Mai wina wakwirira ku munda mwana wake obala ekha...

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 71

  • @SiphokuhlePitar
    @SiphokuhlePitar 2 місяці тому +3

    Welcome back semanai we like you guyz keep it up

  • @SoldierWilison
    @SoldierWilison 2 місяці тому +2

    Welcome back govat ndimakunyadilan guys from Malawi mangochi makanjira

  • @KulisungahWadson
    @KulisungahWadson 2 місяці тому +3

    Kuno ku lilongwe kudziko la malawi mai ameneyo wapalamula mulandu akufunika apite ku court akamuweluze Mr wadson kulisunga ku lilongwe 8

  • @MilikaKilion-tn1bn
    @MilikaKilion-tn1bn 2 місяці тому +4

    Zulo zuloli ndimakuganizilani achina govati mpaka ndimazifusa kuti munasiya kapena vuto ndi phone yangai

  • @WinstonKachali
    @WinstonKachali 2 місяці тому +1

    Welcome back guys (from Mzuzu)

  • @EuniceBangoloh
    @EuniceBangoloh 20 днів тому

    Amangidwe mtsikana yo chifukwa ndikupha kumene wapangako .
    Ngati mwana anali wakufa zinakanika bwanji kuwauz anthu.
    Tidziti mwanayo anabadwa anthu ena asakudziwa.?
    Kuchokela kuno ku South Africa 🌍.

  • @MEGANABIGAILMNTHALI
    @MEGANABIGAILMNTHALI 2 місяці тому +1

    Welcome back my Dear brothers

  • @zaithwachiwaya
    @zaithwachiwaya 2 місяці тому +1

    Munasowa ma guys mm welcome back

  • @JonasiJayilos
    @JonasiJayilos 2 місяці тому +1

    Km zithu zake zomvuta kwambiri why azi mayi

  • @RabeccaGama-f7m
    @RabeccaGama-f7m 2 місяці тому +1

    Welcome back guys

  • @JorgechicoteWilliam
    @JorgechicoteWilliam 2 місяці тому +1

    Ndizoipa zoopsa mmasku otsiriza ndne Jorge phili kuno kumtaka domue

  • @KANJEMATAFALE
    @KANJEMATAFALE 2 місяці тому +1

    M usamasowe ine kuno ku thekeran ku thyalo

  • @LevisNyasulu
    @LevisNyasulu Місяць тому +1

    Komaso ngatii anali.wakufa chamulimbisa ndichanii kukwilila yekha muzingenii nayeso

    • @EmoMphande-ui3xi
      @EmoMphande-ui3xi 20 днів тому

      My comment iyi ifa sichinthu chamasewera munthu akabereka mwana okufa amakhala ndi chisoni ndipo mwana samakwilira yekha ayi amakwilira akuluakulu nde iye akufuna anamize ndani muoneni mene akuyankhila mwano aaaa

  • @AudtinEliya
    @AudtinEliya 2 місяці тому +1

    kukhothiso bomarake rimeneri aaaaa .imeneyo ayithe okha anyakwawa

  • @HendersonDziwa
    @HendersonDziwa 2 місяці тому +1

    Athu akuyaluka ndi umfiti ena kumasowa ana ena kumapha ambuye chtanayeni dzimai ameneyu

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson 2 місяці тому +1

    Koma choncho sibwino ndithu azimayi chonde chonde tchimo loopsa kwambili.esh Ambuye atithandize

  • @RabeccaGama-f7m
    @RabeccaGama-f7m 2 місяці тому +1

    Akaponya bwanji ali okufa matengeranji mimba mpaka kuisunga uyu apite ku police akalagike

  • @FatumaKamala
    @FatumaKamala Місяць тому +1

    Mayo olimba mtima eeeee 5:59

  • @SlyviaPhiri-bd9uu
    @SlyviaPhiri-bd9uu 2 місяці тому +1

    Koma zovesa chisoni kwambiri mumene kumaphwatekela kubeleka zoonadi 💔💔💔💔💔💔💔

  • @TriciaHerbert-f2t
    @TriciaHerbert-f2t 17 днів тому +1

    Kumapha mwana ena ena akumusowa

  • @AnajoiceSozinho
    @AnajoiceSozinho 2 місяці тому +1

    Que coragem é essa?

  • @NatashaBema
    @NatashaBema 2 місяці тому +1

    Chinkhopecho chikuonekadi kuti ndi mfiti ameneyu

  • @AlasonPaulo-ht7zb
    @AlasonPaulo-ht7zb Місяць тому +1

    Ok

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 місяці тому +1

    Chitsiru cha nzimayi mpaka kupha mwana mmmmm anthu akusowa ana

  • @EmoMphande-ui3xi
    @EmoMphande-ui3xi 20 днів тому

    Aaaaa uyu mumangeni ngat mwana wafa iye mphavu azitenga kut zokakwilira mwana yekha aaaa apolice akachitapo kanthu apa , koma popeza apolice akumalawi ndi agalu amamanga oba zitheba kusiya munthu yemwe apha muzake

