Manganya, ati waumba nsalu yake, ati asokoneze DPP ndi UTM ati wodya zake alibe mlandu ati kuonetsa nzeru zake zakufupika ngati ndondocha. Manganya uchenjere unaphetsa chilima ndicholinga kuti ukhale pamenepo. Manganya ndimagwila pakhosi tsiku lina
A Kalindo inuyo yambisani Chanu Chipani basi muzachite zokhozeka enawa alephera kale..ndikale munayamba kubwebweta Lija asàaaa .Tizakuvoterani Manganya has a right as a Malawian Citizen kuyambisa chipani as everyone Malawian Can do
Ameneyi ndi amene watenga 80 percent yonse ya utm.tsono poti aliyense ali ndi ufulu woyambitsa chipani chake basi musiyeni ,inuso mutha kuyambitsa chanu.
Achisilu awa, chisale anabera dziko ma billions omwe anakamangira ma school ndi zipangizo za chipatala koma awa achisilu awa kupita ku khothi kukachemerera mbava ngati chisale. Mmesa umadana ndi katangale. Mbuzi ya munthu iyi. Osamumvera uyu akukonza tsogolo lake.
Nde usi walakwa Chan? Asayambitse chipan chifukwa chot pangotha 7 months chigweren ndege, nde iye asapange zake chifukwa cha malem anuo? Komaso munthu anachita kumchosa mu chipan nde azipangaso za UTM chifukwa Chan, komaso munthu akafa wafa olo mpite where he died siziphula kanthu.
Anthu Ake ati akupha a DPP?? Ndege ija anagwetsa ndi a DPP, mavuto waku BT uja simunapha nokha mkumanamizira azanu. Ngt anapha a DPP y sakumangap aliyese until now
Nonse amene mukumunyoza kalindo nzeru mulibe mwanva izizi ananena kale usi ndendaninso kufupika kwake
❤❤❤❤❤ manganya NDI amene anampha chilima
Mr kalindo,my boss❤
Bonie kalindoooo the DC❤
Koma anthu amene amadana ndi uyu kalindo mutu wake sumagwira chifukwa chomwe wakamba chimachitika kupita kwanthawi iweyo kalindo ndikatundu
Tikavotere Dan Mahata bas😊
The DC big mn I lov u mumKonda malaw
Akalindo mukunene zoona. Munthuyu alibe mzeru
Malawi hope ndi Denis mahata
Give him a chance He has right to do wht he is able to do ..
😅🙏😅🙏👍😊
Kalindo is Good guys chirungamo ichi Big
Guys tiyeni tisethe dziko lathu tivole.. Denis mahata
Usi sangaputsitse anthu ndi mwana wang'ono kwabas
Manganya sangamve chisoni chifukwa ndi obwela ku Malawi he from Zimbabwe.mulungu atithandize
Inu kongobadwira uko
THE DC U THE MAN IN TOWN
Koma ndipo kukonda ndalama muthu was mai
He is an excellent new rebrand. Let's support him to be a DPP member.
Ukaseka nanenesa ndimaseka ndimawona ngati kukuseka ndikuwujeni😂😂😂
Inenso namva chisoni kwambiri kuti Koma izizi ndi zoona?
Ndazindikira kuti Bonikalindo ndimuthu oipa wosafunira anzake zabwino! Zomwe usi akuchita moti sakuona ndithu? Eeee ambambo inu takuzindikirani ndithu.
Asogoleni akumalawi ndiyovesa Chisinau kwambili
The DC respect cz umanena reality before action
Ife bola angotitchenetsa nsalu zo iya ,zikatitopesa tizipanga matewera
Usi ndi wa mcp
Akalindo inu mumafunakut dr usi akutsatileni ku chipani cha dpp kwanuko
Mbuzi iyiyi siyizatheka yisiyeni yizilubwalubwa,
sizingachititse,kt,mcp,ilize,zimenezo,fundo,mulibe,kumango,bweleza,zimodzimodzizo,,km,awawa,anthu,moti,akakuvotenleeni,fundozake,zimenezo,
Kodi awa apenga liti
Anthu adyela zawavuta palibe akuwadyetsela nde misala ikuwathamangitsa pompano tiva
Ine ndiye ndi pambuyo Dr Usi
Manganya, ati waumba nsalu yake, ati asokoneze DPP ndi UTM ati wodya zake alibe mlandu ati kuonetsa nzeru zake zakufupika ngati ndondocha.
Manganya uchenjere unaphetsa chilima ndicholinga kuti ukhale pamenepo.
