im from zimbabwe .i dont even understand the lyrics but eish you guys you underestimate this guy eli njuchi ......i have been repeating this song since yesterday much love
Based on my Intellectual Capacity and my vast Knowledge, Tactically and Tentatively, right from the beginning of the times Especially in the light of Eccentricities evolution, I have come to a concrete, Definite and profound conclusion that ikufunika gugugu cover in Maule message. This song sound ngati yomvera noti yovina.. so people like dancing not listening
chomwe satha Eli Njuchi mwina ndikutamba kokha otherwise eheh💯🥵🥵
Batiliso ndi dolo ?????
Nice and siple... Tose ndi a bullets koma ndifukwa cha mavuto osiyana siyana Ena anabalalirika ndikulowela kwina, koma pasi pa ntima ndi athu ndithu
😂😂😂😂😂
Hindeee 😂😂
Hahaha
Neba samagona tulo😂😂😂, iwe mutu mwakomo muli nyimbo migolo migolo Eli njuchi eeee👐 ❤❤❤
Pansi pa mtima nae neba ngwa Maule 🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳
For the love that I have for Eli njuchi I can't stop listening to this song.. though I do support mighty mukuru wanderers
im from zimbabwe .i dont even understand the lyrics but eish you guys you underestimate this guy eli njuchi ......i have been repeating this song since yesterday much love
Iweyo nd 1 ase... I support you n i will start supporting yo team too😊
Wina aziyimba kuti nzafera Mahule trust me
I support you 😂😂😂
Zoona ase
Maule 🔥
𝐌𝐭𝐰𝐚𝐧𝐚 𝐲𝐚𝐦𝐢.....𝐅𝐨𝐥𝐥𝐨𝐰𝐢𝐧𝐠 𝐲𝐨𝐮🎉
Kkk
In my country we ve several language but when it comes to music we communicate in one language my village Pipo mulipo
Fire Maule🔥🔥🔥🔥 fire njuchi🔥
Mmmmm ndine wa Maule km iyi Eli sunayimake km mafo ndi shoez Aja ndimadoro
straight skukwanila
Ma banker let's gather here
Maule let's gather here,mwana uyu ndiowopsa
No worlds to utter.🎉🎉🎉🎉🎉
Am a Suppoter of Maule and a topfan of eli njuchi 🔥🔥
Pena kuzaveka ngat yachikondi🥱😆🤪sikundimvekela ngat yamaule mmmmm amene mugwirizana nane like osaumila😂😂😂
Neba wangayu samagona tulo pansi pamtima naye ngwa Maule🇮🇩🇮🇩⚽️⚽️⚽️⚽️⚽️🔥🔥🔥
Am Banker ( Silva ) for life koma this song eee
Ife olo atatimanga nyakula tizafela maule ❤
Mbuye mpata ukapezeka ❤❤❤❤
Pansi pa mtima nayenso ndiwa maule 🇦🇹🔥 🇦🇹🇦🇹
Maule. Is. My. Favorite team. I. Love. It. So. So. So. So. Much
𝐌𝐰𝐚𝐧𝐚 𝐰𝐚 𝐂𝐡𝐚𝐛𝐞
𝐍𝐉𝐔𝐂𝐇𝐈 🔥🔥🔥
Pansi pa ntima naye Neba ndi wa Maulle 🔥🔥
your biggest fun from zambia high five bro ndiwe star
Eli ❤️🔥🔥
#GOAT🔥✌🏾
Used to be a fan koma zomwe wapangazi zandinyansa😅..ole ole manoma❤
Pansi pa mtima naye neba ngwama hule 💥💥💥🔥🔥😔
Love song for maule 😅😅😅😅 olo kusapotako kuyambila pati ati mahule
Hit bro...💪😊 💥💥💥🎉🎉
❤❤❤🎉komaya tili. Limodzi osaopa❤
Iyi mwapha man ngati siyochenelera Maule you got vibe bro keep up the good work
Based on my Intellectual Capacity and my vast Knowledge, Tactically and Tentatively, right from the beginning of the times Especially in the light of Eccentricities evolution, I have come to a concrete, Definite and profound conclusion that ikufunika gugugu cover in Maule message. This song sound ngati yomvera noti yovina.. so people like dancing not listening
Ineyo dzafera maule basi ,Iweyo Eli Njuchi ndi one
Ole ole💃💯💯neba naye ndiwa Maule inu💃💃❣️❣️
Apapa ndy neba wamva kutetha ndithu Maule more 🔥🔥🔥
Manoma let's gather here😂😂😂😂
Kuti mutani sopano
Kusokoneza
Basitu ndamutuluka kapoloyu
@@PrinceMapemba-fn4cwsisikugwiridzana mkulu don't be too emotional. Iye akukamba timu yomwe amakonda basi🤣
Tilipano 😂😂😂😂😂
Maule moto ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤ Muti thuya maule
🔥🔥🔥🔥🔥♥️
Ife a Noma takutsika
Sitingadumphire pa stand. Imbani Ina yobeba
My Team
Maule woyeeeeee🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳
🔥🔥🔥
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
🎉🎉🎉🎉 zafela mahule ..
