigondon1126
    @caigondon1126 Рік тому

    Akuluwa ndiwoononga koopsa ndithu ndaona

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib Рік тому

    Akulu amenewa Zambiri akuziona kuukuru

  • @eunicemoyo6024
    @eunicemoyo6024 Рік тому

    Ma ulendo 49 ngat matebule 😀😀😀

  • @YunusuOfesi
    @YunusuOfesi Рік тому +1

    Koma kumalawi kuno kuli chibwana kwambiri

  • @mustaffahhemmad
    @mustaffahhemmad Рік тому

    Amalawi tigwirane manja ..eee 2025 election

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k Рік тому

    Chilichonse chakwera ndi Chakwera!

  • @JohnSaini-b3p
    @JohnSaini-b3p Рік тому

    Muzikhala neutral mukamayankhula nkhani ndangodutsamo 😂

  • @SalvationMumba-rl2fk
    @SalvationMumba-rl2fk Рік тому

    Kod Putin wafika ku south Africa as u was tell us 04/08/2023?

  • @NoahKalima
    @NoahKalima Рік тому

    Ayi koma sakukhalad pasi

  • @georgechikafutwa1334
    @georgechikafutwa1334 Рік тому

    Mafilika tidakaopabe kuima patokha timadalirabe nzungu kwinaku tikusauka iwo naamalerela

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Рік тому

    Mau big man ❤

  • @KINGMANMAKALA-hb9gs
    @KINGMANMAKALA-hb9gs Рік тому

    Chakwela koma anaphinidwa

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 Рік тому

    Chakwera ndi mbuzi yopanda mzeru

  • @TonyBanda-ch6vo
    @TonyBanda-ch6vo Рік тому

    Chakwera atipha ndithu

  • @Blessings-c2i
    @Blessings-c2i Рік тому

    Iweyo ukufuna asamayende? Ulinditchito yowerenga mawulendo mmalo mowerenga ndalama zako ngalu iwe

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 Рік тому

    😂😂😂😮komatso chakwera zoonadi chekwera chawuluka zed mamvuto awa dziko lanthu guy's

  • @matembamadadada8291
    @matembamadadada8291 Рік тому

    ulama captain

  • @abisalomchunga6695
    @abisalomchunga6695 Рік тому

    Chakwela ndi oyipa kwambir

  • @HamdanMasuku-b3n
    @HamdanMasuku-b3n Рік тому

    Inu nd captain bro

  • @edsonkatanda
    @edsonkatanda Рік тому

    Mwala oyenda yenda siuyanga ndele.

    • @aggogokina8992
      @aggogokina8992 Рік тому

      Awa ndiye sayanga ndere ndithu akugudubuzika kwambiri😂😂😂😂

  • @AmiduMmadi
    @AmiduMmadi Рік тому +1

    Km apa nde tinapala a Malawi 😢😢😢

  • @danielkhinguirossejuliasse6106

    Kkkkkkkkk koma kumuwelengatu President Hastings luzurus chakwera

  • @vusoacquaron9084
    @vusoacquaron9084 Рік тому

    Khani ndkukatenga chiself Nd ma guy basi

  • @milliwardchiombeni9983
    @milliwardchiombeni9983 Рік тому

    Malawi anakonza.... Koma president wathu yi umunthu ulipo?

  • @JaphyJ
    @JaphyJ Рік тому

    mtsogoleri wathu ndi citsiru

  • @MobigoIT
    @MobigoIT Рік тому

    Zitsilu za anthu

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 Рік тому

    Ana asatana amaiwala kut kuli infa imene ikhoza kuwatenga mwadzidzidzi

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Рік тому

    This is too much Mr president

  • @johnfarouk8982
    @johnfarouk8982 Рік тому

    Chakwera machende ake

  • @wysonkomela8223
    @wysonkomela8223 Рік тому

    Yooooo pena kumatulukaso tsodzi ndithu ukaganizla zomwe zikumachitika kumalaw akuthipha bas

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Рік тому

    Any anylitics for Zimbabwe elections as it will be conducted on 23rd August, tomorrow 2023

  • @NoahKalima
    @NoahKalima Рік тому

    Komatu akuyenda kwambili

  • @KassimuKachulu
    @KassimuKachulu Рік тому

    Ndipo mfiti iyi chakwelayu mmmmmmmmmmmmm ayi ndithu mulungu atithangatile

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 Рік тому

    CHAKWERA AKUFUNA APEZELEPO MWAYI OZIWA MAYIKO AKUNJA ntchito yake sakuyiziwa Mbuli ya munthu

  • @MavutoTheu-fj4yw
    @MavutoTheu-fj4yw Рік тому

    Akulu awa akuoneka kut amafuna u president kut aziyenda maiko akunja basi mbuz yamnthu

  • @khalifacalvinajass9998
    @khalifacalvinajass9998 Рік тому

    Koma pupwa chakwela eeeeeeee sazamva

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Рік тому

    Kodi Chakwera yu atamwalira lero mpaka wina akhoza kulira?

  • @BorauzimaMuderhwa
    @BorauzimaMuderhwa Рік тому

    Koma kumalawi kuli chibwana

  • @Justman34_dislike
    @Justman34_dislike Рік тому

    Ogo

  • @amadukalambo
    @amadukalambo Рік тому

    Kkkkk Koma Ku Malawi

  • @evancejohn4556
    @evancejohn4556 Рік тому

    Tiuzeni ngat Putin wafika ku SA

  • @JumaMboneka
    @JumaMboneka Рік тому

    Bwanji osangomuloza chakwelayo kuti amwalile kod afit aja alikuti

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior7093 Рік тому

    Chakwera mbuzi ya munthu president opanda mzeru he came to steal kill and destroy Malawi

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Рік тому

    Ufiti chakwera