Phungu Josephy Nkasa-Bolaso DPP Ndi Peter Muthalika

Поділитися
Вставка

КОМЕНТАРІ • 18

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 3 місяці тому +4

    Dziko lomwe linaphulidwa pa moto lija chakwela walitelekapo ambuye atithandize 😢😢 mulungu ave kulila kwathu

  • @mikaeelmumba2408
    @mikaeelmumba2408 3 місяці тому +2

    Moo faya a.JozeyTiyeninazoni.Mwaitha.

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 3 місяці тому +1

    Phungu Joseph ndi ankhala kale poimba nyimbo

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft 3 місяці тому

    Phungu amatha kulemba nyimbo

  • @RafickTawakali
    @RafickTawakali 3 місяці тому

    Mumakwana inuyo ankasa

  • @James-v8v8d
    @James-v8v8d 3 місяці тому +1

    Mmmmm wang,alula

  • @samsonnangwiya1673
    @samsonnangwiya1673 3 місяці тому

    Mkasa ndi katundu 😂😂😂

  • @omardyman8083
    @omardyman8083 3 місяці тому +2

    Ine kudabwa kuti mademo omachita ndiana omwe akunsana ati tione kusintha apa ndiye tikuonadi kusintha kufela ati ndi m'busa osaziwa kuti ubusawo unachokamo kale wangosala u predator

  • @KumbukaniChimbalanga
    @KumbukaniChimbalanga 3 місяці тому +2

    Joseph Mkasa ndi woimba wanzeru kwambiri

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 3 місяці тому +2

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @EuniceAmbang
    @EuniceAmbang 3 місяці тому

    MCP ndichipani cha mapampaya

  • @KachiyataBoyilo-f4w
    @KachiyataBoyilo-f4w 3 місяці тому

    Ulemu. Wanu fumu

  • @geniuselectrical
    @geniuselectrical 3 місяці тому +1

    anamupadi chilima chifukwa cha mpando

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 3 місяці тому +1

    My vote 2025 to Apm

  • @CharityKangulero
    @CharityKangulero 3 місяці тому +1

    Chakwela mada fakaaa

  • @EuniceAmbang
    @EuniceAmbang 3 місяці тому

    MCP ndichipani cha mapampaya