Maule I mean😂😂
Good sound here KPix from Mozambique
❤❤❤
nyimbo yochemelera team ngati yachikondi aaaa watipaka
in my head `ndizafela mahuleeee`
Wakwela yowina aseh 🔥🔥🔥🍒
Big up Eli neba pansi pa mtima ndiwa maule😛
MAULE for Life 🔥🔥🔥🔥
The peoples team let’s gether here ❤
Mwapha ❤
🔥🔥🔥🔥
Iyi ili mwala😊
❤❤❤❤❤❤
Eli ❤️iweo ndi GOAT🔥🔥
@Eli Njuchi, panganinso ya *Popita munditenge*
Ipatse 🔥
Koma ndipo uyuyu anafika kom mmm kumapatsan uremu kom mmm
Neba pano sakugona pano ndinyimbo imeney
Nyimboyi siyabwino, I was expecting more than this
Imbani yanu yabwino ife tipange expect more than yanuyo😏
Ifewo tidzafera mauleee❤❤❤ 🔥 🔥 🔥
Ife nga noma moto buuu❤❤❤
Ndazikonda nyimboyi ❤❤❤❤❤
🔥🔥🔥🔥🔥🔥😭
Maule woyeeeeee
Mn yr so Tallent ❤
There is no song on this current album Iam listening at. All wack tracks. Koma na iyiyi nde ndikusunga adha. Atleast I have something now
❤we are 🎉🎉
Muzaferadi mahule😂😂
Victorious we go !!!!🎉
It's Maule tings 🔥🔥🔥🔥
Maule for life
Maule let's gather here
I can't even like or share,, 😢😢
Nice song koma tonse sitingakhale a bullets kkkk
Apa nde ndakutuluka ngati momwe ndinatulukila dan luu atayamba kuyimba zandale
Koma ndie bola yamafo ija iyi ngt yaukwati or maliro😭😭😭😭💔😂 No molaro
Maule ❤❤❤
Lero neba atiliraso patii?
Mahule
Yeye
Ole ole zafela maule
Maule basi 🎉🔥🔥🔥🔥🔥🔥
On Point ❤🎉❤🎉💯%......!!
Maule woyeee 🔥🔥🔥🔥
Hizoooo🎉🎉🎉
Ndine neba km Maule ijayo🔥🔥
Nyas. Bgbbulrt
Mwati mahule ,,
Tidzafela mahule
Eyah km noma iwina
I'ma ife tiphe Cha wanderers tiposa yakoyi
Maule🔥🔥
Neba ife imati pweteka ndiya Mafo Ija
Pansi pa mtima maye mngwamaule
Inenso dzafela MAHULE!!
Maule let's gather here the people's team 🔥
Ipemelele
Eli 🤸🤸ndfera maule 💪💪
Nyimbo zake ndidilite😅