T0p 10 Most Beutifull Female Celebrities in Malawi, 2021

Поділитися
Вставка

КОМЕНТАРІ • 241

  • @profound-dee8828
    @profound-dee8828 2 роки тому +14

    Analemba list yi watilakwira,🥺 imagine anthu akunjaku kumawona izi. Mwaika akazi otchuka osat top vichi vichi beautiful

  • @mariahtembo2727
    @mariahtembo2727 2 місяці тому +7

    The most beautiful woman in Malawi,its true Mary Chilima you deserve it

  • @benedictwick2507
    @benedictwick2507 Рік тому +6

    Mayi chilima deserves to be number one

  • @priscillahellenphiri798
    @priscillahellenphiri798 2 роки тому +20

    I thought its about beautiful woman
    But this is about popularity

  • @FannymatembaMwale
    @FannymatembaMwale 2 місяці тому +1

    Beauty lies in the eyes of the beholder 👍

  • @user-wq9ex2sf3b
    @user-wq9ex2sf3b 8 днів тому

    Yes ❤

  • @rosamwenelupembe6856
    @rosamwenelupembe6856 2 місяці тому +1

    Thank u Lord for our beautiful ladies in Malawi

  • @veramphande7856
    @veramphande7856 2 роки тому +11

    Apatu sanayike akazi akumalawi okongola koma otchuka

    • @gloriaazele1237
      @gloriaazele1237 5 місяців тому

      Ndipo exactly

    • @StythewsMkwiyo
      @StythewsMkwiyo 2 місяці тому

      I can agree. These are 10 top well known Malawian ladies.

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no Місяць тому +1

    Amene amasankhayo ngwa khungu , kungotiikira abulutu okhaokha , ati poti Ali ndi ndalama , maonekedwe sindalama kapena kutchuka , kuchititsa manyazi kwake !

  • @bdjhjjjgchkb8912
    @bdjhjjjgchkb8912 3 роки тому +37

    But for me my wife is olny position one forever

    • @harrisonmwanga9812
      @harrisonmwanga9812 2 роки тому +1

      😂😂😂😂😂😂

    • @movetikaposa692
      @movetikaposa692 9 місяців тому +1

      Is she a celebrity?

    • @user-bh7hf5lw5l
      @user-bh7hf5lw5l 6 місяців тому

      That's not her title You said celebritys she should not been there .she is beautiful we know but not a celebrity

    • @user-ec4jo9cu4d
      @user-ec4jo9cu4d 3 місяці тому

      Okay 😂😂😂😂😂u mean your wife is cerebrate?

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 2 місяці тому +3

    Marry yekhayo I agree

  • @troychikhwaza-Mw
    @troychikhwaza-Mw Рік тому +2

    Wow Malawi anakoza❤

    • @mosewallace9717
      @mosewallace9717 2 місяці тому

      f cc cc cc cc. c c c c c c. c. c. c.c c. c c c. c.c c c. c a

  • @user-sz6bi3tw5y
    @user-sz6bi3tw5y 2 дні тому

    Grace chinga akanakhala wamoyo akanakhala pa number 1

  • @AutonChalion
    @AutonChalion 9 днів тому

    Mery is number one according second lady in Malawi Rip SKC😭😭😭

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 3 роки тому +13

    Ine pandekha ndimadziona kuti ine ndiwokongola kwambiri mulungu anandilenga ndicholinga

  • @ThandieMushali-gi7js
    @ThandieMushali-gi7js 2 місяці тому +1

    Marry yes❤

  • @berthermtambo14
    @berthermtambo14 3 роки тому +9

    Koma na mulungu anamulenga munthu ndikumusiya dziko lino nati zili bwino yense ngokongola

  • @mariamomar4323
    @mariamomar4323 2 роки тому +5

    I salute my teacher madam kaliati she is beauty of the beauty ❤❤❤❤

    • @mutenimkisi4912
      @mutenimkisi4912 Рік тому

      If your wife is a Cerebrity, then it's ok to you.

