Sizonyengerera_Uncle Sam ft APM {Prod@B2 Studios}

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 жов 2024
  • Nyimbo iyi inaimbidwapo ndi malemu malume anga #Joseph_Tembo nthawi imeneyo chipani cha DPP chikutsgoleredwa ndi malemu #Bingu_Wamuthalika. Tsono ine ndaibweretsanso kachikena yomwe ikukamba za #Profesor_Anthor_Peter Muthalika
    Ndikusaka thandizo kuti nyimboyi ituluke ndipo ithandizire kuchotsa nyasi m'bomamu. Ngati mukufuna kuthandiza palikonse #0992968326 airtel money ndipo imalemba Alice Wonderford
    ~APM MY VOTE ~

КОМЕНТАРІ • 1