Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Mr president wathuwathu ai zikomo mwayakhula chakwera sindimvetsa ndithu! Kapena sayakhula alibe pakamwa!
Iwe born kalindo ndiwe chisiru kwambili kodi uzingokhalila kubwebweta iwo atenga zikwanje inuso muzatenge zikwanje osamangowanyengela iyaaaaaaa
Ku office ya MCP chakwera Adali ndi ambassador WA Ku American *Virginia parmer* inu ndi oopsyadi kwambiri Mr president wathuwathu
Box 26 mulanje Malawi southern Africaaaaaaaa The DCCCCCCCC booooon kalindooooooo ooo.Timkanena anatsilira mumsiizi
Box # muimvesetse
Ganizo la Mai kaliati silabwino anazilakwitsa okha anaenera kuima pa udindo wa secretary General definitely akanawina opanda opikisana naye
❤❤❤❤❤❤ Boni🎉🎉😊
Kodi pano zayamba kuopsa eti? Nthawi yomwe ana adad amamenya anthu atakwera Galimoto ya police simumaona? Zomwe anadzala a DPP akukolora panopa
MCP ndichipani chankhaza
Its stupidity ku opposition kukanika to overpower azikwanjewo
Alkalindo kodi mesa ndiinu nomee munkatiuza kuti tivotele agalu wa? Lero nde mukuti chani? Musatinyase khalani pheee uchitsiru sagawana kuophya kwake kuti za ziiii
Inuchakwer ndi satanic uyo anagurisa mzimu wache ku ndim
Inuyo ndi mbuli pa chakwera amene uja ndi satana weniweni osati inu ndi mene mukuganiziraso kumene kuja kukuonezerani kuti amene uja ndi wakulu wasatanic ndiye inu siyani kulubwalubwa kwanuko
❤❤❤❤❤❤❤karido
Ambuye atimenyere khondo asapitilire 2025 ameneyi
Pajatu ndinu nomwe munatipopa kuti tivotere zipani zanu zomwe zinali mu alliance nde ndi zimenezo apa mumatha kuyankhula koma simukutilelesa
MCP yisapite kwina kulikose kukapanga musonkhano kaya ndinduna zawo azipanga mulilongwe akatuluka akamenyedwe
Khondo iyi sopano amalawi
Mulungu azikudalitsa
Zana kumayamikila zimenezi zinachitika ku ndilande lelo ndizi ukuzuzula ndiwe galu kwabasi
Musapange support zinthu zoipa, kudziwikirathu kuti mutu wanu ndiozizira
Nanga zomwe zinachitika time DPP ikupita Ku mchinji zinali zabwino
Achina chikangwa mcp machimo
Where is MDF?
yiweyo Bon kalindo ungoziya
Language yanji imeneyo
iwe ndi mwana oopya kwambiridi komano what action do u take to save Malawians instead of speaking unsound voice
*Mulungu simunthu*
The Dc
Kkkkkkk kapwitika!!!!!
Ure the one who put in this mcp in government so always doing same thing
Achokegaruyo