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 5 місяців тому

      @@mutenimkisi4912 😃😃😃😃😃

  • @mosesbanda3321
    @mosesbanda3321 5 днів тому +1

    No 1 aaah zoona. wow. then Zani Challe on 2 why exclude her? hv u seen Zanni? No 10 should be no. 3. and 3 should be no. 4. Then all women over 50 shu hv their own list. its not fair clamping them together with the youth. But all women are beautiful in their own ways

  • @sydneysakala7246
    @sydneysakala7246 2 місяці тому

    I really love Wendy❤❤❤❤

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 3 роки тому +12

    Zamasiku ano amai busa kuvala trauzer kkkkkkk

  • @RuthLynda
    @RuthLynda Місяць тому

    Wow the most beautiful woman in malawi is madam Mary chilima ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @sheenahmwalabu
    @sheenahmwalabu Рік тому +1

    Mia, Mary, Patricia, Ethel, for me 🔥🔥

  • @rachelphiri918
    @rachelphiri918 Місяць тому +1

    Ethel, Mia and Chilima

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z 5 місяців тому +1

    Nanga taganizani mpaka aujenk alimguru la most beautiful zoona,mutichimwitsapo apa

  • @FunnierKaunjika
    @FunnierKaunjika 3 місяці тому +4

    Akasukusule kumasoko achose make up tione u beautiful wenwen hiyaaaaa

  • @kingogasteney
    @kingogasteney Рік тому +2

    Wauu 🇲🇿🇲🇿

  • @AnnieChaguluka-v5u
    @AnnieChaguluka-v5u 9 днів тому

    Mkazi amakongola opanda makeup ngati Tamia ja osati enawa iyaaa

  • @user-ec4jo9cu4d
    @user-ec4jo9cu4d 3 місяці тому +1

    This is true story u bring out

  • @user-ym4kf9it2d
    @user-ym4kf9it2d 2 місяці тому +1

    Zose iziii wananena apa ine ndikuwaposa kukongola koma ndalama akundiposa osati kungongola ndiwe galu kwabasi

  • @ChantelleBanda-mn7no
    @ChantelleBanda-mn7no 2 місяці тому +3

    Ndiye bola mary yo zinazo mbuzi

  • @mustafailanga5010
    @mustafailanga5010 2 роки тому +2

    mukanangoti amazing Ali ndi ndalama akumalawi ndi away osati okongola

  • @Olivia-ep9qk
    @Olivia-ep9qk 2 місяці тому

    All women we are beautiful ❤

  • @danjaishmael8554
    @danjaishmael8554 3 роки тому +4

    Wendy Harawa l agree that woman is beautiful 😘😘😘💪

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 6 місяців тому

    There's no one here who's most beautiful than my wife❤❤❤❤❤❤❤ she's my Queen

  • @giftsaidi
    @giftsaidi 6 місяців тому +2

    mwaika anthu otchuka osati okongola chifukwa mu top 10 simungangoika zidebe zokha zokha zoti sizingayende pansewu zopanda makeup

  • @uzaleuzale8603
    @uzaleuzale8603 Місяць тому

    Amaii ine hilco and litah 🙈🙈 alikut kt mukaikepo dorothy

  • @AliceMalongo
    @AliceMalongo Місяць тому

    Wendy 🥰🥰

  • @TariroTobias
    @TariroTobias 9 годин тому

    Kwa ine ndemukunama sakafikirepo Koma mungoti mwaponya anthu atindarama osati owoneka bwino ayi ndiwe galu kwabasi

  • @user-bh7hf5lw5l
    @user-bh7hf5lw5l 6 місяців тому

    Exellent my home country Malawi Never knew they are so much beautiful ladies I am proud of you ladies and my home country God bless Malawi