  • @TrinityBonjesi
    @TrinityBonjesi 2 місяці тому +1

    Mmmmm mayi otani olimba mtima chochi kupha mwana obereka yekha

  • @jfj-bu5wz
    @jfj-bu5wz 2 місяці тому +2

    Amhamata inu misamasoww delo koma ine João mukuvwkela pá Maputo

  • @Odetta-e5n
    @Odetta-e5n 2 місяці тому +1

    Mfiti yamunthu 3:31

  • @gildocelestinomachaia9143
    @gildocelestinomachaia9143 2 місяці тому +1

    Zachisoni 😂

  • @VistorMwale
    @VistorMwale 2 місяці тому +1

    Mmmm mayi wantundu wanji uyu

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371 2 місяці тому +1

    Mai uyu asazapeze mwai pa moyo wake ndithu adzafe imfa yowawa

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 2 місяці тому +1

    Chokwililila mwana wekha olo ali okufa mchani osauza makolo olo anthu adela wapha mwana

  • @ReginaDinesi
    @ReginaDinesi 2 місяці тому +1

    Kulimba mtima kwabwanji uku😢😢

  • @SueWahna
    @SueWahna 2 місяці тому +1

    Akuwoneka tsikanayo amatamba😮

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 2 місяці тому +1

    Wadya kake alibe mulandu koma chakwera ndiye afunika kundende adapha chilima ndi azake kuchikangawa

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa5981 2 місяці тому +1

    Wamupha uyo mwanayo anali wa moyo ,kuthawa udindo

  • @NatashaBema
    @NatashaBema 2 місяці тому +1

    Takulandirani aGovati munasowatu

  • @balancosemanalckgovate8464
    @balancosemanalckgovate8464  2 місяці тому

    Azimayi atayirira, kuyiwala Kuti ena akufuna wana

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 місяці тому +2

    Tinakusowan makusana❤❤❤

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 2 місяці тому +1

    Olo atakhala kuti anali wakufa analakwisa

  • @FrankT-peAssima
    @FrankT-peAssima 2 місяці тому +1

    Okay ndioyipa tisiti hamaopa njala

  • @ShiraSaidi-oz5mx
    @ShiraSaidi-oz5mx 2 місяці тому +1

    Wabodza uyo akanankhara anali wakufa bwezi atauza anthu

  • @Lameckbwanali-l3v
    @Lameckbwanali-l3v 2 місяці тому +1

    Koma azimayi akutsutsa mwanyoooo

  • @RhodaKalumbi
    @RhodaKalumbi 2 місяці тому +1

    Munasowatu abro

  • @EstefaneoCornelio
    @EstefaneoCornelio 2 місяці тому +1

    Pitilizani ntchito ya bwino mukuichitayi

  • @FerecidadedeshilaShila
    @FerecidadedeshilaShila 2 місяці тому +1

    Nfiti ameneyo anakakhala kuti anali wakufa kale analekelanji kuuza akulu akulu kuti nachila mwana wakufa

  • @RhodaKalumbi
    @RhodaKalumbi 2 місяці тому +1

    Koma zina ukamva

  • @LucyShaibu
    @LucyShaibu 2 місяці тому +1

    Komaa

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 2 місяці тому +1

    😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @ChristopherNgalande
    @ChristopherNgalande 2 місяці тому +1

    Akalowe ameneyo basi ngwakupha

  • @EdwardGeorgeKasabola
    @EdwardGeorgeKasabola Місяць тому +1

    Ulemu wanu munasowatu

  • @SabyMkhutche-i2o
    @SabyMkhutche-i2o 2 місяці тому +1

    Ndi hule ameneyo

  • @Odetta-e5n
    @Odetta-e5n 2 місяці тому +1

    Munasowatu big timakunyadirani

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 2 місяці тому +1

    Mmmm kuyipa mtima

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 2 місяці тому +1

    Ndiwakhaza kwambiri amagwidwe ameneyu

  • @VelinaMdala
    @VelinaMdala 2 місяці тому +2

    Ufiti koma

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 місяці тому +1

    Eeeee kma mkaz ameneu Atha kukupha

  • @Odetta-e5n
    @Odetta-e5n 2 місяці тому +2

    Mfiti yamunthu

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 2 місяці тому +1

    Nayeso amphedwe

  • @GiftgervásioGervásiolino
    @GiftgervásioGervásiolino 2 місяці тому +1

    Mumakwana agova

  • @SammyWaGonga
    @SammyWaGonga 2 місяці тому +1

    Akalowe kosungila anthu opha azawo

  • @AnthonyPhiri-e3g
    @AnthonyPhiri-e3g 2 місяці тому +1

    Mr Govat Good morning

  • @VictorSimon-j9g
    @VictorSimon-j9g Місяць тому

    Amaguidwe

  • @DenisFelix-x9s
    @DenisFelix-x9s 2 місяці тому +1

    Wabwelanso

  • @Maklanalfredo
    @Maklanalfredo 2 місяці тому +1

    Welcome back guys

  • @Odetta-e5n
    @Odetta-e5n 2 місяці тому +1

    Mfiti yamunthu 3:31