Nkhani Yoti NRB Amafuna Kubela Mavoti Ku Kanengo Sizoona - Mzika

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 17

  • @ntombiunice8637
    @ntombiunice8637 20 годин тому

    Ndinzoveka ndithu

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal День тому

    Iwe ndi chisilu kwambiri bwanji zapezeka za Lilongwe zokha zamadera ena zili kuti en kuyambira liti malo osungilamo chimanga ikasandusemo mobela mavoti ngati mukuti ndi bodza bwanji simunawuze anthu ena kuti asadabwe ndipo zikuwoneseratu kuti umumu mumalembeseramo afiti inu muwonatu mulungu akukuwonani

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 20 годин тому

    ndipo, sangayende, pakhomo, pako, paliyese,,kudzalawila

  • @BensonPiasi
    @BensonPiasi День тому

    Iwe ndiwe garu why Lilongwe yokha Kodi kunsanje bwanji atiuzekuti kunsanje akupangira kuti kumangochi ku chikwawa iweyo usatiwonengati ndife mburi

  • @FrankRabson-q6j
    @FrankRabson-q6j 23 години тому

    ukuyankhula ngati ukudwala

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 20 годин тому

    mukhaula, chakachake,

  • @KettieNathaya
    @KettieNathaya День тому

    Nde ndichifukwa chiyani akulu akulu sanadziwe? Kut mwapeza nyumba yina . Zitsiru zawanthu

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 День тому

    😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 20 годин тому

    ngat mumazitenga, kt , otsutsa,,simugaluze, mungokhala, chete

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms День тому

    Nanu inu chokani

  • @MandeuleFanny
    @MandeuleFanny 21 годину тому

    Koma abale kupereka umboni wonama

  • @SymonJowabe-y1q
    @SymonJowabe-y1q День тому

    Kkkkk

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 20 годин тому

    kd, akuchitamantha, ndichiyani, akati mpikisano, wina, kuluza, wina, kuwina,,mcp.,sikutekeseka,bwanji, tixingovela, otsutsa,basi,zausilu

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 16 годин тому

      Panopa ndikaganiza zasiku la imfa yanga ndsiku lachiweruzo aaaa Ndikuopa Mulungu modzi basi yemwe alibwana pasiku lachiweruzo mwini zonse liopeni siku lomwe mudzalowe manda

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 16 годин тому

      Liopeni siku lomwe mudzalowe manda

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 16 годин тому

      Chopsera mtima ndi chani anthu mukudya misonkho ya amphawi misozi ya amphawi mudzaimwa imeneyo Mulungu akukanthen nonse komwe uliko