  • @LovenessChinyama-xs4ke
    @LovenessChinyama-xs4ke 4 місяці тому +1

    Ndekuti namizatu, hahaha list ya ma celebu okongola yake nde ya ziii tu

  • @ednanamboyachilambe6901
    @ednanamboyachilambe6901 6 місяців тому +1

    Marry chilima yekhayi ndiye ndizoona BASI

  • @SaizNankambe
    @SaizNankambe 2 місяці тому +1

    My wife is the best ❤

  • @BlessingsKwerani
    @BlessingsKwerani 24 дні тому

    For me Jetu must be no 4

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 6 місяців тому +1

    Mkadzi wanga ndi mbambande zinazi njeeeeeeeee

  • @user-cq1wv9nq4y
    @user-cq1wv9nq4y 5 місяців тому

    I think Getrude Munthalika deserves to be in

  • @user-zb5be9kc9b
    @user-zb5be9kc9b Рік тому

    WOW Mama Mary bushiri i love you

  • @ErnestSakhula
    @ErnestSakhula 15 днів тому

    Ruth Sika please

  • @EuniceChanga-qd5zv
    @EuniceChanga-qd5zv 2 місяці тому

    Mary was a supportive partner wow

  • @LalonaKamanga
    @LalonaKamanga 2 місяці тому

    This is true, mary is number 1

  • @TendaiBongololo-z3h
    @TendaiBongololo-z3h Місяць тому +1

    Mary chilima ekhayu nde ndizoona

  • @TamalaMwale-b2z
    @TamalaMwale-b2z Місяць тому

    Aaaaaaa
    Mayanga is beautiful

  • @VioletSinyangwe
    @VioletSinyangwe 2 місяці тому

    Pa kalista it's true zinaz bodza

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga Місяць тому

    Mukunamizana kwambili kuli anthu okongola mizimu 💪💪💪 not zomwe mwapanga post apapazi chifukwa chakuti ndizot.chuka kale.

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Рік тому +2

    Ine ndingoopnapo Wendy yekha zinazi zidina zenizeni

  • @harveybanda863
    @harveybanda863 Місяць тому

    Understand the narrative please..... Beautiful female celebrities.... Meaning those other beautiful girls you are thinking of are not popular and not celebrities.

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 місяці тому +1

    Kkkkk koma list iyi njopatsa phwete abale azanga ,

    • @bernaphiri
      @bernaphiri 2 місяці тому

      Ndipo ndaseka mwava 😅😅

  • @giftkanjuchi-qm8hf
    @giftkanjuchi-qm8hf Рік тому

    Mrs grace Kanji hi my wife is number 1

  • @kingogasteney
    @kingogasteney Рік тому

    Eu voto na senhora princesa chissulo

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 6 місяців тому +1

    Wi-Fi yanga ineee yapangisa Kuti ndione zasayenera😢😢😢😢😢😢😢😢

    • @MarvellousTech-kz6no
      @MarvellousTech-kz6no 2 місяці тому

      Hahaha koma zinazi m mimba mukuwawa ndikuseka

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 2 місяці тому

      @@MarvellousTech-kz6no 😃😃😃😃😃😃😃Ine ndie Mpakana mutu kuwawa mmmm😃😃

  • @jangiya03
    @jangiya03 5 місяців тому

    This is not about beauty but popularity

  • @tinamanda9138
    @tinamanda9138 2 місяці тому

    Palibe zokongola yapa . Anakati mkazi wochuka .aliyense mkazi payenkha ndi wokongola. Inafe ndife wonyansa?

  • @user-jg3mq4iy6u
    @user-jg3mq4iy6u 2 місяці тому +3

    I think the issue here is about popularity but if it's about the beauty then there was a wrong observation.

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 місяці тому

    Zochititsa manyazi kuti Ku Malawi akazi okongola asowa , kuyesetsa kukokera kuti mwina kapena , kukongola sindalama koma maonekedwe abwino osati izi zili yapazi ayi , azigogo okhaokha kkkk , kodi atsikana kulibe , zamalodza izi

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f Місяць тому

    Inu ndinu abodza bwanji aaaaa paliso zokongola apa zinqzi nde zabodza

  • @IssahHussain-pe4ue
    @IssahHussain-pe4ue Місяць тому

    Aaaa apa nde watinamizat

  • @HopellaBanda
    @HopellaBanda Місяць тому

    A Dorothy wo ndiye mwatinamiza

  • @giftngwira4928
    @giftngwira4928 3 роки тому +5

    🤣🤣🤣 koma inu ankazanga munawaona? Mpaka kaliyati😂😂

  • @davidlungu5215
    @davidlungu5215 6 місяців тому

    Koma chimasowa ni mupata,,,💋💋💋💋
    Kkkkk😅😅😅

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke 21 день тому

    What about Triphonia Mpinganjira

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Місяць тому

    Kunena chirungamo.apa simunayike akazi okongola ayi munayika akazi oremerakwambiri anamadya bwino sinilumuonapo okongola apa