Manganya ndimagwila pakhosi tsiku lina
😂😂😂😂
Munthu ukayambisa chipani zina lachipani limakala losiyana ndichipani chimene unali. Sitipanga makaka ofanana ndi chipani chomwe unali ndiye golden simokoyo muziwe kuti ndifiti yoopsa kwambiri kuthekaso kuti mwina ndiye anagwesa ndege kuti atenge makakawo fiti yimawonekera poyera ngati munthu waphayo sanali olakwa
Wabodza lwe umakhara mbali ya dpp timakudziwa lwe munthu opanda sogolo
kuswa kuswa Kalindo.... tiyenazo....kkkkkk
Iwe osayambitsa chipani chako bwanji?,munthu mwamuthamangitsa ku chipani ndiye mumati atani?,
Koma kumalawi eeeeeeeee Kaya mwe 😢😢😢😢😢😢
Respect
DC mutu sukugwira, munthu uyu wabalalika zokamba zatha wayima mutu
Vuto ndi chani nanuso akalindo usi ndi ufulu wake nsa je pela
kma usi ngati amalephela MP kudela lakwawo ndye upule anukhapo
The Dc
Zinayamba ndikale
Udf inachoka mu mcp
Dpp inachoka ku udf
Pp inachoka mu dpp
Utm mudpp
Pdp inachokaso mu dpp
Chachilendo ndichani
Aliyense pamalo pake mulungu alamula yekha pa 16
Michael Usi is exercising his democratic right. What’s your problem? Komanso mesa UTM inapinyulitsidwa ku DPP
Why is it a crime to be democratic in Malawi.
Mpaka kuvotera odya zake alibe mulandu kkkkkk ndiye kusokeratu
Munthu anachita kuchotsedwa apa muli kukamwa wawawa mxiew
Mcp gwilizano ndi odya zake alive milandu ,,,,, apano maula aathu amwe anali pa upo ogwesa ndege aja mwaagwilatu mupangaso kafukufuku wina ngati
Opepera.akolo.ndioopwe.kwambiri
Tiuze zoveka iwe ulibe zeru iwe uzawerukira yomweyo
A Kalindo inuyo yambisani Chanu Chipani basi muzachite zokhozeka enawa alephera kale..ndikale munayamba kubwebweta Lija asàaaa .Tizakuvoterani
Manganya has a right as a Malawian Citizen kuyambisa chipani as everyone Malawian Can do
Kalindo sanyengelala munthu bwino wa kalindo saopa munthu
Koma zoti mudziwe ndizakuti, Kalulu sangathe kumwamadzi Galu alipambuyo, 😢😢 mwimvi oyang'anila umatosa mmaso,, Bawo ikakutha dziwa kuweya Ina msanga ndiyo khani imeneyo
Tikavote mwaa unyinji bs Mr chikangawa achoke bs
Manganya chinangofupika ngati chindondocha that's why pali sign ya khasu pansalu yomwe wapanga. Ndindondocha manganya
Kd utm inachokela kt nde odya zake alibe mulandu popanga zake Mesa ndufulu iwe ndi mbuzi kwambiri mphuzilako kupanga zako
Ameneyi ndi amene watenga 80 percent yonse ya utm.tsono poti aliyense ali ndi ufulu woyambitsa chipani chake basi musiyeni ,inuso mutha kuyambitsa chanu.
Bas vomelezani inu kut mzanu ndiwazelu kusiyana ndiwe
Nom
Malawi mulungu amalikonda keno malawi ndi dziko lotembeleredwa,tigwire ziti.
Bon kalindo mutu umamuvutitsa . I think misala imamubvutitsa. Dr Usi bravo! Inayi ndi misala isakusokonezeni
You think Usi awina?
Amanena.chocho.amalawi.inde.big❤
Kodi manganya abwelera liti kwawo ku Zimbabwe
Achisilu awa, chisale anabera dziko ma billions omwe anakamangira ma school ndi zipangizo za chipatala koma awa achisilu awa kupita ku khothi kukachemerera mbava ngati chisale. Mmesa umadana ndi katangale. Mbuzi ya munthu iyi. Osamumvera uyu akukonza tsogolo lake.
Adamuphesa chilima ndi USI
Michael usi anamuchotsa ku UTM chifukwa cha uchitsiru manganya ndi wopusa kwambiri
@@mabvutomichaelpanagona1949 wopusa ndi iwe ulichaani tamuwoneni Ali mbu
Koma usi akunama mcp yawanamizi dziwani skc mzmu wake udzakatha wina aliyense
Iwe ulibe abale anamwalira Kuti uziwakumbukira
D C
Munthu anamuchotsa mmati atani munthu amadya msima mwana wake atamwalila siyani jelas
Garu kobasi
😂Ma battery ati
Munthu kuti muziwe kuti zeru alibe choyamba amakhala wamakani sa ava za wina. Amakhala osata mapazi azake kwambri . Amapanga zinthu mwachibisira. Amalimbana kutenga zayeni ndikukhala zako. Munthu wotere ndimunthu wakhaza moopsa.