  • @MphatsoKamande
    @MphatsoKamande 2 місяці тому

    I think we don't have beautiful ladies here in malawi

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f Місяць тому

    Kodi anthu enawa mwati kuntchena or kukongola😂😂😂😂😂😂😂

  • @SabinaNkhoma-sf7kz
    @SabinaNkhoma-sf7kz 2 місяці тому

    Akadapanda kuphoda tikadaona kt bultifull ndindan

  • @MirriamKambale
    @MirriamKambale 2 місяці тому

    She's more beautiful without makeup I mean # 1she really deserve the number sizaenawa nkhope ngati akuchoka kudambwe hiya kuimbira nyau kwambiri pano anayamba kuoneka mwauthakati eee despite being on top of Malawi osatsungulabe eish zknaukaona tortoise like a stone

    • @bernaphiri
      @bernaphiri 2 місяці тому

      Ndipo inu number 1 yekhayo nde oyenera zinazo tikambabe hiyaaa

  • @giftkapichira1633
    @giftkapichira1633 Місяць тому

    Mpaka kaliati eeeeh😂😂😂

  • @EmilyMlotha
    @EmilyMlotha Місяць тому

    Mukungoononga ambili ya malawi mukanangoti akazi otchuka asaa mkazi chilima ekha apa,

  • @zamiwenkosi6810
    @zamiwenkosi6810 2 роки тому +1

    Aliyense ndiwokongola

  • @marianyirenda
    @marianyirenda Рік тому +1

    Koma Malawi ndi dziko lomvetsa chisoni abale inu ,zoona nkhalambazi ,kuteroko anthu akungoseka ku mayiko ena

  • @user-ym4kf9it2d
    @user-ym4kf9it2d 2 місяці тому

    Pa number 10 mwayipara 😂😂

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Місяць тому

    Agwambawo nde mwangowapakatu 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @katheychikoko4678
    @katheychikoko4678 16 днів тому

    Mhuuuuuu 😂

  • @obisanto3615
    @obisanto3615 2 роки тому +1

    Bolaso mkaz wanga apa palibe angamuponse

  • @KeddwaBenjaminMkandawire
    @KeddwaBenjaminMkandawire 2 місяці тому

    Better awo anumber 2 akuonekako bwino ma hips

  • @user-eu7ws6yk4c
    @user-eu7ws6yk4c 2 місяці тому

    My mother and my wife is very beautiful than anyone

  • @husseinmoffatt
    @husseinmoffatt Рік тому

    Thanks mr

  • @gymgrowth1817
    @gymgrowth1817 2 роки тому

    This is bushiti...don't underrated my country....

  • @PeacefulRiverboat-iw3eu
    @PeacefulRiverboat-iw3eu 2 місяці тому

    Anthu otchuka okha okha Pitani mudzimu money beautiful ladies

  • @SalaJawali
    @SalaJawali Місяць тому

    Mkazi wa mulaka maliro alikuti apa

  • @EstherDebwe
    @EstherDebwe 5 місяців тому

    Enawotu amakongola akaphoda koma ndy bwenz mukumawonetsetsa zinthuzi😂

  • @willsonmzumala
    @willsonmzumala Рік тому +1

    Vuto simunaoneko Akazi anga, Onsewa atha kukhala Number 11 kumapita uko😂😂😂

  • @yohanenyasulu
    @yohanenyasulu 2 місяці тому +1

    Zabodza izi

  • @user-ou8ng5kb2n
    @user-ou8ng5kb2n 5 місяців тому

    Sorry but zonse ndinkhalamba komaso mulungu analenga aliyense kuti ngokongola nyasi popularity

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 місяці тому

    Kodi atsikana kulibe munayika azigogo okhaokha ?zoona mayiko akunja adziona zimenezi , hahaha

  • @user-nd8ev3gl2l
    @user-nd8ev3gl2l Рік тому

    Mayi chirima

  • @munirarazakissa1404
    @munirarazakissa1404 Місяць тому

    Zi make up zili thoo

  • @user-ll3qi5im7x
    @user-ll3qi5im7x 5 місяців тому

    Ine andekha ndi beautiful kale❤

  • @OliveMukhuna
    @OliveMukhuna 2 місяці тому

    Asaaa mpaka princes chisulo ndi kaliyati mwatilakwilatu kobasi

  • @angellamakamula3606
    @angellamakamula3606 2 місяці тому

    Mulungu atamaliza kumulenga munthu, kumusiya mu m'dziko anati zilibwino, aliyense ndiokongola

  • @user-xx4mt8ox8e
    @user-xx4mt8ox8e 2 місяці тому

    You haven't seen my wife she's number 1 in the whole world