Nde usi walakwa Chan? Asayambitse chipan chifukwa chot pangotha 7 months chigweren ndege, nde iye asapange zake chifukwa cha malem anuo? Komaso munthu anachita kumchosa mu chipan nde azipangaso za UTM chifukwa Chan, komaso munthu akafa wafa olo mpite where he died siziphula kanthu.
Namanyenga mpaka kuyambitsa chipani koma ndie uwathatu akazi kumeneko
Kkkkkk piliziiiii😂
iweo ukatero zako zimakhala zaayela uzipusisa anthu kwanu komweko ngat dziko lino likuvutika iweo ukuchitapo chani ngat zimakukhuza?
Km zomwe akulakhulazi analakhukapo ndipo apa ndi izi zachitikazi
So do you think he is lying
Golden smoke the DC sopano kkkk
Malawi ndi ovesa chisoni to be honest we are not serious
Mesa ndi zako
Mkunena zamavoti komaadpp akupha anthu akakhala wamcp simyankulapo kod ufulu umene mkumenyela wa anthu adpp wokha okha enawa sianthu zisilu inu komaso afiti inu anthu akumwela
Anthu Ake ati akupha a DPP?? Ndege ija anagwetsa ndi a DPP, mavuto waku BT uja simunapha nokha mkumanamizira azanu. Ngt anapha a DPP y sakumangap aliyese until now
Born ndi kapena uyu
Mbambande
Ndipo ulira sunati, dikila iwenso SI alipo omwe amakutuma? Sunati ulila
Mr Bon Kalindo mudasankha kukhala actist and leave Micheal Usi alone for what he's doing
SIX MONTHS KUYAMBITSA CHIPANI NDIYE ANTHU ACHIKODE ZOONA KOMA MWAZI WA MUNTHU aa NDIOOPSYA NDITHU 😭😭
Kodi kumalawiku kulibe limitation ya zipanizi kamalawi Kang,Ono ng,Ono mpaka ziphani 100 wina aliyense amene walota ndi manthongo thoo kuyambitsa chipani ayi tsuka man
Zipani zonsezo Za chiyani kd
Koma penapake zipani zotsutsa zomwe zili mdziko muno ndizozizila, zofoila
Kuswa Kuswa Golden smoke, Bon kalindo mwana oopsa kwambiri 🎉🎉🎉
Kalindo alibe zelu Muthu amuchotsa amafuna apange bwanji 😂😂😂😂😂
@gwatandingo9502 iweyo ndiye wamzeru 🤭🤭🤭
Eya ayambitse vuto palibe iwenso yambitsa chako chotukaana opposition simukuwina umbuni ndi umenewu usi ♥️♥️❤️🙏 wonetsa ufulu wako MCP my vote ❤️❤️❤️😊😊
😂😂😂ndaitchelatu
Mbali yanga sindikuwonapo vuto pamenepo koma sanje chabe 😂😂😂😂😂
Ndiwe kape
Kwambili
kunali azanu pano ali kut zaziiii
Iwe kapolo, kayambitse chako chipan dzimachende dzako
Iweyo uli ND mango 🥭 ulibe machende
Michael USi anachotsedwa mu UTM ndiye mumafuna apange chani. A Bon Kalindo mwangokhala ndi nsanje
Abwerere ku tikuferanji, that guy is not politician
Ndani anamuchosa usiyo ku UTM usi ndi fiti yayikulu ndipo ndikape kwambiri
😂😂
Iwe mbuzi
Manganizo ndi zolinga ndi zosiyana, Bon sakudana ndi aliyense akungoyankhula zomwe akuziona kuti ndi zothandiza
Auze makapewa
Kkkkkk sanje iwe!!!!
A bon kalindo ndinu a chitsiru mzanu mwamuthamangisa mu chipani chanu nde akanatani
The DC has joined DPP
Zipani zoyambisa ahlomwe zokha kupitilila 10... Ehhh mutofuna chaniii😂...
zosadabwitsa usi anali ndi chipani chake wodya zake alibe mulando utm yisadayambe komaso kufanana kwa mayuforomu sivuto
Nenani fundo akalindo muti chalakwika ndi chan inuso mwa kwela team ina yake2
Galu wa DPP Born kalindo uyuu
Chomwe walakwa usi ndichani?
Akununkha usi
Koma zoti mudziwe ndizakuti, Kalulu sangathe kumwamadzi Galu alipambuyo, 😢😢 mwimvi oyang'anila umatosa mmaso,, Bawo ikakutha dziwa kuweya Ina msanga ndiyo khani imeneyo